Sura ya 19

1 Panja Pilato wadamtenga Yesu ni kumtyapa. 2 Anyiwajha waaskari adavilinga minga ndikukonja taji, adaiika pamwamba pamunthu ya Yesu nikumvalicha chalu za rangi ya zambalau. 3 Adamchata ndikukamba, "iwe mfalme wa Yahudi!" nikumbula ni manja yao. 4 Panja Pilato wadanjoka kubwalo, ndi kuwakambila wanthu, "penyani nipelekelani uyu munthu kwanu ili mnjhiwe kunti ine sidaiyone hatiya yaliyonche mkati mwake." 5 Kwachimwecho Yesu wadachoka kubwalo, wadavala chisoti cha minga ndi chalu za zambalau. Ndi panja Pilato wadakambila, "penyani munthu uyu yapa!" 6 Kwachimwecho nyengo kuhani wamkulu ndiwakulu akulu yapo wadamuona Yesu, adapiga kelele adakamba, "msulubisheni, msulubisheni" Pilato adawakambila, "mtengeni anyiimwe mwanjinawene mkamsulubishe, pakuti ine sini iyona ndande mkati mwake." 7 Wayahudi adamyankha Pilato, "ife tulinayo sheria ndi kwesheria imeneyo ifunika kufa kwandande iye wadanjitita kunti mwana wa Mulungu." 8 Pilato panja wadavela mau yaya wadazidi kuusopa. 9 Wadalowa Praitorio ndikumkambila Yesu, iwe uchoka kuti? Atamchimwecho Yesu swadayange. 10 Lakini Pilato, bwa iwe siukamba ndi ine? Bwa iwe siunchiwa kuti ine nili ni mamulaka ya kukuchakulila ni kukusulubisha? 11 Yesu wadayankha, "sudakakala ndi mphavu zidi yanga ngati sudakapachidwa kuchoka kumwamba. KWachimwecho, munthu wanichoncha kwako wali ni zambi yaiukulu." 12 Kuchokana yanko ili, Pilato wadafuna kumsia huru, nampho Wayahudi wadapinga kelele wadakamba, "ngati sumsie huru basi iwe osati mbwenji wa Kaisari; Kila wnjitita kuti mfalme kukamba mmbuyo Kaisari." 13 Pilato yapo yadavela mau yaya, wadampeleka Yesu kubwalo kumkalicha pampando wa hukumu pamalo paja pajulikana ngati masakafu, nampho kwa Kiebrania, Gabatha. 14 Siku ya maandilizi ya Pasaka yapoudafika ndiyani ya saa sita Pilato wadakambila Wayahudi, penyani Mflume wanu uyu yapa. 15 Adapiga makelele, mchocheni mchocheni, msulubisheni, Pilato wadakambila, "ndi msulibishe mfalme wanu?" Nayo kuhani wamkulu wadayankha "ife tilibe mfalme ingakale Kaisari." 16 Ndeyapo Pilato wadamchocha Yesu kwao ili watesedwe. 17 Nao adamtenga Yesu. NAe wadachoka hali wautenga msalaba wake mwene mpaka kueneo lidanidwa fuvu la mutu, ndi Kihebrania litanidwa Golgotha. 18 Ndiyapo adamsulubisha Yesu pamojhi nae wachimuna awili, mmojhi upande uu ndimwina upande wina, ndi Yesu pakatikati. 19 Potela Pilato wadalemba alama ndikuiika pamwamba pa msaba pamenepo padalembedwa; YESU MNARETH, MFALME WA WAYAHUDI. 20 Ambili wa Wayahudi adaisoma alama ija kwani pamalo paja adamsulubisha Yesu padali pafupi ndi muji. Alama ija idalembedwa kwa Kiebrania kwa Kirumi ndi kwa Kiyunani. 21 Potela wakulu wa makuhani wa Mayahudi adamkambila Pilato, "si udalemba, Mfalme wa Wayahudi, mpha iye wadakamba ine ndi mfalme wa Wayahudi." 22 Nae Pilato wadayankha, "yayonayalemba na yalemba." 