1 Ndipo Eliashib mukulu wansembe ananyamuka naba bale bake bansembe, banamanga chipata cha nkhosa. bana ipatula nakufaka chiseko pa malo. Bana ipatula kufikila ku tawa ya handiredi nakufika ku tawa ya Haraneli. 2 Kufupi nayenve bamuna bamu Jriko banali kusebenza, kufupi nabenve Zaka mwana mwamuna wa Imri anali Kusebenza. 3 Bana ba Hassenah bana manga chipata cha nsomba. barachipangila matabwa. nakufaka chiseko, nama bawuti namipiringizo. 4 Meremoti anakoza gawo inakonkapo. Nimwana wa Uriya mwana wa Hakkozi. 5 Pafupi nabeneve Meshullamu ana konza. Nimwana wa Berechiah mwana wa Meshezabel. Pafupi kwabenve Zadoki anakonza. Nimwana wa bwana. Pafupi nabenve ba Tekoyiti banakonza, koma olemekeza bawo banakana kuchita nchito yamene banalamilidwa kuli woyanganila awo. 6 Joirada mwana wa Paseah na Meshulamu mwana wa Besodeiah anakonza chipata chakudala. Banaipangila matabwa, nakuyika chiseko, nama bawuti namipiringozi. 7 Pafupi kunlai bamuna bochokela kuli Gibiyoni na Mizpa-Melatiah mu Gibiyoniti na Jodani mu Meronotayiti-mupando wachifumu wa kazembe wamuchigawo chopilila mumana. 8 Pafupi naye Uzziel mwana wa Harhaiah, omwe wabosula golide, anakonza, ndipo pafupi nayenve kunali Harhaiah, wopanga mafuta onukila. Bana manga Yelusalemu kufikila ku khoma lotakata. 9 Pafupi nabenve Rephaiah mwana Hur anakonza. Anali woyanganila hafu ya disitilikiti mu Yelusalema. 10 Pafupi nabenve Jedaiah mwana wa Harumaph anakonza kufupi nanyumba yake. Pafupi nayenve Hattush mwana wa Hasabneiah anakonza. 11 Malkijah mwana mwamuna wa Harimu na Hasshub mwana wa Pahati-Mowabu anakonza gawo inangu mosatira tawa yama fanasi. 12 Pafupi nabenve Shallamu mwana wa Hallohesh, wayanganira hafu ya disitilikiti ya Yelusalemu, anakonza, mosatira naba nake bakazi. 13 Hanun na bonkala mu Zanoah banakonza chipata cha chigwa. Banayimanya nafuti nakufaka chiseko, nama bawuti, nampiringizo. Banakonza mikono il chikwi kufikila chipata cha ndowe. 14 Malkijah mwana wa Recabu, woyanganila na disitilikiti ya Beti Haeremu anakonza chipata cha ndowe. Anayimanga nakuyoka chiseko, nama bawuti, namipingizo. 15 Shalumu mwana wa Kol-Hozeh, woyanginila madilisilikiti ya Mizpa, anamanga nafuti chipata chakasupe. Ananyimanga, nakuyika chivinnikolo pamwamba nakuyika chiseko, ma bawuti, namipiringizo. Anamanga nafuti khoma ya dziwe ya Silomu mu munda wa mfumu, kufikila ku masitepe yeyanda pansi kuchokela mu muzinda wa Davide. 16 Nehemiya mwana wa Azbuki, woyanganila theka ya disilikiti ya Beti Za, anaonza kufika kumalo yopila kuchokela ku manda ya Davide, kufika kudziwe yopangiwa na bantu, naku nyumba ya bamuna bampamvu. 17 Kuchokela enve ba Levayiti banakonza, kufikilapo Rehumu mwana wa Bani nakufupi nayenve. Hashabayi, woyananila theka ya disitilikiti ya Keila, ku disilikiti yake. 18 Kuchokels yenve ba bale bawo banakonza, kufakikapo Binnui mwana wa Henadadi, woyaganila theka ya disilikiti ya Keilah. 19 Pafupi nayenve, Ezeri mwana wa Yesgua, woyanganila pali Mizpa, anakonza gawo inangu yamene inali kuyangana kukwera kuzida zankondo pa ngodya ya chibumba. 20 Kuchokela enve Baruchi mwana wa Zabbai mwachangu anakonza gawo inangu, kuchokela ku ngodya ya chibumba kufikila chiseko chanyumba ya Elishibi mukulu wansembe. 21 Kochokela enve Meremoth mwana wa Uriah mwana wa Hajjozi anakonza gawo inangu, kuchokela kuchiseko chanyumba ya Eliashib kufikila kosilila nyumba ya Eliashib. 22 Pafupi nayenve bansembe, bamuna bamu malo yozinguluka Yelusalemu, banakonza. Kuchokela benve Benjamin na Hasshub banakonza moyanganizana nyumba yabo. 23 Kochokela benve Azariya mwana wa Maaseiah mwana wa Ananiah anakonza pafupi na nyumba yake. 24 Kuchokela yenve Binnui mwana wa Henadadi anakonza gawo inangu, Kuchokela ku nyumba ya Azariya kufikila kungodya ya chibuumba. 25 Palali mwana wa Uzai anakonza moyanganizana ngodya yachibumba na tawa yamene iyendelela kumwamba kuchokela kunyumba yapamwamba ya mfumu pa bwalo yabamalonda. Kochokela yenve pedaya mwana wa Parosh anakonza. 26 Manje bakapolo bamu tempele bonkala mu Ophel banakonza kufikila kumalo yoyanganizana chipata cha manzi chakumawa na tawa yochokelela. 27 Kuchokela yenve ba Tekoyiti banakona gawo inangu, yamene inali yoyanganizana a tawa ikulu inali yochokelela kufikila kuchibumba cha Ophel. 28 Bansembe banakonza pamwamba pa chipata cha kavalo,alionse kuyanganiza nanyumba yake. 29 kukonka benve Zadoki mwana wa immer anakonka gawo yoyanganiza nyumba yake, Ndipo kukonka yenve Shemaya mwana wa Shecaniah, wosunga chiptata chakumawa, anakonza. 30 Kukonka yenve Hananiah mwana wa Shelemiah, na Hanun mwana wa sikisi wa Zalaph, anakonza gawo inangu. Kukonka yenve Meshullamu mwana wa Berehiah anakonza moyanganiza chipinda chake chogona. 31 Kukonka yenve Malkijah, omwe wabo wosula golide, anakonza kufika ku nyumba ya kapolo wamu tempele na malonda yanali moyanganiza chipata cha musonkano na chipinda chogonela chapa mwamba pangodya. 32 Bo wosula golide na malonda banakonza pakarti pa chioinda chogona chapa mwamba cha ngodya na chipata cha nkosa.