Mutu 16

1 Mu caka ca seventini ca Pekah mwana mwamuna wa Remaliah, Ahaz mwana mwamuna wa Yotamu mfumu ya Yuda, anayamba kulamulira. 2 Ahaz anali ndi zaka twentipamene anayamba kulamulira, analamulira zaka skisitini mu Yerusalemu. Sanacite coyenera pamenso pa Yahwe Mulungun wake, monga mwamene makolo ake Davide anacitira. 3 Koma, anayenda monga mafumu ya Israyeli; zoona, anapanga kuti mwana wake apite mu mulilo, kukonkha voyesa vocitika mucalo, zimene Yahwe anacosa pamenso ya Israyeli. 4 Anapereka nsembe zoshoka zonunkhila pamwamba, pansi pa zobilibila pamtengo. 5 Ndipo Rezin, mfumu ya Aram na Pekah mwana mwamuna wa Remaliah, mfumu ya Israyeli, anabwela ku Yerusalemu mukumenya. Bana mulepesa Ahaz, koma sibanamukngonjese iye. 6 Pa nthawi iyo, Rezin mfumu of Aram anabwezela Elath kuli Aram na kucosa amuna ba Yuda mu Elath. Ndipoi Arameans anabwela ku Elath kwamene banankhala mpaka lelo. 7 Pamene apa Ahaz anatuma opereka uthenga ku Tiglath-Pileser mfumu yaku Assyria, nakuti,"Ndine wa nchito wako na mwana wako. Bwela kuno unipulumuse mu manja ya mfumu yaku Israyeli bamene banimenyana ine." 8 Koma Ahaz anatenga siliva na golide zamene zinapezeka mu nyumba ya Yahwe na katundu yamene inali mu nyumba ya mfumu nakuzipela ngati mphaso ku mfumu yaku Assyria. 9 Mfumu yaku Assyria anamvelela eve, ndipo mfumu yaku Assyria inamenya Damascus, nakungonjesa iyo nakukunyamula banthu bake kunkhala andende ku Kir. Anapayanso Rezin mfumu yaku Aram. 10 Mfumu Ahaz anayenda ku Damscus kuti akumane na Tiglath-Pileser mfumu ya Assyria. Ku Damascus anaona guwa. Anatuma Uriya wa nsembe amene alini cionekelako cake ca guwa cifanizo cake pa nchito yake yonse yofunika. 11 Ndipo Uriya wa nsembe anamnga guwa kuti mkhale monga mfumu Ahaz anafunila anatuma ku Damascus. Anasiliza pamene mfumu Ahaz asanabwele kucoka ku Damascus. 12 Pamene mfumu inabwela kucoka ku Damascus anaona guwa; mfumu inafika pafupi na guwa nakupasa copereka pa iyo. 13 Anapanga copereka na kupereka nsembe zo imiwa za ku munda copereka, anathira pa guwa cakumwa pa iyo ngati copereka, anawaza magazi ya kusankhana copereka pa guwa. 14 Guwa ya mkuwa yamene inali pa Yahwe-anaibwelesa pasogolo pa tempele,pakati pa guwa na tempele ya Yahwe nakuika ku mphoto kwa guwa. 15 Mfumu Ahaz analamulira Uriya wa nsembe, nakukamba kuti, "Paguwa ikulu shoka kuseni zoshoka zopereka na mumazulo zopereka zakumunda, zopereka zoshoka za mfumu na zopereka zoimila anthu onse ba mu mzinda uja, na zopereka zakumunda na zakumwa zoeleka . Thila momwaza magazi ya nsembe yoshoka na magazi yonse ya nsembe. Koma guwa ya mukwa izankhla yanga yofumisilaka moyendela." 16 Uriya wa nsembe annacita zamene mfumu Ahaz analamulira. 17 Mfumu Ahaz anacosa masekele zo amphaka nacosa mimo pa anasisa thawale: pamwamba pa ng'ombe zinali pansi pake nakuika pamwamba miala. 18 Anacosa cobisa capa sabata camene banamanga pa nyumba ya Mulungu, pamozi na mfumu pongenera kunja kwa nyumba ya Yahwe, cifukwa ca mfumu ya Assyria. 19 Pa nkhani zinango zokamba pa Ahaz na zamene anacita, kodi sizinalembewe mubuku ya zocitika mu mfumu wa Yuda? 20 Ahaz anagona na makolo ake anaikiwa na makolo ake mumalo ya Davide. Hezekiah mwana mwamuna wake anabwela ankhala mfumu mu malo mwake.