Mutu 7

1 Elisha anakamba, "Nivela mau ya Yahwe. Ichi ndiye chamene akamba Yahwe: 'Mailo monga nthawi zino muyeso wa unga opangila mukate wabwino uzagulisiwa pa sekeli na miyeso ibili ya belele pachipata cha Samaria." 2 Pamenepo oyanganila kwanja yake azanka munthu wa Mulungu, nati, onani angankale Yahwe akapange mawindo kumwamba, mwati ivi vingacitike?" Elisha anayanka kuti, "Uzatamba vichitika na menso yako, koma simuzadya kanthu." 3 Manje panja papolobela mumzinda panali bamuna bali foo bezeli nama khate. Bana kambisa beka beka, "Nichani chamene tizankalila kuno panka tife? 4 Ngati takamba kuti tiyende mu mzinda, pamenepo njala ili mzinda ndipo tiza fela mwamene muja. Koma tikankala chabe pano tizafa. Manje tiyeni tiyende ku gulu ya nkondo ya Aramean. Ngati bazatisunga ba moyo, tizankala ba moyo, ndipo bakatipaya tizafa." 5 Pamenepo anauka mu mazulo kuti angene mu msonkano wa Aramean; anafika kumapeto kwenikweni kwa msaso anapeza kuti palibe munthu. 6 Nichifukwa Mulungu anapanga bankondo ba Aramean kunvela chongo cha magalata, nachongo cha matavala - chongo chinangu cha chongo chinangu cha bankondo, bambili, ndipo bana kambisana, "Mfumu wa Israyeli yanvelana na mafumu yaku Hittites na Egypto kutiukila ise." 7 Ndiye bankondo bana ima naku mbululuka kumazulo; bana siya ma tenti yabo, makavalo yabo, mabulu yabo, na msonkano monga mwamene yenzeli, naku tamanga mopulumusa moyo wabo. 8 Pamene bamuna bakhate banabwela kumbali ya msonkano, banayenda mu tenti imozi na kudya na kumwa, ndi kutenga siliva na golide na vovala, nakuyenda ku vibisa. Banabwelela naku ngena mu tenti inangu ndipo banatenga vintu vosiyana siyana kuja, ndipo bana vibisa. 9 Ndiye bana kambisana, "Sitichita vabwino. Iyi nisiku ya nkani yabwino, koma tinkala zee pali yeve. Ngati tizayembekeza mpaka siku kubwela, chilango chizabwela paliise. Manje, bwelani, lekani tiyende na kuuza nyumba ya mfumu." 10 Mwaicho banayenda naku itana bapa chiseko chamuzinda. Bana bauza, kukamba, "Teze tianyenda ku msonkano waba Aramean, koma kwenzelibe munthu aliyense na chongo cha aliyense, koma kwezeli ma hosi yomangililiwa, nama bulu yo mangililiwa nama tenti mwamene mweyenzelili. 11 Ndipo bapa chiseko bana punda pali nkani, ndipo inauziba mukati mwa munyumba ya mfumu. 12 Ndipo mfumu anauka usiku naku kamba kuli banchito bake, "Niza ku uzani vamene ma Aramean bana chita kuli ise. Baziba kuti ndise okalipa, mwaicho banachoka musonkano naku bisama mu munda. Banakamba, 'Bakachoka panja pa mzinda, tizabatenga ba moyo, naku ngena mumzinda.'" 13 Umozi waba nchito wa mfumu anayanka naku kamba, "Nikupempalela, bamuna benangu batenge makavalo yali faivi yaza salapo, yamene yasala mu mzinda. Bali monga magulu yabanthu baku Israyeli bamene banyenda - bambili bana nafa nakufa manje; lekani titum 14 Kotero iwo anatenga magaleta awiri ndi akavalo, ndipo mfumuyo inawatumiza iwo kutsata gulu lankhondo la Aaramu, nati, "Pitani mukawone." 15 Anawatsatira mpaka kukafika ku Yorodano, ndipo njira yonse inali yodzaza ndi zovala ndi zida zomwe Aaramu anataya mofulumira. Choncho amithenga aja anabwerera kukauza mfumu. 16 Anthuwo anapita kukafunkha msasa wa Aaramu. Choncho ufa wosalala unagulitsidwa pa sekeli, ndi miyezo iwiri ya barele ndi sekeli, mogwirizana ndi mawu a Yehova. 17 Mfumu idalamula kapitawo yemwe adatsamira dzanja lake kuti aziyang'anira chipata, ndipo anthu adamupondereza pachipata. Adamwalira monga adanenera munthu wa Mulungu, yemwe adayankhula pomwe mfumu idatsikira kwa iye. 18 Ndipo kudatero monga munthu wa Mulungu adanena kwa mfumu, kuti, Nthawi ngati iyi chipata cha Samariya chidzakhala ndi miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, ndi muyeso umodzi wa ufa ndi sekeli. 19 Woyang'anira wamkuluyo adayankha munthu wa Mulungu nati, "Onani, ngakhale Yehova atapanga mawindo kumwamba, kodi izi zingachitike?" Elisa adati, "Udzionera ndi maso ako, koma osadya kanthu." 20 Izi n’zimene zinamuchitikira, chifukwa anthu anam’ponda pachipata ndipo anamwalira.