1 Ine ndine mvinyo wauzene ndi atata wanga alimi a mvinyo. 2 Ntawi iliyonche mkati mwaine wamenelo silibala chipacho ndi kuliyelecha mtundu wa ntawi lime libala vipacho ndi kulichocha dala kuti likoze kubala kupunda. 3 Anyiimwe mwakala bwino chifukwa cha utenga umene nidatokukambilani. 4 Mkale mkati mwanga nanencho ndikale mkati mwanu ngati ntawi imene sitikoza kubala loka ngati losakala pa mvinyo chi majimoji anyiimwe ngati simkala mkati mwanga. 5 Ine mvinyo anyiimwe ni ntawi, walimbikicha mkati mwanga nanencho ndili mkati mwake muntu mmeneyo wabara vipacho vambili pakati popande ine sipanga chitidwe chinthu chilichonche. 6 Ikakala muntu waliyenche siwakala mkati mwanga siwatanidwe ngati ntawi ndi kuuma, wanthu alombekane ntawi zonche kutaya pamalo ndi kutelatu. 7 Ngati simkale chikalileje mkati mwaine ndi ngati mau yanga siyakale chikalileje mkati mwanu pemphani chilichoche simdiiune namwencho sinichitidwile. 8 Paili tata wanga walemekezedwa kuti mbala vipacho vambili ndi kuti oyaluzidwe wanga. 9 Ngati simuyagwile malambo yanga simkale pa chikondi changa ngati umo ndidagwirila malamulo ya atata wanga ndi kukala pakati pa chikondi chake. 10 Ngati simuyagwile malambo yanga, simkale pa chikondi changa ngati umo ndidagwirila malamulo ya atata wanga ndi kukala pakati pa chikondi chake. 11 Nde kamba nkani izi kwa anyaimwe dala kuti chisangalalo changa chikale mkati mwanu ndidela kuti chisangalalo chano chichitika pauzene. 12 Ili nde lamulo langa kuti mjikondeni mwachinawene kwa mwachinawene ngati ine umo nde kukudelani. 13 Palije muntu wali ndi chikondi chachikulu kupunda ichi kuti wachoche kulama kwake chiuko cha mabwenji lake. 14 Anyaimwe mabwenjo langa ngati simchite yamene ndi kukambilani. 15 Sindikutanani akaporo pakuti kaporo siwachijiwa icho wachichita wamkuru wake nakutanani anyaimwe mabwenji chifukwa chakujiwichani nkhani zonche ndezivela kuchokela kwa atate. 16 Simdeni sankule ine ikapanda ine na kusankhulani anyiimwe ndi kukuikani kuti m'bale vipacho ndi chipacho chano nikoze kukala. Ichi chilichimwe dala kuti chilichonche mpempha kwa atate kupitila mjina laine siakupacheni. 17 Nkani izo ndi kupachani kuti mjikondana aliyenche ndi mujake. 18 Ngati jiko silikuipileni mjiwe kuti mdandiipila ine pambuyo simdaipidwe anyiimwe. 19 Ngati mkadakala ajiko jiko likadakukondani ngati akumo nampho pakuti anyiimwe osati ajiko ndi chiuko ndidakusankhulani kuchokela mjiko nde chifukwa jiko likuipilani. 20 Kumbukilani mau ndidakukambilani kaporoi osati wamkuru kupunda wamkuru wake ngati adandivuticha ine ndi anyaimwe simvutichdwe ngati adagwira mau langa akadaligwila kwa anyaimwe. 21 Siakuchitileni nkanizi zonche chifuko cha jina langa chifuko samjiwa mmene wandituma. 22 Ngati sindideka bwela ndikukambilani siakadachita machimo nampho chapano alibe chokamba chifuko cha machimo yao. 23 Wandipita ine wanipita tata wanga. 24 Ngati sindichita nchito mkati mwao ikakala imene palije mmoji waichita akada kala alibe chimo nampo chapano achita yonche yawili aona ndi andipila ine ndi atate wanga. 25 Ichi chachokela kuti mau ligwirizila limene lalembedwa pa lamulo lao: "andiipila ine palije ndande" 26 Ntawi mtondoza wafike mmene sindimtume kwanu kuchokela kwa atata wanga uyu ndiye mtima wa zene mmene wachokela. 27 Anyaimwe namwencho mundu jililila chifuko mdali nane chiyambile mmayambo.