Sura ya 20

1 Chisanga siku loyamba la juma, kukali kuli mdima. Mariamu Magdalena wadaja kukaburi, wadauona uja mwala wachochedwa pakaburi. 2 Kwa icho wadatamanga liwilo kupita kwa Simoni Petro ni kwa yuja opuzila mwina ambae Mpulumusi wadamkonda, badae wakamkambila, "amtenga Ambuye pakaburi, nae sitijiwa uko amng'oneka." 3 Nampho Petro ni yujha opuzila mwina adachoka, kupita kukaburi. 4 Onche adatamanga liwilo kwa pamoji, yuja opuzila mwina wadatamanga kwa chisanga kumshinda Petro nikufika kukaburi oyambila. 5 Wadaima ni pambuyo kuzuzumila pakaburi, wadaione ija nchalu yoela yagone, nampho wadalowe mkati. 6 NAmpho Simoni Petro nae wadaika ni kulowa mkati mwa kaburi wadaiona ija nchalu yoela yagona paja 7 nichija chitambaa chidali kumutu wake siidagone pamoji ni zija nchalu zoela (sanda) bali idali yagona pamphepete payoka. 8 Ndipo yuja mwina nae wadalowa mkati mwa kaburi, wadapenya ni kukulupalila. 9 Pakuti hadi nthawi imeneyo akali adayajiwe malembo kuti idaunika Mpulumusi wahyuke ncho kwa akufa. 10 Pambuyo opuzila adapitancho kunyumba yao. 11 Ata nchimwecho, Mariamu wadali wa wakali waima pakaburi walila, yapo wadali wakali kuendekela wadaima pambuyo wadapenya mkaburi. 12 Wadaona angelo awili ali ni nkhope yoela akala mmoji kumutu ni mwina kumyendo pamalo yapo Mpulumusi wadali wagone. 13 Nao adamkambila, "wamkazi, ndande chiani ulila?" Nae wadamkambila, "ni ndande amtenga Ambuye wanga, nane sinijiwa uko amuika." 14 Yapo wadatokamba yameneyo, wadang'anamuka ni kumuona Mpulumusi wangoina. Nampho wadamjiwe kuti ngati iye wadali Mpulumusi. 15 Naye Mpulumusi wadamkambila, "mama, ndande chiani mlila? Mumfunafuna yani?" Nao uku akaganiza kuti ni openyelela bustani adamkambila, "Ambuye, ngati ni imwe mwamtenga, nikambileni uko mwamuika, nane nikamtenga." 16 Mpulumusi wadakambila, "Mariamu" naye wadang'anamuka mwene nikwakambila kwa Kiaramu, "Raboni," ili ni kukamba, "Opuzila." 17 Mpulumusi wadamkambila, "siudanigusa, pakuti nikali osakwele kupita kwa atate, bali upite kwa achabale wanga ukakambile kuti nikwele kupita kwa atata wangu ambao anyiimwe atata wanu. Mulungu wanga ni Mulungu wanu." 18 Mariamu Magdalena wadaja kwakambila opuzila, "niona Ambuye," nikuti amkambila mambo yaya. 19 Ni yapo idali ujulo, siku limenelo, siku loyamba la juma, vicheko vamangidwa pamalo opuzila yapo adali kwa kwaopa Wayahudi, Mpulumusi wadaja ni kuima pakati pakati pao nikwakambila, "mtendele ukale kwa anyiimwe." 20 Yapo wadatokamba yameneyo wadalangiza manja yake ni nthili yake. Nao opuzila yapo adamuona Ambuye adasekelela. 21 Pambuyo Mpulumusi wadakambilancho, "mtendele ukale ni anyiimwe, ngati muja baba adanituma ine, chimwecho ine nane nikutumani anyiimwe." 22 Mpulumusi yapo wadatokamba yameneyo, wadachelela wadakambila, "landilani Mzimu oyela. 23 Waliyonche umlekelele chino, alekeleledwa, ni anyiwaja mwamangila amangilidwa." 24 Tomaso, mmoji wa anyiwaja kumi ni awili, watanidwa, Dismasi, siwadali ni opuzila achanjake yapo wadaja. 25 Anyiwaja opuzila wina adamkambila pambuyo, "taona Ambuye." Nae wadakambila, "ngati siniona alama za misumari katika manja yake, ni kuika vyala vanga kuzimenezo alama, ni pia kuika janja lanja kunthiti yake sinikulupalila." 26 Baada ya siku nane opuzila adali kuchumbancho, nae Thomaso wadali pamoji nao. Nthawi vicheko yapo vidali vachekedwa Mpulumusi wadaima pakatikati pao, ni wadakamba, "mtendele ukale namwe." 27 Pambuyo wadamkambila Thomaso, janancho chala chako ni upenye manja yanga, janayo pano manja yako ni uike mthili mwanga, wala siudakala osakulupalile, ila okulupalila. 28 Naye Thomaso wadayankha ni kumkambila, "Ambuye wanga ni Mulungu wanga." 29 Mpulumusi wadamkambila, pakuti waniona wakulupalila, adaasidwa anyiyao akulupalila popande kupenya. 30 Pambuyo Mpulumusi wadaita langizo lalikulu pamaso pa opuzila, izo zidawahi kulembedwa katika chikala kala ichi. 31 Nampho izi zalembedwa dala kuti mkoze kukulupalila kuti Mpulumusi. Mwana wa Mulungu, nikuti pokulupalilapo mkate ni umoyo kwa jina lake.