Sura ya 4

1 Yesu yapo wadajiwa kuti Afasiri afarisi ajiwa kuti Yesu wali ndi omphuzila ndi kubatiza kuposa Yohana, 2 (ingakale Yesu mwenye siwama batiza ila omphuzi na wake), 3 wadachoka ku Yudea ndi kupita Kugalilaya. 4 Kwaicho kudali mate kupitila Kusamaria. 5 Ndi wadafika mujhi wa Samaria, uo utanidwa Sikari, paupi ndi liwala ilo Yakobo wadampacha mwana wake Yusufu. 6 Ndi chitime cha Yakobo chidali pamenepo, Yesu wadali walema chiukwa cha ulendo ndi wadagona pafupi ndi chitima. Idali nyengo ya usana. 7 Wamkazi wa Kusamaria wadaja kutunga majhi ndi Yesu wadamkambila, "ndipache majhi ndimwe." 8 Ndadnda omphuzira wake adapita kumzinda kukagula chakudya. 9 Yuja wamkazi wadamkambila, "ikala bwanji iwe Muyahudi, kundipempha ine wamkazi Msamaria, chinthu cha kumwa?" Ndande Ayahudi siavanichana ndi Asamaria. 10 Yesu wadayankha ngati ukadajiwa mphatso ya Mulungu, ndi yuja wakukambila ndi pache majhi, nkadamuphempha, ndiwadakuninkha majhi yopeleka umoyo. 11 Wamkazi wadayankha, "bambo mulije msomelo utungila majhi ndi chiteme ndi chonyowa, siuyapata kuti majhi ya umoyo. 12 Bwanji iwe ndi wamkhulu, kuposa atate wathu a Yakobo, iye wadatininkha chitime ichi?" 13 Yesu wadayankha, waliyenche uyo siwamwe majhi yaya siwaonancho tujho, 14 Nampho waliyenche uyosiwamwe majhi yayo sinimpache ine siwaonancho lujo. Pambuyo pake majhi yayo sindimpache siyakale ngati mchogololo umwaza majhi muyaya. 15 Yuja wamkazi wadamkambila, Ambuye, ndiyaona majhi yameneyo kuti ndisakale ndi lujo, ndi kuti ndisachanchika kuja pano kutunga majhi. 16 Yesu wadamkambila, "pita kamtane mmunako, ndi ujhe." 17 Wamkazi wadamkambila, "ndilije wa mmuna. Yesu wadayankha wamkamba bwino ulije wammuna. 18 Pakuti ulindi wa chimuna asano, ndi mmojhi ulinayo sazino osati mmunako. Yapa wakamba uzene." 19 Wamkazi wadamkambila, "abwana ndiona imwa ndi alosi. 20 Achatoto watu amapemphera pa phili ili, nampho anyaimwe mkamba Kuyerusalemu ndo malo wanthu afunika kupemphela." 21 Yesu wadayankha, "wamkazi ndi kulupalile, nthawi ifika iye simupempha Ambuye pa pili lino kapena Kuyerusalemu. 22 Anyaimwe wanthu mlambila icho simuchijiwa nampo ife tilambila icho tichijiwa, ndandeno mboli uchokela kwa Ayahudi." 23 Atachimwecho sije nyengo, ndi sazino ulipano nyengo anyiao alambila uzene salambile atate mumzimu ndi uzene ndande atate wauna una wanthu amtundu, umeneo kukala wanthu wake yao amlambila. 24 Mlungu ndi mzimu, ndi anyiwaja amlambila afunika kumlambila kimzimu ndi zene. 25 Wamkazi wadamkambila, "ndijiwa kuti wakuja Mpulumusi, (watanidwa Kristo). Iye yapo siwaje siwatikambile yonche." 26 Yesu wadamkambila, "ine ukamba nane nde iye." 27 Nyengo imweyo omphuzila wake adabwela nao adazizwa ndande chiyani wakambana ndi wamkazi, nampho palije uyo wadaesa kumafuncha, ufuna chiyani? Kapina, "ndande chiyani ukamba ndi uyu?" 28 Kwaicho wamkazi wadausiya mchukho wake ndi kupita kumzinda ndi kwakambila wanthu, 29 "majani mpenyo munthu wandikambila nkhani zanga zonche izo ndazichita, bwanji ikozekana kuti nde Kristo?" 