Mutu 3

1 Agalatiya opusa! Kodi nidani amene afaka masenga pa inu? Panali pamaso pa inu pamene Kristu anaonetsedwa kupachikidwa. 2 Ici cheka ndifuna kuphunzila kwa inu: kodi munalandila mzimu ndi nchito ya lamulo kapena ndi kumvela kwa cihkulupililo? 3 kodi iye ndi opusa? Popeza muzasiliza ndi thupi? 4 Kodi inu munavutika na zintu zambili kwa chabe- ngati poyenera anali kwa chabe? 5 Ndipo iye amene akupatsa inu mzimu ndi kusebenza nchito zamphamvu mwa inu, kodi ndi nchito za lamulo kapena ndi kumvela kwa cikhulupililo? 6 Monga Abrahamu anakhulupilila Mulungu ndipo kunalengedwa kwa iye cilungamo, 7 cotero zindikilani, kuti, iwo amene alinacikhulupililo ndi ana a Abrahamu. 8 Ndipo malembo, pakuoneratu kuti Mulungu adzayesa dungama amitundu ndi ndi cikhulupililo, anayamba kale kulalikila uthenga wa bwino kwa Abrahamu, kuti, "mwa iye mitundu yonse izadalisidwa." 9 Kotero kuti, iwo amene alina chikulupililo. 10 Onse amene atama nchito za lamulo ali ndi tembelelo; ndiponso chinalebedwa,"'wotembeledwa ali yense wosankhala m'zonse zintu zinalembedwa mubuku za lamulo, ndikuchita izi." 11 Ndipo chinkhala koyera kuti kulibe ali yense wamene ayesedwa wolungama ndi lamulo pamaso pa Mulungu, chifukwa azankhala ndi moyo ndi chikulupililo." 12 Koma lamulo sichokela kwa chikulupililo, koma munthu amene achita izi nchito za lamulo adzankhala ndi izi. 13 Kristu anatiombola ku tembelelo la chilamulo, pakunkhala tembelelo m'malo mwathu- pakuti mwalembedwa, " Wotembeleledwa ali yense wopachika pamtengo"- 14 kuti dalitso la Abrahamu mwa Kristu Yesu lichitike kwa amitundu, kuti tikalandile lonjeza la Mzimu. 15 Abale, ndinena monga munnthu. Pangano lingankhale la munthu, kulibe aliyense chabe, amene anga fake pambali kapena kuonjezalako, pamene yakukhazikila na lamulo. 16 Ndipo panopa malonjeza ananenedwa kwa Abrahamu ndi kwa mbeu yake. Sanena, " kwa zimbeu, ngati kunena zambili, koma kunena na imodzi, " ndipo kwa mbeu yako, " ndi ye Kristu. 17 Ndipo ichi ndinena: lamulo, limene linafika zinapita zaka mazana anai mphambu makumi atatu, pangano ya kukhazikika kale ndi Mulungu. 18 Pakuti ngati kulowa nyumba kuchokela kulamulo, sikuchokela kulonjezano. Koma Mulungu anapatsa Abrahamu kwa lonjezano. 19 Kodi, nanga, chinali cholinga cha lamulo? chinaonjezeka chifukwa cha zolakwa, kufikila mbeu ya Abrahamu amene analonjezela ndi angelo m'zanja la mkhalapati. 20 Koma mkhalapati siliya imodzi, koma Mulungu ali modzi. 21 Kodi lamulo itsusana nao malonjezano a Mulungu? Iyayi simwanene nditu! Chifukwa ngati lamulo inapasiwa kuti ipase moyo, ndipo chilungamo sembe chinabwela na malamulo. 22 Koma malemba yanamanga machimo yonse. Mulungu anachita ichi pakuti lonjezo lopulumusa ise mwachikululupilo muli Yesu ungapasiwe kuli bamene bakulupilila. 23 Koma pamene chikulupililo chikalibe kubwela, ife tinali wogwidwa mulamulo, mpaka chisomo china vumbulisidwa. 24 Momwemo chilamulo chinakhala woyanganila mpaka kubwela kwa Kristu. Kuti tikayesedwe olungama ndi chikulupililo. 25 Koma popeza kuti chikulupililo chabwela, sitinkhalanso muyansi a mkhalapakati. 26 Pakuti inu onse muli ana a Mulungu mwa chikulupililo cha mwa Kristu Yesu. 27 Pakuti onse amene munabatizidwa kwa Kristu munavela Kristu. 28 Muno mulibe myuda, kapena Greeki, muno mulibe kapolo, kapena omasuka, muno mulibe mwamuna ndi mkazi, pakuti muli onse mwa Kristu Yesu. 29 Koma ngati muli a Kristu, inu muli mbeu za Abrahamu, nyumba monga mwa lonjezano.