1 Siku sita kabla ya Pasaka, Yesu wadapita Bethania,uko wadali Lazaro, iye uyo wadamuhyusha kuchoka pakati pa akufa. 2 Basi adamwandalia chakudya cha unchula kumeneko, ndi Martha wadamtumikila, nyengo imeneyoLazaro wadali mmonchi wa anyiwancha adakhala pa kudya pamonchi ndi Yesu. 3 Ndeyapo Mariamu wadatenga latli ya manukato yayoyadakonchedwa kwa nardo yabwino, ya ntengo waukulu, wadampaka Yesu mmyendo, ndi kumpangusa mmyendo kwa chichi lake, nyumba yanchi idanchala mnunkha wa manukato. 4 Yuda Iskariote, mmonchi wa anyiwancha opuzila wake ambaye ndeuyo siwamuukile Yesu, wadakamba, 5 "ndande chiyani manukato yaya sidakagulinchidwa kwa dinari miazi tatundi kwaninkha asauko?" 6 Nayo wadakamba yameneyo, osati kwa kuwaonela lisungu osauka, ila ndande wadali mnkhungu; iye nde uyo wadagwila nthumba la hela ndi wadatenga baadhi ya ivovidaikidwa mmenemo ndande yake mwene. 7 Yesu wadakamba, "msiye waike icho walinacho ndande ya siku ya kuzikidwa kwanga. 8 Osauka simkhale nao siku zonche; nampho simnkhala ndi ine siku zonche." 9 Basi gulu lalikulu la Wayahudiadapata kunchiwa kuti Yesu wali kumeneko, naoncho adancha, osati ndande ya Yesu pe, ila amwone ndi Lazaro uyu Yesu wasamhyusha kuchoka pakati pa akufa. 10 Naoncho wakulu anchembe adachita maganizo ili amuimphe Lazaro; 11 pakuti ndande yake ambili pakuti pa Wayahudi adapita ndi adamkhulupalila Yesu. 12 Ndi siku ya kawili yake gulu la likulu lidancha pa sikukuu yapo adavela kuti Yesu wakuncha ku Yerusalemu, 13 adatenga nthawi za mitengo ya mitende ndi kuchoka kubwalo kupita kumlandila ndi kubula mapokoso, "Hosana! iye wakuncha kwa nchina la Ambuye, Mfumu wa Israeli." 14 Yesu wadampata mwana wa punda wadakwela, ngati ndimuncha umoidalembedwa. 15 "Usidaopa, mwali wa Sayuni, penya, mumu wako watokuncha, wakwela mwano wa punda." 16 Opuzila wake siadaelewe vinthu vimenevo pamenepo huti; nampho Yesu yapodatukuzidwa, ndeyapo adakumbuka kuti vinthu ivi wadalembeledwa iye ndi kuti achita vinthu ivi kwake. 17 Basi lincha gulu la wanthu anyiyawa adalipo pamonchi ndi Yesu nyengo yapo wadamtana Lazaro kuchoka kumakaburi, adashuhudia kwa wina. 18 Ndi idali ndande imeneyoncho kuti gulu la wanthu adapita kumlandila ndande adavela kuti wadachita ishara imeneyo. 19 Mafarisayo adakmbichana anyiiwo kwa anyiiwo, "penya saino simkhoza kuchita chalichonche, penya, nchiko lapita kwake." 20 Chipano baadhi ya Wayunani mkali mwa anyiwancha amapita kuabudu pa sikukuu. 21 Anyiyawa adamchata Filipo, ambaye wadachaka Bethsaida ya Galilaya, adamphempha adakamba, "Ambuye, ife tukhumbila kumwona Yesu." 22 Filipo wadapita wadamkambila Andrea; Andrea ndi Filipo adapita ndi kumkambila Yesu. 23 Yesu wadaanchibu wadakamba, "saa yafike ndande ya mwana wa Adamu kutukuzidwa. 24 Uzene, Uzene, ndikukambilani, chembe ya ngano ngatisiigwa pakati pa nchika ndi kua, inkhala hali imweyo yakhope, ila ikafa, siibale matunda ya mbili." 25 Iye wakonda umoyo wakesiwautaize, ila iye wauipila umoyo wake pakati pa nchiko ili siwaulamiche hata umoyo wa muyaya. 