23 Pambuyo askari kumsulibisha Yesu, adatenga vivalo vake ndi kuyagawa mafungu, yanai, kila askari fungu limoji,kwa chimwecho ndi kanzu, chipano lija kanzu, silidali losokedwa nampho lidali lofumidwa lonche kuchola kumwamba. 24 Potela adakambichana achinawene kwa achinawene, "sitidaling'amba ila tilitimbile kura ili tione siikale ya yani." Ilimenelo lidachoke lija lembo litimie ilo lakambidwa adagawana nchalu zanga ndi "valo langa adalipigira kura." 25 Waaskari wadatenda mama yaya. Mama wake Yesu ndi Mariamu mke wa Kleopa ndi Mariamu Magdalena. 26 Yesu yapowadamuona mama wake pamoji ndi yujha opuzila uyowadamkonda adaima pafupi wadamkambila mama wake wamkazi kapena taona, mwana wako uyu yapa. 27 Potela wadamkambila "yuja opuzila penya uyoyapa mama wako." Chokela chipano uyo yuja opuzila wadamtenga kupita kukomo kwake. 28 Pambuyo pa ili. Hali Yesu adajiwa kutiyonche yatokala kuta ili kuyatimiza malembo wadakamba, "niona lujo." 29 Chombo icho chida likujala siki chidali chaikidwa paja kwachimwecho adiika sifongo iyo idajala siki pamwamba pa ufito wa hisopo adamwikila mkamwa mwake. 30 Nae Yesu yapowadailawa imeneyo, Wadakamba, "yotela potela wadakulamicha mutu wake, wadaikabidhi roho yake." 31 Kwa pakuti idali ndi nyengo ya maandalio ndi kwa ajili matupi siyadafunike kukala pamwamba pa msalaba nyengo ya sabato, pakuti sabato idali nthawi ya bwino, Wayahudi adamphempha Pilato kuti myendo yao waja yaowadali asulubishidwa ityake, ndikuti matupi yao ichichidwe. 32 Ndipo asikari yapoadaja ndikutyola myendo ya munthu oyamba ndi akawili uyowadali amsulubisha palimoji ndi Yesu. 33 Yapo adampeza Yesu, adampeza tayali wadali watokufa kwa chimwecho siadamtyole myendo yake. 34 Ata chimwecho, mmoji wa askari adam'bucha Yesu mntiti kwa mkuti, ndi mara yadachoka maji ndi mwazi. 35 Nae wadapenya wachocha ushuhuda, ndi ushuhuda wake, ndi wauzene iyo wajiwa kuti ichowachikamba ndi cha uzene ili namwe mvanenavo. 36 Vinthu ivi ili likwanile lijalakambidwa lipate kukwanila, "palibe ata wake mmoji uosiotyole." 37 Tena lembo lina likamba, "siampenyele iye uyoamtosa." 38 Pambuyo pa vinthu ivi Yusufu wa Arithamaya kwachimwecho wadali opuzila wa Yesu. Nampho kwa kwa siri ya kuwaopa Wayahudi, adamphempha Pilato kuti walitenge tupi la Yesu. Nayo Pilato wadampacha ramulo. Kwa chimwecho Yusufu wadaja kuchocha tupi la Yesu. 39 Nayo Nikodemo ambapo pamenepo poyamba wadamchata Yesu usiku nayo wadaja, iyo wadampeleka mchanganyiko wa manemane ndi udi, yapate kulemela ratili mia moja. 40 Kwachimwecho adalitenga tupi la Yesu adauvilinga msanda ya kitani ndi pamoji ndi yaja malashi ngati umoidali kawaida ya Wayahudi nyengo yakuzika. 41 Pamalo wadani Yesu adamsulibisha padali ndi bustani, mkati ya ija bustani mdali ndi kabuli la mpya ambalo padalibe muntu wadawahi kumzika mmenemo. 42 Basi pakuti idali siku ya maandalio kwa Yahudi ndikwa chija likabuli lidali karibu, basi adamgoneka Yesu mkati mwake.