Mutu 19

1 Zinali pamene mfumu Hezekiah anamvela ripoti, anang'amba zobela zake, anabvala masaka , nayenda ku nyumba ya Yahwe. 2 Anatuma Eliakim, amene anali mu nyumba yake, na Shebna wolemba, na akulu-akulu ansembe, bonse banazivalika masaka, Isaya mwana mwamuna wa Amoz, muneneli. 3 Banakamba kuli eve, " Hezekiah kuti, ' Siku iyi ni siku ya masauso, cizuzulo, na masuso, pakuti bana bafika pa nthawi yo badwa, koma kuli mhamvu kuti ba badwe. 4 Cilingati kuti Yahwe Mulungu wanu azamvela mau onse ya mkulu wa nkondo, wamene mfumu ya Assyria mkulu wa nchito wake amutuma atonze Mulungu wamoyo, naku zula mau amene Yahwe Mulungu wanu amvela. Manje ngamulani mapemphero yanu kwa baja bamene bana sala. 5 Ndipo ba mfumu Hezekiah bana bwela kuli Isaya, 6 na Isaya anabauza beve, " Kambani kuli mukulu wanu; ' Yahwe akamba, " Musayope pali mau mwamvela, yamene uyu wanchito wa Assyria anitukwanilapo ine. 7 Onani, nizaika pali eve mzimu, ndipo azamvela mau yena nakubwelela ku malo yakwao. Nizamupanga kuti angwe na lupanga ya mumalo ya kwa." 8 Ndipo mkulu wa nkondo anabwela nakupeza kuti mfumu ya Assyria amenyana na Libnah, cifukwa anamvela kuti mfumu ayenda ku Lachish. 9 Ndipo Sennacherib anabvela kuti mfumu Tirhakah waku Cush na Egypto anaika pamodzi banthu ku amenyane naye, eve anatuma mthrnga kwa Hezekiah. 10 "Kamba kuli Hezekiah mfumu ya Yuda, 'Musalole mulungu wanu wamene mukhulupirilamo kuminamizzani imwe, kukamba, " Yerusalemu sazapasiwa mmanja ya mfumu ya Assyria." 11 Onani, mwamvela vamene mfumu ya Assyria anacita kuli malo yonse anayaong'onga kosilizilatu. Ndipo muzapulumusiwa? 12 Kapena milungu ya ziko yabapulumusa beve, ziko yamene makolo yanga atate anaononga: Gozani, Haran, Rezeph, na banthu baku Eden mu Tel Assar? 13 Mfumu yaku Hamah, ilikuti mfumu yaku Arpad, mfumu yaku malo yaku Sepharvaim, Hena, na Ivvah?" 14 Hezekiah analandila kalata iyi kucokela kwa mesenja ndipo anaibelenga. Ndipo anayenda pamwamba pa nyumba ya Yahwe na kuika kalata pamenso ya Mulungu. 15 Hezekiah anapempera kuli Yahwe na kuti, " Yahwe wamene akhla pakati, Mulungu wa Israyeli, imwe amene mukhala pakati pa kerabi, imwe mweka Mulungu wa ufumu wa kumwamba na pansi. Munapanga kumwamba na pansi pa calo. 16 Mvelani matu yanu, na kumvela. Segulani menso yanu, Yahwe, na kuona, naku mvela mau ya Sennacherib, yamene atuma kunyoza Mulungu wa moyo. 17 Zoona, Yahwe, mafumu ya Assyria yaononga calo cao na malo yao. 18 Baika milungu yao pa mulilo, pakuti siinalin milungu koma nchito ya banthu amuna na manja yao, mitengo na mwala. Ndipo Assyria baononga zonse. 19 Koma manje, Yahwe Mulungu wanthu, tipulumuseni ise, nikupemphani, ku mphamvu zake, kuti mafumu yanango yazibe kuti ndimwe, Yahwe, Mulungu mweka. 