1 Pakuti nifuna njiwe kuti umo nili ndi tabu ya kulu chifuko chanu, kwa mwaonchhe muli Kulaodikia ni kwa onchhe anyimwe mudapeye nkhope yanga ya tupi. 2 Nichita nchito mitima yao ikoze kukulupililidwa kopelekedwa pamoji ndi chikondi ndi ufulu wonche wa vambili vazene vakwamila va njelu ndi kujiwe chisisi cha zene cha ambuye mpulumusi Kristo. 3 Kuti nkhani zonchhe za njelu ndi kujiwa zabisidwa. 4 Nkamba chimwechi kuti munthu waliyonche wasaja kukuitilani voipa kulalika va namiza. 5 Pamoji kuti sindili pamoji ndi anyiimwe kitupi, nampho ndili nanyiimwe kimzimu. Nikodwa kupenya ukalo wanu wa bwino ndi nkongono ya chikulupi chanu kw mpulumusi. 6 Ngati umo mwamladilila mpulumusi ambuye endani ndi iye. 7 Mpachidwe machili ndi iye, muuzidwe ndi iye mpachidwe machli kwa chikulupi ngati umo mwayaluzidwa, ndi kumangidwa kwa yamiko la mbili. 8 Penyani kuti munthu waliyonchhe wasakukodwechani kwa kuchenjela ndi mau yachabe ya unami kutengela ndi malandilidwe ya wanthu kutengela malamulo ya jhiko, asati kulingano ndi mpulumusi. 9 Pakuti katika iye msiizilo wonchhe wa Mulungu ukala kalika tupi. 10 Anyiimwe mwajazidwa ndi uje. Iye ndi mutu wa icho chikozekana ndi malamulo. 11 Kwa iye tidaswedwa utonga uo siuchilika ndi wanthu katika kuchochedwa tupi la nyamo, nampho ndi utonga wa mpulumusi. 12 Mdazikidwa pamoji ndi iye katika ubatizi ndi kwa njila ya chikulupi katika iye mdahyushidwa kwa nkhongono za Mulungu, uyo wa hyushindwa kuchoka kwa akufa. 13 Yapo mmdali mwafa kwa kulakwa kwanu ndi kutokuswedwa utonga kwa matupi yanu, adakuchitami amoyo pamoji ndi iye ndi kutulekelela volakwa vatu vonche. 14 Adatima kuikumbukilanngawa idalembedwa ndi malamulo yali kumbuyo ndi ife. 15 Wadazichoche mkhongono ndi malamulo wadayaita pa danga ndi kuyachita yakale chisangalalo chokoza kwa njila ya mtanda waiye. 16 Kwa icho munthu waliyonche siwadakulamulani anyiimwe katika kudya ndi katika kumwa, ame kukala siku ya sikukuu ama mwezi wa chapano ame siku za sabata. 17 Ivi ni vituncha va ivo vikuja, nampho mtimani mpulumusi. 18 Munthu waliyoncheyo wasidanyengedwa ufulu wake kokumbila kujichicha ndi kolambila angelo. Munthu wa mtundu umeneo walowa kumkhani yayowayaone ndi kunamizidwa ndi maganizo yake ya kitupi. 19 Iye siwaugwililila mutu, ndi kuchoka katika mutu kuti tupi lonche kupitila viwalo vake ndi vifupa kulunjidwa ndi kuikidwa kwa pamoji ndi kukula kwa ukulaji uchochedwa ndi Mulungu. 20 Ikakala mdafe pamoji ndi mpulumusi kwa vichito va jiko Nampho mlama ngati mchita nchhito pa jiko. 21 Msidagwila wala kulakwa wala kugusa. 22 Yaya yonchhe yalamulidwa kwa ndande ya kuwananga kukuja ndi kutumikila. 23 Malamulo yaya yali ndinjelu za wanthu za konjedwa kwa kujipenya iwe kwa kujichicha kwa mazunjo ya tupi. Nampho zilije ulemelelo pakali pamakumbilidwe.