30 Adachoka kumzinda ndi kuja kwaiye. 31 Nyengo ya usana omphuzila wake adamupempha ndi kukamba, Apuzisi idyani chakudya. 32 Nampho iye wadaakambila, ine ndili ndi chakudya icho simuchijiwa anyaimwe. 33 Omphuzila adakambilana, palije uyo wampacha chinthu chalichonche kudya, "bwanji adapeleka?" 34 Yesu wadakambila, chakudya changa ndi kuchita mafuno ya iye uyo wanditumiza ndi kwakanicha nchito yake. 35 Bwanji simkamba kuti ikali miezi isano ndi zokololedwa zisikale zakwana? Ndikukambilani penyani minda umoili yakwanila kukolola. 36 Uyo wakotola walandila mkokolo ndikusonkhanicha vipacho ndande ya umoyo wa muyaya, kuti uyo wavyala nayenche wakotola kuti akondwelele pamoji. 37 Pakuti mkambo uwu ndi zene, mmojhi wavyala ndi mnjake wakolola. 38 Ndidakutumani kukolola icho simdagwile nchito, wina achita nchito ndi anyaimwe mkati mwa chisangalalo cha nchito yao. 39 Asamaria ambili pa mzinda uja adamkulupalila chiukwa cha wamkazi yuja wamatilila umboni nkhani zake, wadanikambila vonche ivo ndidavichita. 40 Kwaicho Asamaria yapo adaja adamphempha kuti wakhale, nao ndi wadakala kwa anyaio masiku mawili. 41 Ndi ambili kupunda adamkulupalila chifukwacha mau lake. 42 Adamkambila yuja wamkazi, "tukulupalila osati kwa mau yakope, ndande tachinawene tavela, ndi chipano tijiwa kuti iyende mpulumusi wa jhiko." 43 Pambuyo pa masiku ya wili wadachoka kupita Kugalilaya. 44 Ndande iye mwene wake wadatolengeza kuti mlosi walije ulema kumuji wake mwene. 45 Yapowadaja kuchokela Kugalilaya, a Kugalilaya adamlandila, adaona vinthu vonche ivo wadavichita Kuyerusalemu kuchisangalalo. 46 Wadajancho ku Kana ya Galilaya, kumeneko wadang'anamuka majhi kukala vinyo. PAdali ndi wamkulu iye mwana wake wadali odwala Kukapernaumu. 47 Yapowadavela kuti Yesu wadachokela ku Yudea ndi kupita Kugalilaya, wadapita kwa Yesu ndikumupempha wachike wamuchirise mwana wake, uyo wadali paupi kumwalila. 48 Nde Yesu wadamkambila, anyaimwe mkasia osaone chizindikiro ndi vodabwicha simu ngate kukulupalila. 49 Nduma wadanena, Ambuye chikani panchi mwana wanga wakaliosamwalila. 50 Yesu wadamkambila mapita mwana wako wa moyo, yuja munthu wadakulupalila mau wadakamba Yesu ndi wadapita. 51 Yapo wamachikha, anchito wake adamulandila ndikumukambila mwana wako wadali wa moyo. 52 Kwaicho wadaauncha mwachira nyengo yanji? Adayankha, julo nyengo ya saa saba nthenda idamusia. 53 Nde atate wake adajiwa kuti ndi nyenbo imweija wadakamba Yesu. Mwana wako walama kwaicho iye ndi amnyumba mwake adakulupalila. 54 Ichi chidali chizindikilo cha kawili wadachita Yesu yapo wadachoka Kuyudea kupita Kugalilaya.