Mutu 18

1 Ndipo munali mu caka ca citatu ca Hoshea mwana mwamuna wa Elah, mfumu ya Israyeli, Hezekiah mwana mwamuna wa Ahaz, mfumu ya Yda anayamba kulamulira. 2 Anali na zaka twenti-faivi pamene anayamba kulamulira; analamulira zaka twenti-naini mu Yerusalemu. Amai bake beze Abijah; bezeli mwana mukazi wa Zakaria. 3 Anacitazoyenera pamenso ya Yahwe, anakonkha cisanzo chazamene Davide, anali anacita. 4 Anacosa malo yapamwamba, anaononga miyala yaimikila mizati, ana gwesa voimikila Asherah. Anatiola njoka yamene Mose ezeli anapanga, cifukwa banthu ba Israyeli bezeli ku shoka vonukilisa kuli ico; zina yake yeze "Nehushtan." 5 Hezekiah anakhulupilira muli Yahwe, Mulungu wa Israyeli, nakuti pambuyo pake kunalibe wingo ezeli ngati eve pamafumu bonse ba Yuda, kapena pa mafumu bezelipo akalibe kukhalapo eve. 6 Anagwilira kuli Yahwe, Sanaleke kumukonkha koma anasunga malamulo, yake yamene Yahwe anapasa Mose. 7 Ndipo Yahwe anali ndi Hezekiah, konse kwamene anayenda analemela. Anaukira mfumu ya Assyria ndipo sana mutumukile iye. 8 Anamenya Afilisti ku Gaza na malile apafupi, kucokela ku nsanja yaolonda malo opotulika yaja. 9 Mu caka ca cinai mfumu Hezekiah, cinali caka seveni ca Hosheah mwana mwamuna wa Elah mfumu ya Israyeli, Shalmaneser mfumu ya Assyria analobelela Samaria ndi kuitenga. 10 Pa kusila kwa caka ca citatu banatenga, mucaka ca sikisi cah Hezekiah, camene cize caka ca naine ca Hoshea mfumu ya Israyeli; munjila iyi Samaria inatengewa. 11 Pamene apo nfumu ya Assyria anatenga Israyeli nakuyenda ku Assyria naku baika ku Halah, napa mabali pa kamana ku Gozan, na mumalo yaku Medes. 12 Anacita ivi cifukwa sibanakonkhe mau ya Yahwe Mulungu wao, koma banapwanya cipangano, vosevamene Mose mutumiki wa Yahwe analamula. Banakana kumvela kapena kucita. 13 Ndipo mucaka ca fotini cha mfumu Hezekiah, Sennacherib mfumu Assyria anamenya onse malo onse ya malinga anakupoka. 14 Ndipo Hezekiah mfumu ya Yuda anatuma mau kuli mfumu ya Assyria, wamene ezeli pa Lachish, kuti, " Nakulakwila iwe. Ucoke kuli ine. Ciliconse camene uzaniuza kucita nizacita." Mfumu ya Assyria inafuna kuti Hezekiah mfumu ya Yuda kuti alipile matalanta yali handiredi ya siliva na matalanta yali feti ya golide. 15 Na Hezekiah anapasa iye siliva yonse yamene inapezeka mu nyumba ya Yahwe na mosungila za umfumu. 16 Hezekiah nthawi iyi anakwangwe golidi yaku ciseko caku tempeleya Yahwe naku voimila kuja vamene anavika vitali; anapasa golide mfumu ya Assyria. 17 Koma mfumu ya Assyria anasonkhaniza asilikali ba nkondo ampha,vu kutumanduna na madoda na mukulu wa nkondo waku Lachish kuli mfumu Hezekiah ku Yerusalemu. bana yenda na mendo pansi nakufika ku Yerusalemu. Nakufika pa manzi pa yapamwamba munjira yaku mwaniko amene asoka nyula. 18 Pamene anaitana mfumu Hezekiah, Eliakim mwana mwamuna wa Hilkiah, amemne anaona nyumba ya mfumu, na Shebna olemba, na Joash mwana mwamuna wa Asaph, amene anali kulemba mbili. 