1 Manje pali iyo nthawi mfumu Herode anamanga bengu bamene anali bamumpingo kuti abasause. 2 Anapaya Jemusi m'bale wake wa Yohane na lupanga. 3 Pamene anabona kuti ici cinakondwelesa Ayuda, anamanga futi Petro naye. Ayo yanali masiku yapwando la pasaka. 4 Pamene anamunga, anamuyika mujele anayika basilikali bali 4 mumagulu 4 kuti bamuyanganile yeve, ananganiza zomuleta kuli banthu pwando Yasaka itasila. 5 So Petelu anamusungila mujele, koma banamupempherera maningi kuli baja benzeli mumpimgo. 6 Siku pamene Herode akalibe kumucosa, usiku uja Petro anagona pakati pa asilkali babili, omangidwa namacheni yabili, ndipo omuyanganila benzeli pasogolo paciseko benzo yanganila jele. 7 Onani apo, mngelo wa Ambuye anabonekela mwazizi pali yeve, ndipo laiti inabonekela mu celo. Anamugunduza Petro pambali nomubusha nokamba ati, "Nyamuka mwamsanga." Ndipo ma cheni yake yanacoka mumanja mwake. Mngelo anakamba nayeve kuti, 8 " Zivalike wake ndipo vala namasanda. Petro anacita socabe. Mngelo anakamba nayeve ati, "Vala malaya yakunja ndipo unikonkhe." 9 So Petro anamukonkha ndipo anacoka. Sanazibe kuti camene cinacitika na mngero cenzeli ca zoona. Ananganiza kuti enzo ona maso mphenya. 10 Pamen anapita oyanganila oyamba nawacibili, anafika pageti yasimbi yamene yenzoyenda mu tauni; inazisegukila yeka kuli beve. Banacoka ndipo banayenda mumsebo, ndipo pamene apo mngero anamusiya yeka. 11 Pamene Petro anazindikila zamene zinacitika, anakamba ati, "Manje niziba kuti Ambuye atumu mngero wabo kunicosa mumanja ya Herode, nakuciyembezo ca banthu aci Yuda." 12 Pamene anazindikila izi, anayenda kunyumba ya Maria maiwake wa Yohane wamene ciwongo cake ni Mariko; okhulupilila bambili benzeli banakumana kwamene ndipo benzopemphera. 13 Pamene anagogoda paciseko ca gedi, wanchito mkazi zina lake Roda anayankha. 14 Pamene anazindikila mau yaPetro, mwacimwemwe anakangiwa kusegula ciseko; m'malo mwake anabwela anathamangila mucipinda; norepota kuti Petro enzeli imilile paciseko. 15 Ndipo anakamba kuti kwa yeve, "Ndiwe ofuntha." Koma analimbikila kuti ndiye mwamene cilili. Banabwela bakamba ati, "Nimungelo wake." 16 Koma Petro anapitiliza kugogoda, ndipo pamene anasegula ciseko, banamuona ndipo anadabwa. 17 Petro anabakambisa nakwanja kwake kuti bankhale zii, ndipo anabauza mwamne Ambuye banamucosela mujele. Anakamba ati, Muripote ivi vinthu kuli Jemusi na abale." Ndipo anacoka noyenda kumalo yenangu. 18 Manje pamene kunaca, kwenzelibe cisangalaro ciliconse pakati pa asilikali, pazamene zinacitika pali Petro. 19 Pamene Herode anamusakile yeve ndipo sanamupeze, anafunsa oyanganila ndipo anapeleka lamulo kuti apayiwe. Ndipo anacoka ku Yudeya noyenda ku Sizeliya nonkhala kwamene kuja. 20 Manje Herode enzeli okalipa nabanthu baku Taila na Sidoni. Banayenda kuli yeve pamozi. Banagonjesa Bulatasi, othandizila mfumu, kuti abathandize. Anapempha mtendere, cifukwa ziko lao inalandila vakudya kucoka ku ziko la mfumu. 21 Pasiku yoikika Herode anazivalika zovala va ufumu nonkhala pamu pando wacifumu, anapeleka mau kwa beve. 22 Banthu banapunda ati, "Aya nimau yakamulungu, osati yamunthu!" 23 Pamene apo mngero wa Ambuye anachaya yeve, cifukwa sanapase Mulungu ulemelero; anadyewa nanyongolosi nomwalila. 24 Koma mau ya Mulungu yanafalikila nopakilako. 25 Pamene Banabasi na Sauli anasiliza nchito yao ku Yelusalemu, banacokako uko; banatenga Yohane wamene ciongo cake ni Mariko. (Ma baibolo yene yebelenga kuti, Banabasi na Sauolo anabwelela ku Yelusalemu (olo kuja))