1 Pambuyo yapamene padasi ndi sikuku ya Wayahudi, ndi Yesu wadakwela kupita Kuyerusalemu. 2 Ndikuja Kuyerusalemu padali ndi bikila pakoma pa mbelele, ilo limatanidwa kwa lukha ya Kiibraniya Bethzatha, nalo lili ndi vikhao visano. 3 Wandhu ambili odwala idalipo, sapenya, anyao adalumala adali agona makundi yayo chatilila. (Mau ya mzele waka 3 siyaonekana katika nakala ya bwino na kale amalindila maji kuvundulidwa). Kolongosola ndawi yakuti angelo wadachika mnyumba mwa Mbuye ndi kuyavundula maji. 4 Ndiposo yuja wadili oyamba kulowa mnyumba mwa badue maji kuvundulidwa wachitidwa kuvundulidwa wachitidwa kulama kuchokana ndi chilichonje chidali chamgwila ndawi imeneyo. 5 Ndi mundu mmoji wadali wadwala kwa vyaka 38 wadali mkati mwavi ngao. 6 Yesu yapo wadamuona wagona mnyumba ya vigawo ndi baada yojiwa kuti wagona paja pandawi yaitali Yesu wadamkambila, "Bwa ukonda kulama?" 7 Yuja odwala wadayanga, "Ambuye nilibe mundu, wakuniika mbilika yaoi maji ya vunduka, yapo niesa kulowa mundu mwina wanichogolela." 8 Yesu wadamkambila, "ukandi utenge tandiko lako upite." 9 Popo yuja mundu wadalama, wadatenga chitanda chake wadapita ndi siku limenelo lidali siku la sabato. 10 Chocho Ayahudi wadakambila yuja mundu walamichidwa, "lelo ndi siku ya sabata, ndi siuvomelezedwa kutenga tandiko lako." 11 Wadayanga, iye wanilamicha nde wanikambila, "tenga tandiko lako ndiupite." 12 Adaunja, "ndiyani wakukambila utenge tandiko lako upite?" 13 Ngakale, yuja wadalamichidwa, siwada mjiwe, pandande Yesu wadali wachoka kwa chisisi pakuti kudali ndi wandu ambili pamalo pamenepo. 14 Pambuyopo Yesu adampeza yuja mundu mnyumba ya Mbuye wadamkambila, "penya, walama! Usidachita machiminjo usidaja kupatidwa ndi machimo loipa kupunda." 15 Yuja mundu wadapita kwanikha ngani Wayahudi kuti Yesu ndeuyo wamlamicha. 16 Chocho pandande ya vindi vimene Wayahudi adammenya Yesu, pandande wadachita vindu ivi siku la sabato. 17 Yesu wadakambila, "Atate wanga apata njito mbaka chopano nane ndi chita njito." 18 Pandande imeneyo Ayahudi adapunda kuunauna ili ampe opande pe pandande ya kuityola sabato, ndipo kwakutana Mulungu atate wake, wamajitita kuti walingana ndi Mulungu. 19 Yesu wadayankha, "mvomele, mvomele, mwana siwakoza kuchita chindu chalichonje ingakale chinja ambacho wamwona atate wake wachichita, pakuti chilichonje tate wachichitacho ndipo ndimwana siwachichite. 20 Pakuti atate akonda mwana, ndi amulangiza kila chindu ichoachichita ndi samulangize vindu vavikulu kuposa yaya ndipa kuti muzidi kudabwa." 21 Pakuti ngati vija ambavo atate wanchavo wandu akua ndikwanikha umoyo, chocho mwananjo kunikha walionje wamkondwe. 22 Pakuti atate siatoza walionje, ndipo wanikha mwana kutoza konje. 23 Ndipo kuti onje amulemekeze mwana ngati vija mwana ivo walemekeza atate. Iye uyosiwalemekeza mwana siwalemekeza atate yao atuma. 24 Vomelani, vomelani, iye wavelae mau langa ndikuvomeleza iye uyowanituma walinao umoyo wa mtendele ndisiwatozedwa. Pambuyo pake, wapita kuchoka kunyifa ndi kulowa muufumu. 25 Vomelezani, vomelezani, nikukambilani ndawi ibwela ndi chopano ulipo uwo akua siavele mau ya mwana wa Mulungu ndioje yao savele salame. 26 Pakuti kuti vija atate ivo ali ndi umoyo mkati mwake mwene, 27 chocho wanikha mwana kukala ndi umoyo mkati mwake, nditate wanikha mwana madalaka ili kuti walamule pakuti ndi mwana wa Adamu. 28 Msidadibwichidwa ndi ichi, pakuti ndawi ibwela ambao wakua onje yao alimviliza savele sauti yake, 29 nao sachoke kubwalo kwa yao achita vabwino kwa kuchidwa kwa mtendele ndi yao achita voipa kwa kuuchidwa kwa kulamulidwa. 30 Sindikoza kuchita chindu chilichonje kuchoka kwanga namwene. Ngati umo ndivelela, chocho ndenilamula ndi kulamula kwanga ndi ya uzene pakuti sndiuna chikondi changa, bali chikondi chake uyo wanituma. 31 Ngati sindijakambile namwene, upungu wanga siudakakala wauzene. 32 Kuli mwina uyo wayaona kuhusuine ndijiwa pauzene uzene uwo wauwona ndi wauzene. 33 Mwamtuma kwa Yohana nae waivomeleza uzene. 34 Hata chocho, uzene uwo ndiulandila siuchokha kwa mundu ndiyakamba yaya kuti mkoze kupulumuchidwa. 35 Yohana wadali ndinyali iyoidali kwakundi kungala, ndimudali ovomela kuisekelela pandawi yaitali mulu yake. 36 Uzene ndilinao niwaukulu kuposa uja wa Yohana, panjito izo atate andipacha kuzimalizila, njitozo ndizichatazo zivomeleza kuti atate andituma. 37 Atate yao andituma iwo wene apenya kuti ine simudawai kuvela mau yao wala kuliona umbo lake ndawi iliyonje. 38 Palibe mau lake likakala mkati mwanu pakuti simumkulupilila iye watumidwa. 39 Uyo mumchunguza malembo ndi muganiza mkati mwake muli ndi umoyo wa mtendele, ndi yayo malembo yavomeleza khani yanga ndi 40 wimufuna kubwela kwanga ili mpate umoyo wamtendele. 41 Msidalandila sifa kuchoka kwa wandhu, 42 nambo ndijiwa kuti mulibe chikondi cha Mulungu mkati mwanu anyiimwe mawene. 43 Adabwela pajina la tate wanga, simudakoze kunilandila ngati mwina yapo siwaike pajina lake muda kumlandila. 44 Bwa, mkoza kuvananavo anyiimwe ivo mulandila sifa kuchoka kwa kila mmoji wanu nambo simulandila sifa kuchoka kwa Mulungu wa yoka? 45 Musadakhaniza ine sindikumangene pachogolo patate. Yao akumangani anyiimwe ndi Musa, uyo anyiimwe mwamuika chifuno chanu kwake. 46 Ngati mmakakala muvananavo va Musa, simudakananavo vaine pandande wadalemba kulingana ndi khani zanga. 47 Ngati simuamini malembo yake, simukoze bwanji kuvananavo malembo yanga?