Mpambo 3

1 Ikhakhalanjha Mulungu akuuchani pamoji ndi Kristo, vifuneni vinthu va kumwamba uko Kristo wakhala janja la kuchimuna la Mulungu. 2 Ganizila kupitila vinthu va kumwamba, osati kupitila vinthu va mjikho. 3 Pakuti mwafa, ndi umaya wanu wabisidwa pamoji ndi Kristo kupitila Mulungu. 4 Nyengo Kristo yapo swadanechane, iye nda umoya wanu, chipano ndi anyiimwencho simwonekane nayo kupitila ulemelela. 5 Chipano musie vinthu vilipo kupitila jhiko yaani, chiwelewele, uchafu hamu ya ipa, kuganizila ka ipa, ndi khumbilo, ambavo ndi ibada ya mzimu. 6 Ndi kwa chifuko cha vinthu ivi phwai, ya mulungu ikuja pa mwamba pa wana anyiawo selemekeza. 7 Ndi kwa chifuko cha vinthu ivi anyiimwe namwe mdaenda nayo yapo mmaishi pakati pao. 8 Chipano saina lazima mvichoche vinthu ivi voche yaani mbhumu, kuipidwa, maganizo ya ipa, matukano, ni mau ya chafu yachaka mka mwa mwanu. 9 Simdanyengana mwachinawene kwa mwachinawene, pakuti mwavala ulemu wa kalendi vichito vaka. 10 Mwavala ulemu wa sopano kupitila njeru kuchakana ndi mfano wa yuja wadamuumba. 11 Pitila njiru ii, palibe Myunani wa Myahudi, kutainidwa wala kutokutainidwa, asoma sasame kapolo, osati kapela, nampha badala yake Kristo nde vinthu vonche kupitila yonche. 12 Ngati achagulidwa a Mulungu Oyela akandedwa valani ulemu wa bwina, valani ulemu wa bwina, valani ulemelela wa bwina, ukarimu, kulemekeza, upole ndi kuvumilia. 13 Tengelelani anyiimwe kwa anyiimwe. Lengelelanani lisungu kila munthu ndi njake ngati munthu walalamika zidi ya njake, wamlekelele kwa jinsi lija iya ambuye adakulekelelani inyiimwe. 14 Zaidi ya vichito vimenevo vanche, mukhale ndi chikondi ambacho nde chimenecha cha chimikizila kupunda. 15 Mtindele wa Kristo uwachongoze mmitima yanu idalindi kwa ndande ya mtendele iyi ndi kuti mda tilidwa kupitila thupi limoji mkhale ndi kuyamika. 16 Mau la Kristo likhale mkati mwanu kwa ulemelela kwa ulemu wanche, yaluzanan ndi kukambana anyiimwe kwa anyiimwe kwa zaburi, ndi nyimbo, kuimba kwa mmitima mwanu kwa Mulungu. 17 Ndi chali chonche mchitacho, kupitila mau au kupitila vichito, chitani yonche kupitila jina la Ambuye Yesu mpachoni kuyamika Mulungu atate kupitila iye. 18 Wachikazi, alemekezeni acha munanu, ngati umo ikwadilichila kupitila ambaye. 19 Namwencho wachimuna, akandeni acha kazanu simdakhala wakalipa zidi yaa. 20 Wana, alemekezeni akubali wanu kupitila vichinthi vanche, ndande ndande nda umai kwadilichile ambuye 21 Anyatate simma yamba wana wanu, ili kuti sadaja kudul nkhumbilo. 22 Makapolo, alemekezeni achambuye wana kupitila mnthupi kwa vichito vanche asati kwa huduma ya masa ngati wanthu. Okondwelecha pe, ila kwa mtima wa uzene. Muoponi Mulungu. 23 Chalichonche mchitacho, chitani kuchaka mmitima mwanu ngati kwa ambuye ndi asato ngati kwa wanthu. 24 Mujiwa kuti simlandile mphata ya chindhu kucheka kwa Ambuye ndi Ambuye Kristo uyo mutumikila. 25 Ndande waliyonche uyowachita yayo asati haki siwalandile lamula kwa vichintha ivo asati haki yayo wayachita, ndi palibe kupendelea.