Mpambo 4

1 Anyambuye, chochani amangidwa vindu vili vazene ndi yauzene. Mujiwa mujiwa pakuti mulinao ambuye kumwamba. 2 Endekelani kukala okulupililika pakati pama pembelo, kalani maso pa ili koyamika. 3 Pembani pamoji ndinjila yatu iyi ilikuti Mulungu amasulidwe koma pandande ya mau, kukamba chimsisi cha uzene cha Kristo. Pandande ya ili namangidwa minyororo. 4 Ndikupembani kuti mukoza kuliika muzene ngati umo vanibidi kukamba. 5 Pitani paulemupawaja aokoledwa pabwalo, ndi muokowe ndawi. 6 Mau yanu yakala ndimayamiko ndawi zose, ndi yakome mchele pandawi yoje kuti mkoze kujiwa kuti umoyo afunikila mayakgo kila mundu. 7 Panjito inikuza ine, Tikiko siwachite yofwikana pa iye ndim'bale okondedwa, otumidwa akululupililika, ndiotumidwa mnjatu pakati pa ambuye. 8 Ndamtuma kwanu pandande iyi, yakuti mkozi wajiwa vindu vikuzana nafe ndi kuti ukoza kwatila mzimu. 9 Ndimtuma pamoji ndi Onesimo, m'bale watu akondedwa okululupilila, ndi mmoji wanu sakukambileni kilachindu chidachitika yapa. 10 Aristarko, amangidwa mnjatu, wakulonjelani, ndi Marko binamu wake ndi Barnaba mudayalandila kopola kuchoka pake, "ngati siwanje kwanu mlandileni," 11 ndi pakuti Yesu waitanidwa Yusto. Uyu yoka ili watailidwe ndi yao agwila njito anjatu panjila ya ufumu waMulungu. Akala ndilaha kwanga. 12 Epafra wakulonjelani iye nimmofi wanu ndi atumidwa wa Kristo Yesu. Iye wachita kujituma pakupembela panjila, yakuti mkoze kuima pauzene ndi kujiwichidwa pauzene pachikondi cha Mulungu. 13 Pakuti muyamikila, kutiwangwila njito kofituma panjila yatu, payao aomboledwa Laodikia payao alipo Hierapoli. 14 Luka, yufa mfumu okondedwa, ndi Dema akulonjelani. 15 Mwalonjele abale watu alipo Laodekia, ndi nimfa, ndikanisa lija lilipo mnyumba mwake. 16 Utenga u yaposakale wasomedwa mutima mwanu, isomedwe paja pajapakanisa la wa Laodikila, namwe muya aminishe muya some ija baluwa kuchoka Laodikia. 17 Kamba pa Arkipo, "penyani ija njito iyo wailandila pakati pa ambuye, kuti itumika kuichita." 18 Moni iyi ije pajanja panga namwene Paulo uyikumbukile minyololo yanga ufumu ukale ndi anyiimwe.