Sura ya 6

1 Pambuyo pankanizi Yesu wadaenda pampepete za Galilaya, ota chimwecho itanidwa nyanja ya Tiberia. 2 Msonkano waukuru adali mkumchata chifuko adaona chilangizo wamachichita kwa achaamene adali odwala. 3 Yesu wadakwela pamwamba kusikwa pamwamba papili ndi wadakala kumeneko ndi oyaruzidwa wake. 4 (Ndi Pasaka,sikuku ya Ayahudi idali ndi iwandikila). 5 Yesu yapowadakweza maso yake kwamba ndikuona lintu lambili uli mkuja kwaiye wadamkambila ilipo sitipite kuti kukagwa mikate dala anyiyawa akoze kudya? 6 (Nampo Yesu wadayakamba yaya kwa ilipo pakumuyesa chifukwa iye mwene wake wadajiwa icho siwachidie). 7 ilipo wadayankha, "ata mikate ya ndekana anike siungakoze kulamicha wanthu wonche ingakale waliyenche wakada peza pang'ono." 8 Andrea mmoji wa oyaluzidwa wake m'bale wake Simoni Petro wadamkambila 9 Yesu "kuli mnyamata pano wali ndi mikate isano ndi nchomba ziwili nampho siitandize chiyani kwa wanthu ambili ngati anyiyawa?" 10 Yesu wadamkambila, "akazikeni panchi wantu" 11 Pambuyo Yesu wadatenga iji mkate isano ndi kuyamika ndi kwa agawila anyiwaja adakala panchi chimoji maji wadanagawila nchomba kwa mmene adafunila. 12 Wanthu yapo adakuta wadaakambile ajiyaluza wake viikeni limoji vodulidwadulidwa vokala vokalila dala kuti sichidataika chilichonche. 13 Mmwemo adaviikila limoji ni kutila misece iwili vodulidwa va mikate ya nganovidachurukila ndi achameneo adadya. 14 Pambuyo wantu yapo adapenya ine chitidwe ya chilangizo adanena "chazene uyunde yuja olosu." 15 Yesu yapo wapo wadajiwa kuti ameuna kumgwira dala kuti amchile umu wao wadajiike pamphepete ndiwadapita kupiri iye yeka. 16 Yapo idali ujulo oyaluzidwa wake adachika kupita kunyanja. 17 Adakwera mbwato ndi amayo mboka kupita Kukapernaumu. (Mdima udalowa ndi Yesu wadali wakali osaika kwa anyaiwo). 18 Ntawi imeneyo mpepo ya mpavu idali mkupepeta ndi nyanja idali ndi inyendekela kuwangika. 19 Ndipancho oyaruzidwa wake pamene amapalasa nkafi ngati ishirini ndi zisano kapena thelasini adamuone Yesu ndiwayenda pamwamba panyanja kuwandikila bwato ndi adaopa. 20 Nampo wadaakambila, "ndiliine msada ndiopa." 21 Ndiponcho adakala ajikonja kumbara mbwato ntawi yomweyo apeze bwato waika kujiko limenelo anapita. 22 Siku limechatira msonkhano udaima kumpepete mwanyanja ndi adepenya kulibe bwato ulionche ikapanda umweija Yesu ndi oyaluzidwa wake siada kwelemo nampo oyaruzidwa wake adapata achinawene wake. 23 (Ingakale padalipo mbwato yochepa kuchokela Tiberia paupi ndi malo amadyela mikale pambuyo umu kuchocha mayamiko.) 24 Ntawi msonkhano yapo udajiwa kuti osai Yesu ingakale oyaruzidwa wake adali kumeneko nchuke wene wake adakwera mkati mamabwato adapita kukapera nami kupita ndia muneune Yesu. 25 Pambuyo pakumpeza maloyena yanyaiya adamfuncha, "Rabi udajaliti kuno?" 26 Yesu wadayankha wadaakambila chazene mundifunefune ine. Osati chiukwa mdeona malangilo nampo ndande mdedya mikate ndi kukuta. 27 Siani kuchilichitila nchito chakudya eno wanangika nampo mchitile chito chakudya cholana ntawi zonche chija chimene mwana wa muntu siwakupacheni chifuko cha Mulungu tate waika chizindikililo pamwamba pake. 28 Pambuyo anamkambila, "chiyani tiunka kuchita dala kwachita nchito za Mulungu?" 29 Yesu wadayankha, "indechito ya Mulungu kuti mumukurupalile iye watanidwa." 30 Mmwemo adamkambila, "ndi chizindikililo chiti chimene ukoza kuchita dala tichione ndi kukurupalila? Siuchite chipalilo? 31 Achaatata watu adadya mkate pandanga ndenga ngati mmene idalembedwela wadaapacha mikate kuchokela kumwamba dala adye." 32 Pambuyo Yesu wadayanka, "cheza chazewa osati Musa wadaapacha mikate kuchokela kumwamba ikapanda atate wanga nde mmeneyo wakapechani mikate yazwe kuchokela kumwamba. 33 Pakuti mkate wa Mulungu nde uja uchika kuchokera kumwamba ndi kumpacha mtendele jiko. 34 Adamkambila, "umu tipache mkate umeneo ndawi yonche." 35 Yesu wadaakambila, "ine nde mkate wa mtendele imene siwaje kwaine siwapeze njara ndi mnene siwakulupalileswapeze rujo." 36 Ingakale ndidakukambilani kuti mwandione ndi mkali osadiona. 