19 Anakamba nao kazembe kuti kamba na Hezekiah, yakamba mfumu ikulu ya Assyria, kuti, "Chikhulupiro cako ciloza kuti" 20 Ukamba mau acabebe cabe, kuti kuli umphingu na nkondo, mwaiye ukhulupilira kuti ukile ine. 21 Ona ukonda na kukhulupilira ndodo yotyoka iyiya bango. Koma ngati mwamuna asamilako, inkhalila mu manja yake nakubola. Ndiye vamene Farao mfumu ya Egypto ziliku okhulupilira eve. 22 Koma ngati ukamba naine kuti, 'Tikulupira muli Yehwe Mulungu wantu,' simwamene ali pamwamba pa malo na maguwa yamene yanapangiwa na Hezekiahyatengewe, ndipo akamba kwa Yuda na Yerusalemu, 'Mufunika ku pembeza guwa iyi mu Yerusalemu'? 23 Manje mvelani, nifuna kupasani zabwino kucokera ku mfumu ya Assyria. Mkulu wanga nizakupasa akavalo zikwi ziwili, ngati mwapeza amene afunika kuziyendesa. 24 Mungakane bwanji mkulu wa nkondo monzi wa mone inezi wa mfumu yanga? Mwaika chikhulupilop canu mwa Egypto na nkondo zao na akavalo a nkondo bao. 25 Sininayendepo ine ku mwamba kwa nkondo kulibe Yehwe naku iononga? Yehwe anakamba naine, 'menya malo aya yaononge." 26 Pamene apo Eliakim mwana mwamuna wa Hilkiah, na Shebnah, na Joah anakamba kuli mukulu wa nkondo , " Nipepha kamba kwa banchito mucitundu ca Aramaic, pakuti tivela. Osakamba naise muchi Yuda pa menso pa banthu amene bali ku malinga." 27 Koma mkulu wa nkondo anati, "Kodi mkulu wanga wa nchito sana kutumire kuli mkulu wa nchito wanga kuti mukambe mau aba? Kodi sana itume kuti bamuna bamene ba nkhala ku cipupa amene afunika kudya zonyansa zao nakumwa mitundo yao pamodzi naimwe?" 28 Anamulira kazembeyu nakukamba mokuwa mu ci Yuda anati, " Mvelani ku mau ya mfumu ya mfumu ikulu, mfumu ya Assyria. 29 Mfumu inati, ' Musalole Hezekiah akunameni imwe, cifukwa sazakamba ku kupulumusani imwe ku mphamvu yanga. 30 Musalole Hezekiah kuti akupangeni imwe kuti mukulupilire Yahwe, ati " Yahwe azatipulumusa ife zoona, ndipo malo aya sizapasiwa kwa mfumu ya assyria." 31 Musamvele Hezekiah , cifukwa izi ndiye zamene mfumu ya Assyria yakamba: ' Mupange mtendele na ine mucoke kuli ine. Aliyense azamwa vakumwa vake vopangiwa kucoka ku mtengo wa mpesha, na manzi yonse ku mkuyu wake na manzi yaku msinje. 32 Uzacita ivi mpka ine nibwele mutengani mupelekani ku malo yaku kwanu, malo yazomela na vinyo wa nyowani, malo ya mkate na mpesha, malo ya azitona na uci , kuti mkhale na moyo osafa.' Musamvele Hezekiah pamene afuna ku kukhani imwe, akuti 'Yahwe azakupulumusani imwe.' 33 Kodi milungu inango ya banthu yaba pulumusa mu manja ya Assyria? 34 Ilikuti milungu ya Hamath na Arpad? Ilikuti milungu ya Sepharvaim, Hena, na Ivvah? Kodi banapulumusa Samaria mumanja yanga? 35 Pali milungu yonse ya pamalo yano, kodi alipo mulungu anapulumusa chalo cake mumanja yanga? Yahwe angapulumuse bwanji Yerusalemu kucosa mu mphamvu yanga?" 36 Koma banthu banali zii sibanayankhe, pakuti mfumu inalamulira ," Osamuyankha iye." 37 Ndipo Eliakim mwana mwamuna wa Hilkiah, amene asebenza mu nyumba ya mfumu; Shebna wolemba; na Loah mwana mwamuna wa Asaph, analemba, anabwela kwa Hezekiah na zobvala zong'ambika, ndipo anamuza eve mau amene wa mukulu wa nkondi anakamba.