Mutu 4

1 Manje umozi mwana mwamuna wa mneneli mkazi wake na bwelela alila kuli Elisha,kukamba, "Wanchito wanu mwamuna wanga afa, ndipo uziba kuti wanchito wanu enzo yopa Yahwe. Manje bokongolesa babwela kutenga bana banga babili bankale banchito bake." 2 Mwaicho Elisha anakamba kuli eve, "Nichani che ninga kuchitile? Niuze unachani munyumba mwako?" Anakamba, alibe chili chonse wanchito wako munyumba koma che poto yama futa." 3 Ndiye Elisha anakamba, "Kapempe ma jah kuli bapafupi bako, muma jah mulibe vili vonse. Pempa yambili monga yeunga pempe. 4 Ndiye ungene mukati naku vala chiseko kumbuyo kwako kwako na bana bako, nakutila mafuta muma jah yonse, uchosepo ma jah yazula. " 5 Mwaicho anamusiya Elisha naku vala chiseko kumbuyo kwake nabana bake. Ndiye banaleta ma jah kuli eve naku ikamo mafuta. 6 Pamene vina zula, anakamba kuli mwana wake mwamuna , "Niletele jah inangu." Koma anakamba kuli eve, "Kulibe ma jah yenangu. Ndiye mafuta." Yanaleka kupita. 7 Ndiye anabwela naku uza mwana mwamuna wa Mulungu. Anakamba, "Kagulise mafuta; lipila nkongongole yako, nakunkala nabana bako bamuna." 8 Siku ina Elisha anayenda ku Shunem kwamene mukazi ana muuza kudya naye. Mwaicho monga kambili enzo pitako Elisha, enzo imilila kudya. 9 Mukazi anakamba kuli mwamuna wake, "Ona, manje, nazindikila kuti uyu ni mwana wa Mulungu oyela wamene ama pitililako. 10 Lekani tipange ka pinda ka Elisha pamwamba pa malata, naku ikamo pogona, tebulo, mupando, na laiti. Ndiwe akabwela kuli ise, azankala paja." 11 Mwaicho pamene siku ina bwela futi kuti Elisha aimilile paja, anankala mu chipinda naku pumulilamo. 12 Elisha anakamba kuli Gehazi wanchito wake, "Muitane uyu Shunammite." Pamene ana muitana, anaimilila pasogolo pake. 13 Elisha anakamba kuli eve, "Kamba kuli eve, 'Wayenda muma vuto yonse kusamalila ise. Nichani chinga kuchitikileni? Tinga ku kambile kuli mfumu olo wolamulila wa nkondo?"' Anayanka, "Ninkala pakati pa banthu banga" 14 Mwaicho Elisha anakamba, "Nichani che tingamuchitile kanshi?' Gehazi anayanka, "Nimotere, alibe mwana mwa muna, ndipo mwamuna wake ni okota." 15 Mwaicho Elisha anayanka, "Muitane." Pamene ana muitana, anaimilla pa chiseko. 16 Elisha anakamba, "Nthawi ino ya chaka, mu nthawi chaka chobwelela, uzagwila mwana mwamuna ." Anakamba, "Iyayi, mbuye wanga na mwana wa Mulungu, osamunama wanchito wako." 17 Koma mukazi anabala nakunkala na mwana mwamuna nthawi yamene ija chaka chokonkapo, monga Elisha ana muuza. 18 Pamene mwana anakula, siku imozi anayenda panja kuli batate bake, bamene banali nabo lima babo. 19 Anakamba kuli batate bake, "Mutu wanga, mutu wanga." Batate bake bana kamba kuli ba nchito babo, "Munyamuleni kuli bamai bake." 20 Pamene banchito bake bana munyamula naku peleka mwamuna kuli bamai bake, mwana anankala pama konkola pabo mpaka namuzuba nakufa. 21 Mwaicho mukazi ananyamuka naku goneka mwamuna pogona pa munythu wa Mulungu, anavala door naku choka. 22 Anaitana bamuna bake, naku kamba, "Napapata nitumimeni wa nchito umozi na donkey. Mwaicho kuti niyendese kuli mwana wa Mulungu naku bwelela." 23 Bamuna bake bana funsa, "Nichani ufuna kuyenda kuli eve lelo? Simwezi yanyowani olo sabata." 