MUTU 3

1 2 Muchaka chakumi ndi tusanu pamene analikulamulila Tibarias siza_ pamene ponshas paileti anali mukulu wa boma mu judeya, Helodi anali tetrachi wamu galili, mubale wake philipu anali tetrachi muchigao cha ituriya ndiponso trachonitis, ndiponso lysanias anali tetrachi wa Abileni, ija nthawi ya opelekanse ya Annas ndiponso kefasi_ mau ya Mulungu wanabwela kuli Yoani mwana wa Zakaliya, muchipululu. 3 Anaenda muchigao chozungulila Jodani, kutumikila ubatizi olapa pa kukululukila kwa machimo. 4 Monga vamene chinalembedwa mubuku ya mao ndi Yesaya muneneli, ''Liu laumozi lilikuitana muchipululu, 'Konzekani njila ya Mulungu, konzani njila yake iyondoloke. 5 6 Chipululu chilichonse chizazozedwa, ndiponso phiri ili yonse izabwelesewa panshi, ndiponso njila iliyonse yosayondoloka iza konzewa ndi kuyondoloka, ndiponso ndi ijayosakonza iza mangiwamo manjila, nkanda yonse izaona chipulumuso chamulungu.'' 7 Ndipo Yoani ananena ku magulu yakulu yabanthu bamene banali kubwela kubadizika ndi iye, '' imwe bana banjoka!nindani ukuchenjezani kuti mutabe kuukali wamene ubwela? 8 Pokapo, belekani zipaso zamene zoyenekela ndi chilapilo, ndiponso musayambe kunena mwaimwe mweka, ' Kuti tilindi Abraham wamene alinitate watu; ninakuuzani kuti Mulungu akwanisa kunyamulamo bana ba Abraham mumwala izi. 9 Apamanje ndi katemo nikokonzeka kuchaya kumizhu zamitengo. koma mutengo ulionse wamene siupeleka zipaso zabwino uzajubiwa pansi ndiponso uzataiwa mumulilo. 10 11 Ndipo aya magulu yanapitiliza kumufunsa, ndikunene, ''Kuti kansi tingachite bwanji?'' Iye anabayanka, ndi kunena kuli iwo, ngati winawache alina na zovala zibili, afunika kugabana ndi mumunthu wamene alibe, ndi uja alina zakudya afunikila kuchita chimozimozi.'' 12 13 Baja otenga misonko ndi iwo anabwela kubadizika, ndiponso ananena kwa iye, ''Mupunzisi, nichani chamene tingachite?'' Ananena kwaiwo, ''Musatenge ndalama zopitilila kupambana pazamene mwauziwa kutenga.'' 14 Basilikali ndiiwo anamufunsa, ndikunena, ''Nanga ise? Tizachita bwanji?'' Ananena kwaiwo, Musatenge ndalama kumunthu aliyense mokankamizila, ndiponso musakankamize kunamiza wina mopatikiza.Munkale okutila ndizamene mufola.'' 15 16 Koma pamene banthu banali ndi chilakolako kuembekeza kubwela kwa kristhu, aliyense anali kuzifufuza mumitima mwao paza Yoani ngati angankale kristhu. Yoani anabayankha bonse, '' koma ine, nikubadizani ndi manzi, koma alikubwela winawake wamene alina mphamvu kupambana ine, ndiponso siniyenela ndi kumasula ntambo zansapato zake.Azakubadizani ndi muzimu oyela ndiponso ndi mulilo. 17 Ndi chokololelako alinacho mumanja kuti awamise bwino gome yake ndiponso kukolola witi kufaka munyumba yosungilamo.koma azashoka zinyalala ndi mulilo wamene siusila.'' 