Mutu 6

1 Bana bamuna ba mneneli bana kamba kuli Elisha, "Pamalo pamene tinkala iwe naise tonse ni pan'ono manigi. 2 Leka tiyende ku Jordan tapapta, ndipo uleke mwamuna aliyense ajube mutengo, naku tileka timange malo yonkalapo kuja kwamene tingankale." Elisha anayanka, "Munga yende." 3 Umozi pali beve anakamba, "Yenda naba nchito bako." Elisha anayanka, "Nizayenda." 4 5 Mwaicho anayenda nabo, ndipo pamene banabwela ku Jordan, banayamba kutema mitengo. Koma pamene umozi anali kujuba, analila naku kamba, "Iye mbuye wanga chinali chopempa!" 6 Mwaicho mneneli anakamba, "Chagwela pati?" Mwamuna analangiza Elisha pa malo. Ndipo anajuba ka mtengo, ku kataila mu manzi, nakulegesa chisulo kubwela pamwamba pa manzi. 7 Elisha anakamba, "Chi dobe." Ndipo mwamuna ana pitisa kwanja yake nakutenga. 8 Manje mfumu wa Aram enzo chita ndeo kuli ba Israyeli. Ana nvelana naba nchito bake, kukamba, "Musonkano wanga uzunkala so na malo ya so." 9 Mwaicho mtumiki wa Mulungu anatuma kuli mfumu wa Israyeli, kukamba, "Chenjela osapita ku malo aya, chifukwa ma Aramean bayenda kwamene kuja." 10 Mfumu wa Israyeli anatuma mau ku malo yamene mtumiki wa Mulungu anakamba naku muchenjeza. Kuchila kamozi olo kabili, pamene mfumu anayenda kuja, enzeli ku londewa. 11 Mfumu Aram anakalipisiwa nama chenjezo aya, ndipo anaitana banchito bake naku kamba kuli beve, "Simuzani uza pakati paise wamene ali kumbali kuli mfumu wa Israyeli?" 12 Mwaicho umozi pali banchito bake anakamba, "Awe mbuye wanga, mfumu, chifukwa Elisha mneneli wa Israyeli amauza mfumu wa Israyeli amakamba vamene mumakamba mu chipinda mwanu." 13 Mfumu anayanka, "Yendani muone kwamene ankala Elisha kuti ninga tume bamuna kumugila." Anauziwa, "Ona, ali mu Dothan." 14 Mwaicho mfumu anatuma ma hosi, magalata naba nkondo bambili. Banabwela usiku nakuzunguluka malo. 15 Pamene banchito ba mtumiki ba Mulungu bana uka uka kuseni nakuyenda panja, ona, ba nkondo bambili nama hosi na magalata bana zunguluka malo. Wanchito wake anakamba kuli eve, "Iye mbuye wanga! Tizachita chani?" 16 Elisha anayanka , "Osayopa, chifukwa bamene bali naise bali bambili kuchila bali nabeve." 17 Elisha ana pempela naku kamba, "Yahwe nipempa mu musegule menso kuti aone." Ndiye Yahwe anasegula menso ya wanchito ndipo anaona. Onani, lupili inalifulu nama kavalo na mgalata kuzungulika Elisha! 18 Pamene ma Arameans yanabwela pansi kuli eve, Elisha ana pempela kuli Yahwe naku kamba, "Ba pangeni mpofu bantu aba nikupempani." Mwaicho Yahwe ana bapanga mpofu monga mwamene Elisha anapempa. 19 Ndiye Elisha anauza ma Arameans, "Iyi, sinjila, kapena malo. Nikonke ndipo nizakuletani kuli mwamuna wamene musakila." Ndiye anaba sogolela ku Samria. 20 Chinabwela chakuti pamene bana bwela mu Samaria, Elisha anakamba, "Yahwe segulani menso yaba muna aba kuti bangone." Yahwe anasegula menso yabo banaona, na Onani, banali pakati pa malo ya Samaria. 21 Mfumu wa Israyeli anakamba kuli Elisha, pamene anabaona, "Tate wanga, niba paye? Niba paye?" 22 Elisha anayanka, "Musa bapaye. Kodi unga paye bamene wagwila nabemba yako naku gwada? Ba pasaeni mukatenna manzi beve, kuti badye nakumwa, ndipo bayende kuli mbuye wao." 23 Mwaicho mfumu anakonza vokudya vabo vambili, ndipo pamene banamwa nakumwa anapisha, naku bwelela kuli mbuye wabo. Ija gulu yaba nkondo baku Aramean sibana bwelele nthawi itali mumalo ya Israyeli. 24 Pambuyo pake uyu Ben Hadad mfumu wa Aram bana kumana naba nkondo bake bonse naku menya ba Samaria na kuizunguluka. 25 Mwaicho panali njala yaikulu ku Samaria, taonani, azangulila mzinda uyu mpaka bulu mukulu azagulisiwa na ndalama zasiliva makumi asanu ndi atatu, na cha chinai cha munkola yakunda matuvi na siliva. 26 Pamene mfumu wa Israyeli enze kupita pa chipupa, mukazi analila kuyli eve, kukamba, "Tandiza mbuye wanga, mfumuy wanga." 27 Anakamba, "Ngati Yahwe sana kutandize ninga kutandize bwanji? Kulikochili chonse chamene chi chokela popuntila kapena mopenolela pesa?" 28 Mfumu anapitiliza, "Nichanoi chamene chiku vita?" Anayanka, "Uyu mukazi anakamba kuli ine, 'Pasa mwana wako mwamuna kuti tumudye lelo, ndipo tizadya mwana wanga mwamuna mailo."' 29 Ndipo tina mupika naku mudya mwana wanga mwamuna, ndipo nina muuza pa siku yokonkapo, "Pasa mwana wako mwamuna kuti timudye, koma anamubisa mwana wake mwamuna." 30 Ndipo pamene mfumu ananvela mau ya mukazi, anayamba vovala vake (manje anali kupita pa chipupa), ndipo banthu bana langana nakuona kuti anavala masaka, kutupi yake. 31 Ndipo anakamba, "Mulungu anilange mobilikiza, ngati mutu wa Elisa wa safati unkale pakem lelo." 32 Koma Elisha anali nkale munyumba mwake naba kulu bana naye. Mfumu anatuma mwamuna kuchoka pasogolo pake, koma pamene mtumiki anabwela kuli Elisha, anakamba kuli bakulu, "Onani uyu mwana wa muna wa paya atuma kuti atenga mutu wanga? Onani pamene mtumiki azabwela, valani chiseko, na kugwila naku vala chiseko. Kodi sikubveka kwamendo ya mbuye wake kumboyo kwake?" Pamene enzeli akali kukamba nabeve, mtumiki anabwela pansi kuli eve. 33 Mfumu anakamba, "Onani, kuvutika uku kuchokela kuli Yahwe. Nichani chamene nizayembekezela Yahwe?"