1 Yehova, Mulungu amabwezela chilango, Mulungu wobwezela chilango, wawala pali ise. 2 Nyamukani, woweluza ziko yapansi, pelekani ku ozivela kuyenela navo. 3 Kodi boipa bazasangalala mpaka liti, Yehova? 4 Bachosa mau yao ozitukumula; bonse bochita voipa azinvela. 5 Baphwanya bantu banu, Yehova; bavutisa mtundu ya bantu banu. 6 Bapaya mukazi wamasiye na mlendo okhala muziko yawo, nakupaya bana balibe batate. 7 Bakamba, "Yehova saona, Mulungu wa Yakobo sadziba." 8 Muvesesa, bantu opusa imwe! Opusa imwe, mudzaphunzila liti? 9 Eye wamene anapanga matu, samavela kodi? Eve wamene anapanga menso, saona? 10 EVe wamene amalanga mitundu, kodi salanga? Eve wamene amapasa muntu nzelu. 11 Yehova amaziba maganizo ya bantu,ali nthunzi. 12 Odala muntu wamene mumalangiza, Yehova, bamene mumphunzisa mulamulo yanu. 13 Mumampasa kupumula mumasiku ya mavuto, mpaka chisengu choipa ikumbiwa. 14 Pakuti Yehova sazasiya bantu bake kapena kusiya choloba chake. 15 Pakuti kuweluza khuzalako chabolungama; ndipo bonse bolungama mtima bazakonka. 16 Ndani azani pulumusa kubochita voipa? Nindani azanitandiza mumalo mwanga ku boipa? 17 Yehova nga ananitandiza, Nganina gona pansi pamalo yazi. 18 Pamene ninakamba, "Mendo yanga yatelemuka," Chipangano chikhulupililo chanu, Yehova, ananigwilila. 19 Pamene anisamalila muli ine muli bambili, zotonthoza zanu zimanikodwelesa. 20 Kodi mpando wa ufumu ugwilizane na chiwonongeko muli imwe , wamene apanga malamulo osalungama? 21 Beve bamapangana voipa kuti bapayeaphe bolungama na kuweluza muntu wosalakwa kupaiwa. 22 Koma Yehova ndiye nyumba itali yanga, na Mulungu wanga ndiye mwala otabilko wanga. 23 Eve azabwelesa machimo yawo ndipo azabaononga chifukwa cha kuipa kwao. Yehova Mulungu wathu azabajuba.