18 19 20 Ndi bambiri enanso ozinyamula, Yoani analalikila utenga wabwino kubanthu. Pamene Herodi ndi tetrachi bana vomekezedwa kukwatila mukazi wamubale wao, Helodias, ndi zinthu zonse zonyansa zamene anachita ndi Helod, anafakilako pamilandu zonse zamene anachita: anakomela Yoani mujele. 21 22 Manje chinabwela chachitika kuti, pamene bonse banthu anabadizika, Ndi Yesu anabadizika. Ndiponso pamene akali kupempela, kumwamba kunaseguka, ndi muzimo oyela anabwela pansi muchifanikizo chatupi monga nkunda, ndiponso liu linabwela kuchoka kumwamba, '' Ndikuti iwe ndiwe mwana wanga mwamuna, wamene nikonda. Ndine okondwela ndi iwe.'' 23 24 Pamene Yesu anayamba utumiki wake, Anali ndi zaka makumi yatatu.Anali mwana mwamuna(wamene benzoganila) kuti ni wa Yosefe, mwana wa Heli, mwana mwamuna wa matthat, mwana mwamuna wa Levi, mwana mwamuna wa Melchi, mwana mwamuna wa Janani, mwana mwamuna wa Yosefe. 25 26 Yosefe anali mwana mwamuna wa Mattatiyas,mwana mwamuna wa Amos, mwana mwamuna wa Naham, mwana mwamuna wa Esili, mwana mwamuna wa Naagi, mwana mwamuna wa Maati, mwana mwamuna wa Mattatiyas, mwana mwamuna wa Simeni, mwana mwamuna wa Yoseki, mwana mwamuna wa Yoda. 27 28 29 Yoda anali mwana mwamuna wa Yoanani, mwana mwamuna wa Resa,mwana mwamuna wa Zelubabel, mwana mwamuna wa Salathieo, mwana mwamuna wa Neri , mwana mwamuna wa Melchi, mwana mwamuna wa Addi, mwana mwamuna wa Kosamu, mwana mwamuna wa Elimadam, mwana mwamuna wa Er, mwana mwamuna wa Yoshua, mwana mwamuna wa Elyaza, mwana mwamuna wa Yorimu, mwana mwamuna wa Matthat, mwana mwamuna wa Levi. 30 31 32 Levi anali mwana mwamuna wa Simoni, mwana mwamuna wa Yuda, mwana mwamuna wa Yosefe, mwana mwamuna wa Yonam, mwana ,mwamuna wa Eliakimu, mwana mwamuna wa melea, mwana mwamuna wa Menn, mwana mwamuna wa Mattatha, mwana mwamuna wa Nathan, mwana mwamuna wa Davidi, mwana mwamuna wa Yesse, mwana mwamuna wa Obed, mwana mwamuna wa Boazi, mwana mwamuna wa salmoni, mwana mwamuna wa Nahashoni. 33 34 35 Nahashoni anali mwana mwamuna wa Aminadabu, mwana mwamuna wa Adimini, mwana mwamuna wa Arni, mwana mwamuna wa Heziron, mwana mwamuna wa Perezi, mwana mwamuna wa Yuda, mwana mwamuna wa Yakobo, mwana mwamuna wa Isaaki ,mwana mwamuna wa Abraham, mwana mwamuna wa Tera, mwana mwamuna wa Naha, mwana mwamuna wa serugi, mwana mwamuna wa Reu, mwana mwamuna wa Pelegi, mwana mwamuna wa Eba, mwana mwamuna wa Shelah. 36 37 38 Shelah anali mwana mwamuna wa Kanani, mwana mwamuna wa Arphaxad, mwana mwamuna wa Shem, mwana mwamuna wa Noah, mwana mwamuna wa Lameki, mwana mwamuna wa Methusela, mwana mwamuna wa Enoki, mwana mwamuna wa Yared, mwana mwamuna wa Mahalaleel, mwana mwamuna wa Kenani, mwana mwamuna wa Enosi, mwana mwamuna wa Sethi, mwana mwamuna wa Adam, mwana mwamuna wa Mulungu.