37 Wonche achameneo atate andipacha siaje kwanga ndi waliyenche siwaje kwaine sindi msia kubwalo. 38 Chifuko ndechika kuchokela kumwamba osati yuja kuachita voune vanga ikapanda vochita vaiye wandipacha utenga. 39 Ndiyaya ndiyo yoana yake mwene wandipacha utenga kuti ndi sadamtaya mmoji waacha ameneo wandipacha ikapaga sinde abweze kumanda ntawi yotela. 40 Chifuko ichi ndicho chofuna tata wanga kuti waliyenche wampenya mwana ndi kumkulupalila wakale ndi mtendele woseta nanencho sindimbweze kuwanda ntawi yotela. 41 Pambuyo pake Wayahudi adamdandaulila kupande iye chifuko wadakamba ine nde mkate wachika kuchokela kumwamba. 42 Adakamba, "uyu si Yesu mwana wa Yusufu, mme tata wake ndi mayi wake timjiwa? Ikara bwanji chapano wakamba, nde chika kuchokera kumwamba?" 43 Yesu wadayankha wadaakambila msada dandaulane mmalo mwanu mwa achinawene wake. 44 Palije munthu siwaje kwaine popande kukokedwa ndi tata wanga wandhu pacho utenga nanencho sindimbweze kumalo ntawi yotela. 45 Chifuko yalembedwa mwaolopi, "siyaluzidwe ndi Mulungu." aliyenche wavela ndi wajiyaluza kuchokela kwa tata watu wa kuja kwaine. 46 Osati kuli Mulungu wamuone tate ikapanda mmene wachokela kwa Mulungu wamwe one atate. 47 Zindikileni wadakilani waliyenche wa kulupalila wali ndi mtendele wosata. 48 Inende mkate wa mtendele wosata. 49 Acha atate wanuadadya mikate pandenga danga ni adamwalila. 50 Uu ndi mkati uchika kuchokela kumwamba dala kuti wadyeke malo yake dala siwadamwalila. 51 Ine ndi mkate ulama umeneo wachika kuchokela kumwamba ngati munthu waliyenche siwadye malo yamkate uu siwalame vyaka vonche mkate sindiuchocho ndi tupi langa chiuko cha kakanidwe kajiko. 52 Ayahudi adakwiyilama achinawne ndi adayamba kukangana ndi akamba muntu uyu akoza bwanjo kutipacha tupi lake tidye? 53 Pambuyo Yesu wadaakambila, zindikilani ngati simudya tupi la mwana wamuntu ndi kuwa mwazi wake simkala ndi umoyo wosata mkati mwanu. 54 Waliyenche wakudya tupi langa ndi kumwa mwazi wanga wali ndi umoyo wosata nanencho sindi mchocho kwanda ntawi yotela. 55 Pakuti tupi langa ndi chakudya chazene mwazi wanga ndi chomwela chabarimu. 56 Mmene wakudya tupi langa ndi kuwa mwazi wanga wakala mkati mwanga nanencho mkati mwake. 57 Ngati atate ali ndi mtendele mmenemo anitumizila ine nde ngati umo ndili chifuko cha atate nayenche siwalame chifuko chaine. 58 Uu nde nde mkate uchika kuchokela ku mwamba osati ngati mmene adadyela anya atate ndi kumwalila mmene wakudya mkate uu siwakale ndi malamedwe yosafa. 59 Yesu wadakamba mau yaya mkati mwa koyumba ya Mulungu pamene wame yaluza kumene Kukapernaumu. 60 Nde pamenepo oyaruzidwa wake ambili adavela yaya adakamba, "ili ndenyaluzo lolimba yani wakoze kumlandila?" 61 Yesu chiuko wadajiwa kuti oyaluzidwa wake adandaulila nkani iyi adawauncha bwanji nkani iyi ya kudandaulichani? 62 Chapano siikale bwanji mkamwona mwana wa muntu ndiwachika kuchokela ukoesdsli mmayambo? 63 Mzimu ndi umeneo uchocha mtendele tupi silitandazika chilichonche mau neya kamba kwanu mtima ndi mtendele. 64 Mkali pakati panu amene sialolela." Chifukwa Yesu wadajiwa chiyambile mmayambo mwene yuja siakoze kulolela ndiye mmeneyo siwasanduke. 65 Wadaakambila ndi chifukwa chake ndidakukambilani kuti palibe muntu wakoze kuja kwaineingakale wapelekedwa ndi atate." 66 Pambuyo payameneyo oyaruzidwa wake adabwela mmbuyo ndi siada chatane nayencho kukalila limoji naye. 67 Yesu wadaakambila anyiwaja makumi ndi awili, "bwanji anyiimwe mufuna kuchoka?" 68 Simoni Petro wadayankha, "bambo tipite kwa yani mbona imwe mulinayo mau ya malamidwe yosata, 69 ndi favananavo ndikujiwa kuti iwe ndi muntu oyela wa Mulungu." 70 Yesu wadaakambila bwanji ine sindidakusankuleni anyiimwe ndi mmoji wanu si wabwino? 71 Chapano wa makambila nkani ya Yuda mwana wa Simoni Iskariote, chifukwa wadali iye wali mmoji wa anyiwaja kumi ndi awili mmene wa mafune mzukira Yesu.