24 Ndiye ana kwela pa donkey naku kamba kuli wanchito wake, "Yenza mwa musanga, osa yenza pangono koma ngati naku uza." 25 Mwaicho anayenda naku bwela kuli mwana wa Mulungu pa pili ya Carmel. Manje pamene mwana wa Mulungu ana muonela patali, ana kamba kuli Gehazi wa nchito wake, "Ona, apa bwela mukazi wa Shunammite. 26 Napapata mutamangile naku kamba kuli eve, 'Mwati vonse vili bwino iwe naba muna bako na mwana."' Anayanka , "Vili bwino." 27 Pamene anabwela kuli mwana wa Mulungu pa lupili, anagwila mendo yake. Gehazi anabwela pafupi na eve kuti amu choseko koma mwana wa Mulungu anakamba , "Muleke, chifukwa niokalipa manigi, na Yahwe abisa vuto kuli ine, ndipo kulibe vamene anniuza." 28 Ndiye anakamba, "Nina ku pempani mwana mwa muna, mbuye wanga? Sini nakamba kambe, 'Kuti osa ninama'?" 29 Ndiye Elisha anakamba kuli Gehazi, "Vala vapa ulendo na kunyamula vintu vanga mumanja mwako. Yenda kunyumba kwake. Ngati wakumana na mwamuna aliyense, osa mmuposha, ndipo ngati aliyense aku posha, osa muyanka ugoneke vintu vanga pa menso pa mwana." 30 Koma mai wamwana anakamba, "Monga Yahwe wamoyo, monga naiwe wa moyo, siniza kuleka." Mwaicho Elisha anaimilila naku mukonka. 31 Gehazi anayendesa pasogolo pabo nakugoneka vintu pamnso pa mwana, koma mwamna sana kambe olo kunvela. Ndiponso Gehazi anabwelela ku kumana na Elisha naku muuza kukamba, "Mwana sana uke." 32 Pamene Elisha anafika panyumba, mwana anali okufa enzeli akali pogona. 33 Mwaicho Elisha anangena naku vala chiseko pali mwana na eve nakumu pempelela kuli Yahwe. 34 Anayenda pamwamba naku mugenela mwana; anaika kamwa yake pakamwa pake, menso yake pamenso yake ndipo manje yake pa manja pake. Ana ziyondolola pali mwana, ndipo tupi yamwana inathuma. 35 Ndiye Elisha ananyamuka naku zunguluka chpinda naku nyamulka futi naku ziyondolola pali mwana. mwana ana etyemula kali seveni ndiye kusegula menso yake! 36 Mwaicho Elisha anaitana Gehazi naku kamba, "Muitana Shunammite!" Mwaicho anamuitana, ndipo pamene anangena mu chipinda, Elisha anakamba, "Mutenge mwana wako mwamuna." 37 Ndiye anagoneka pamenso pake pansi pa memndo yake nakugwanda pansi, naku munyamula mwana wake mwamuna nakuyenda panja. 38 Ndiye Elisha anabwela futi ku Gilgal. Kwezeli njala mumalo muja, na bana bamuna ba mneneli banali nkale pasogolo pake. Anakamba ku banchito bake, "Ikani poto ikulu pa mulilo naku pika supu yabana bamuna ba baneneli." 39 Umozi pali beve anayenda kuika pamozi ndiyo zamatepo. Anapeza vinyu yamusanga nakuika pamozi nongo zamusanga kuzulisa zake. Bana juba na kuika pamozi mu nyama, koma sanazibe mutundu wakayena. 40 Mwaicho bana tila nyama kuti bamuna badye. Nthawi ing'ono pamene benze kudya, bana lila naku kamba, "Mwana wa Mulungu, muli infa mu poto!" MWaicho sibanadye nafuti. 41 Koma Elisha anakamba, "Letakoni unga opangila buledi ." Anaitila mu poto naku kamba, "Batitile banthu kuti banthu badye." Pamenepo munalibe kanthu kubasausa mumphika. 42 Mwamuna anachokela ku Ball Shalisha kuli mtumiki wa Mulungu naku bwelesa mikate twenti ya bale mu saka yake kuchokela nthawi yokolola, na ngalata zasopano. Anakamba, "Pasani banthu ivi kuti badye." 43 Na wanchito wake anakamba, "Nivichani vamene niza faka pasogolo pali bamuna bali handredi?" Koma Elisha anakamba, "Bapaseni ivi banthu, kuti badye, chifukwa Yahwe akamba, ' Bazadya navinangu ku salako." 44 Mwaicho banchito bake bana faka pasogolo pabo; banadya, navinangu kusalako, monga mwamene mau ya Yahwe yana lonjeza.