26 Munthu waliyenche wakanitumikila ine, ndi waninchite; nane yapo ndilipo, ndiyapo ndi mtumiki wanga ndiyapo siwakhalepo. Munthu waliyenche wakanitumikila, tate siwamlemekeze. 27 Chipano mzimu wanga waipidwa; nane nikambe bwanchi? Atate, anilaminche pakati saino? Nampho kwa ndande ii naiikila saino. 28 Atate, mulitukuze jina lanu, ndeyapo sauti idaja kuchoka kumwamba ndi kukamba, ndalitukuza nane si ndilitukuzencho. 29 Basi gulu lidaima pafupi naye adavela adakamba kuti kuli mtungulu, wina adakamba, "angelo wakamba naye." 30 Yesu wadajibu ndi kukamba, "sauti ii siidaje ndande ya ine, ila ndande yanu. 31 Chipano hukumu ya nchiko ili ilipo; chipano wamkulu wa nchika ili siwatanidwe kubwalo. 32 Nane ndikainulidwa pamwamba pa nchiko, si ndiaguze onche kwanga." 33 Wadayakamba yameneyo ndiwalangizakuti kwa ndisi wa ife. 34 Gulu lidajibu, "ie tavela pakati pa lamulo kuti Kristo siwadumu paka muyaya. Nawe ukamba bwanchi mwana wa Adamu lazima wainulidwe pamwamba? Uyu mwana wa munthu ndi yani?" 35 Basi Yesu wadaakambila, "dangalila likali pamonchi ndi anyiimwe muda kidogo. Mapitani pakuti mlinalo dangalila, ili kuti mdima usidanchakukukhozani iye wapita kumdima siwajiwa uko wapita. 36 Mkhakala mkali ndi dangalila likhulupaliloni limenelo ili mpate kukhala wana adangalila." Yesu wadayakamba yameneyo ndi wadapita zake wadajibisa asidamwona. 37 Ingakhale Yesu wadachita ishara zambili mtundu umeneo pachogolo pao, nampho siadakhulupalile 38 ili likamichidwe mau la Isaya olosa , ila wadakamba, "Ambuye ndi yani wadavomela mau yanthu? Ndi chancha la Ambuye wamasulidwa yani?" 39 Ndo chifukwa cha anyiiwo siadakhulupalile, pakuti Isaya wadakamba ncho, 40 "wachita siaponya maso, ndi waichita yolimba mitima yao; asadancha kupenya kwa maso yao ndi kunchiwa kwa mitima yao, ndi kung'anamuka ndi ine kuwalamicha." 41 Isaya wadakamba mau yameneyo pakuti wadaona uulu wa Yesu ndi wadakamba mau yake. 42 Nampho, ata wakulu akulu ambili adamkhulupalila Yesu; nampho ndande ya Maarisayo, siwadavechele ili asidancha kubagulidwa ndi kanisa. 43 Adakonda sifa za wanadamu kuliko sifa zichoka kwa Mulungu. 44 Yesu wadapaza sauti ndi kukamba, "iye wanikhulupaliloa ine, siwanikhulupalila ine pe, ila ndi iye uyowanituma ine, 45 ndi uyo waniona ine wamuona ndi uyo wanituma." 46 Ine nancho ngati dangalila la panchiko ili kila munthu wanikhulupalila ine siwadakhala kumdima. 47 Ikakhala munthu waliyonche siwayavenchele mau yanga nampho siwayagwila, ine sindimuhukumu pakuti sindidancho ili ndihukumu nchiko, ila nilaminche nchiko. 48 Iye wanikana ine ndi uyosiwavomela mau yanga, walinayo wa kumuhukumu; mau ili ilo nakamba nde ilo silimuhukumu siku ya nthela. 49 Pakuti ine sindidakambe kwa mtima wangape, ila ndi atate yawo anipeleka, iwo wene anigwiliza yayosindikambe. 50 Nane ndinchiwa kuti gwiliza lake ndi la umoyo wa muyaya, basi yameneyo ndikamba ine ngati atate umoadanikambila, ndeumo ndikambila kwanu."