Mpambo 3

1 Mapeto yake aalewanga msangalale pakati pa ambuye sindione mavuto kukulembe lamincho mau yayaja mkani izi sizikupacheni kuleme kwa bwino. 2 Mjipenyelele ndi agalu mjipenyelele ndio chita nchito oyipa jipenye leleni ndi achameneo aya kana maina yao. 3 Chifukwa ife ndiachameneo owo taswidi ife ndiachameno ti mpempa Mulungu kwa mpavu za Mzimu Oyela tikulupalila Yesu Kristo ndi achemeneo filibe mpavu ya mofupi. 4 Atachimwecho ngati kudakakola ndi muutu wokulupalila tupila ine ndikade koza kuchila chimwecho kupunde. 5 Chifukwa ndida suwidwa pa nyengo ya nane ni debadwa pa kamule Iziraeli ine wkamu le Benjamini ina ndili Muebrania wa Waebrania pakupeza mfe ndele wa malamulo ya Musa ndi dali farisayo. 6 Kwa pamvu zanga ndideli chaucho chaucho kanisa kwa muvemelezo uzene wa lamulo. Sini dedandaulidwe pamedandaulo ya lamulo. 7 Nampo pakati pamkani izi ndida zione kutizilindi ueneleli twaine ndida welenga ngati zinyalela chifukwa cha kunjiwa Kristo. 8 Chauzene ndiya walenga yonche yeya kuti yowanangika kuchokela ubwino wakumjiwa Mulungu wanga. 9 Ndijilangize mkati mwake andilije lamulola lengalanga kuchokela kuchokela lamulo ikapanda ndilinelolemeo lija lipezeka kwa chikulupalilo pakati pa Kristo ichokela kwa Mulungu lili ndi chiyambi pakati pa chikulu palilo. 10 Chapano ndifuna kumjiwa mmenayo ndi mpavu ya uzuka kwake ndi umoji wa mavuto yake. Ndifuna kunganemulidwa ndi Kristo pakati pa moyaluzo ya nyifa yake. 11 Mbasako ndikale ndi chikulo pi paku zuka kwa wantu amene adefa. 12 Osati zene kuti noyapeze ya meneyo kapena kuti ine ndili wabwino kupunda paya meneyo ikapanda ndiji kakamula kuti nikoze kupeza chija chipatikana ndi Kristo. 13 Abale wange siniganize kuti nato kuyapeza machitidwe yoya ikapanda ndichiti chimfu chimoji ndiwalila ya mmbuo ndi ya penya ya mchogoro. 14 Ndiji kakamula kuti ndifike umo ndifunila dala kuti ndipata mpaso ya ikuhe pa mwamba pakutanidwa ndi Mulungu pakati ndi Yesu. 15 Taoche ta pulumuko tifunidwa kuganizila chimwecho, ndingati sikale mwino watu waganizile kwa mtundu wosiana pankani iliyonche Mulungu noyenche siwkulangizeni limenelo kwanu. 16 Ngati mmenemo ti tiyende ngati umo ili. 17 Achenjanga ndi chefeni ine apenyechecheni kupunda achemene ayenda ngati umomuyendela amuya imure. 18 Ambili alama nde achemeo ntawi zambili no kukambilani ndicho pamo ndikukambileni kwa masozi ambili alamo ngati adawi a mtanda. 19 Mapeto yao kuwanengi kudwa chifukwa Mulungu wao tumbo ndi mbwinya zao zilincho nizao aganizile nkani zajiko. 20 Ikapande maloyatu yaliku mwamba kumeneko tikulupalila mpulumuchi watu Yesu Kristo. 21 Siwangane mule metupi yatu yamere yalife mpavu kukale ngati kwa mpavu zimwezija zikozeche kuvimonga vintu voche.