20 Isaya mwana mwamuna wa Amoz anatuma uthenga kuli Hezekiah, kuti, " Yahwe, Mulungu wa Israyeli akuti, 'Cifukwa wa pemphera kuli ine kukamba za Sennacherib mfumu ya Assyria, nakumvela iwe. 21 Aya ni mau yamene Yahwe akamba pali eve: " Namwali mwana mukazi wa Ziyoni nkhakhale kuti unyoza naku seka. Mwana mukazi waku Yerusalemu ana pukusa muli wako kuli iwe. 22 Nindani amene waononga naku tukwana? Kuli uyo amene mwakweza na mau yako nakunyamula menso yanu mozikweza? Nakunyoza Oyera yaku Israyeli 23 Mwa amesenja banu mwacimwila Mulungu, ndipo mkuti, ' Naza mkhondo zanthu nayenda kumwamba pamaphiri, pamwamba pa Lebanon. Nizagwesa utali wa mikungaza na mitengo yosankhiwa ya mlombwa. Niloba futi mngika mukati, mweni mweni mkkati mwa sanga. 24 Nakumba motapa manzi namwa manzi yakunja. Na yumika tumana twa mu Egypto mwa miyendo yanga. 25 Simunamvele kuti ninacitta kudala masiku yaja yakudala? Na sebenza mwa ma masiku ya makolo yanthu sopano nifuna vicitike. Mulipo kuti kucosako ma minzi aya mumalinga ya munja. 26 Onkhalamo: ba mhamvu zing;ono avaliwa naku mvesewa nsoni. Ni voshanga va mu munda vili gilini mauzu a mtenje kapena ma munda, yashokewa yaka libe kukula. 27 Niziba kunkhala pansi kwako, kuyenda kunja kwako, kubwela kwako, naku nizazila kwako kwa nga. 28 Cifukwa ca kunizazukiola kwako kuliine. Cifukwa n thota zaka zamveka kuli ine nizaka mbeza mu mphuno mwako, na cokumwa canga mu kamwa mwako; nizakuikaka kumbuyo, monga unabwelela." 29 Ichi chizankhala cindikilo cako: Cino caka uzadya za molulumukwa, mu caka cibwela mufunika kushanga. Koma mu caka cacitatu mufunika ku shanga nakokolola, mu shange mphesha na kudya zbala zake. 30 Bosala ba Yuda bazaika mizu naku bala zipaso. 31 Kucoka ku Yerusalemu osala azacoka, kucokela ku malupili ya Zayoni opulumuka bazabwela. Cofuna ca Yahwe onkhala pakati azacita izi. 32 Pamene apo Yahwe anakamba izi pa mfumu ya Assyria: " Sazabwela mu malo kapena kulusa mkondo pali ponse pazankhala palibe nkhide. Covala pa cifuba, kapena kumanga malo yobisalamo pomenya nkhondo. 33 Njila yamene azabwelelamo niyamene azayendelamo; sazaloba mumalo - alamula Yahwe." 34 Nizabachingiliza malo yano nakuyapulumusa, cifukwa cacifunilo canga na cifukwa ca Davidi mutumiki wanga." 35 Cinabwela pa usiku uja kuti mungelo wa Yahwe anayenda kunja nakumenya malo ya Assyria, kupaya ba nkondo185,000. Pamene bamuna banauka kuseni-seni, ma thupi yakufa yanali paliponse. 36 Ndipo Sennacherib mfumu ya Assyria anachoka ku Israyeli nakuyenda ku nyumba ndipo anakhala ku Nineveh. 37 Patapita nthawi, pamene anali ku pemphla mu nyumba ya Nisrok mulungu wake, bana bake bamuna Adrammelek na Sharezer bana mupaya na lupanga. Ndipo banatabila ku malo aku Ararat. Na Esarhaddon mwana wake mwamuna anakhala mfumu.