1 Basi kudali ndi Farisayo ambayo jina lake Nikodemu mmonchi wa otumidwa pakati pa bwalo la Wayahudi. 2 Munthu uyu, wadamchata mbuye Yesu usiku ndi kumkambila, "apuzisi, tujiwa kuti uli puzisi, kuchoka kwa Mulungu, pakuti palibe munthu wakhoza kuchita viwalilo ivi vonche Mulungu siwadakhala pamonchi naye." 3 Yesu wadanchibu, "uzene, uzene, munthu siwakhoza kulowa pakati pa ufumu wa Mulungu ngati siwabadwa mala ya kawili." 4 Nikodemo wadakamba, "munthu wakhoza kubadwa wali mdala? Siwakhoza kulowa mmimba mwa mama ake mala ya kawili ndi kubadwa, bwa wakhoza?" 5 Yesu wadanchibu, "uzene, uzene, munthu uyo siwabadwa kwa maji ndi mzimu, siwakhoza kulowa pakati pa ufumu wa Mulungu." 6 Icho chabadwa kwa nthupi ndi nthupi, ndi icho chabadwa kwa Mzimu ndi mzimu. 7 Usidashangaa ndande ndida kukambila, ndi lazima ubadwe mala ya kawili. 8 Mphepo ivuma palichocnhe yapoikonda ndi sauti yake muivela, nampho simuchiwa uko ichoka wala uke ipita. Ndeuma ili hali hali ya kila uyowabadwa ndi mzimu. 9 Ni kaddema wadanchibu, kokamba, "vinthu ivi vikhozekana bwanchi?" 10 Yesu wadanchibu, "iwe uli puzisi wa Israeli, ata siunchidwa vinthu ivi?" 11 Uzene, uzene, ndi kukambila chicha tuchinchiwa tuchiikila umboni kwa chicha tachiana.Nampho siwalandila umboni wanthu. 12 Ngati namkambila vinthu va yapa pa nchika ndi simukhulupalila, simkhoze bwanchi kukhulupalila ngati ndikokambilani vinthu va kumwamba? 13 Pakuti palibe uyowakwela pamwamba kuchoka kumwamba ila iye wanchika, mwana wa mwanadamu. 14 Ngati muncha Musa umowadanyakula nchaka papururu, mchimwecho mwana wa mwanadamu lazima wainulidwe, 15 ili kuti onche anyiwo siakhulupalile apate umoyo wa muyaya. 16 Pakuti kwa namna ii Mulungu wadalikonda jhiko, kuti wadamchocha mwana wa chisamba, ili kuti munthu waliyonche wamkhulupalila siwadangamia ila wakhale ndi umoyo wa muyaya. 17 Ndande Mulungu siwadamtume mwana wake panchika ili wahukumu nchika, ila kuti nchika lilamichidwe mkati mwa iye. 18 Uyowamkhulupalile iye siwahukumidwa. Uyo siwamkhulupalila tayari wanthohukumidwa ndandesiwadakulupalile nchina la mwana wachisamba wa Mulungu. 19 Iii ndo ndande ya hukumu, ya kuti dangalila lancha panchiko, nampho wanadamu udakonda mdima zaidi ya dangalila ndande vichito vao vidali vachimo. 20 Kila munthu wachita voipa waliipila dangalila ili vichito vake sividancha kuikidwa wazi. 21 Nampho, iye wachita bwino wakuncha kudangalila ili vichito vake vionekane kuti wachitika kwa kumvechela Mulungu. 22 Baada ya yamena, Yesu pamonchi ndi opuzila adapita pakati pa nchika la Yudea, kumeneko wadatumi muda pamonchi nao wamata batiza. 23 Chipano Yohana nayo watabatiza kumeneko ku Ainea kalibu ndi Salim pakuti kudali ndi manchi ya mbili pancha, wanthu amancha kwake ndi kubatiza, 24 Pakuti Yohana wadakali asapenyedwe kujela. 25 Ndeyapo padachokela mabishano pakati pa opuzila Yohana ndi Wayahudi kuhusu sikukuu ya kuchukidwa. 26 Adapita kwa Yohana kumkambila, "puzisi, iye udali nayo nchidya la mnchinche Yorodani, iye wadashuhudia mau yake, penya wabatiz ndi onche apita amnchata." 27 Yohana wadanchibu munthu siwakhoza kulandila chinthu chalichonche ingakhale ngati waninkhidwa kuchoka kumwamba. 28 Anyiimwa mwachinawene mushuhudia kuti ndi dakamba kuti, "ine osati Kristo, badala yake ndidakamba, ndatumidwa pachogolo pake." 29 Iye wali ndi bibi arusi ndi mbuye arusi chipano bwenchi wa mbuye arusi, waima ndi kuvechela chimwemwe sana ndande ya sauti ya mbuye arusi chipano ndi chimwemwe changa chakamilika. 30 Wafunikana kuzidi, nane nifunikana kupungua. 31 Iye wachoka pamwamba, wali pamwamba pa yonche. Iye wali wa panchiko wachaka panchiko ndi wakamba vinthu va panchiko. Iye wachoka kumwamba wili pamwamba pa yenche. 32 Iye washuhudia yancha wayaona ndi kuyavela, nampho palibe walandila ushuhuda wake. 33 Iye walandila ushuhuda wako wahakisha kuti Mulungu ndi mzene. 34 Ndande iye watumidwa ndi Mulungu wakamba mau ya Mulungu pakuti siwaninkha mzimu kwa chipimo. 35 Tate wamkonda Mwana ndi walinao umoyo wa muyaya, nampho kwaiye siwamvela mwana pamwamba pake. 36 Iye wamkulupalila Mwana walinao umoyo wa muyaya, nampho kwaiye iwamvela mwana siwauona umoyo, ila asila ya Mulungu igwilizana pa mwamba pake.