Mutu 15

1 Mu caka ca twenti-seveni Jeroboam mfumu ya Israyeli, Azariah mwana wa Amaziah mfumu ya Yuda anayamba kulamulira. 2 Azariah anali na zaka sikisitini pamene anayamba kulamulira, kwa zaka fifite-tu mu Yerusalemu. Amai ake zina yabo banali Jekoliah, anali aku Jerusalem. 3 Anacita zoyera pamene Yahwe monga atate bake banacitilira. 4 Zinali pamene, malo ya pamwamba siyanatengewe. Banthu banali bakali kupeleka nsembe na kushoka zonukhila pamalo ya pamwamba. Yehwe anaidwalitsa mfumu kuti inankhala na khate mpaka siku ya kufa anakhala mu nyumba inango. 5 Yotamu, mwana wa mfumu anali mu nyumba muja ndipo analamulira mu malo muja. 6 Koma nkhani zinango zokamba pali Azariah, zonse zamene anacita, sizinali zinalembewa mu buku ya zo itika ya mfumu ya Yuda? 7 Choncho Azariah anagona na makolo ake akudala; anaikiwa na makolo bake mu malo ya Davide. Yotamu, mwana wake, anabwela ankhala mfumu mu malo muja. 8 Mu caka ca feti-eyitica Azariah mfumu ya Juda, Zakariya mwana wa Jeroboam analamulira mu Israyeli mu Samaria kwa miyezi sikisi. 9 Anacita camene cinali coipa pa menso ya Yahwe, monga atate bake banacita. Sana leke kuli ayttate bakeJeroboam mwana wa Nebat, Analengesa Israyeli kuchimwa. 10 Shallum mwana wa Jabesh banayenga Zakariya, banamumenya ku Iblem, nakumupaya, Ndipo anakhala mfumu eve mumalo yaja. 11 Kukamba pa nkhani zokamba pali Zakariy, zinalembewa mubuku ya zocitika mu ufumu wa Israyeli. 12 Aya yenze mau ya Yahwe kuti anakmba na Jehu, nati," Makolo yazankhala pa mupando wa ufumu mu mibado wa ufumu ili foo ibwela." Izi ndiye zinacitika. 13 Shallum mwana wa Jabesh anayamba kulamulira mu caka ca fetini ca Azariah mfumu ya Yuda, ndipo analamulira cabe mwezi unozi mu Samaria. 14 Menahem mwana wa Gadi anayenda ku Tirzah nakufika ku Samaria. Anamenya Shallum mwana wa Jabesh, mu Samaria. Anamupunga nakunkhala mfumu mu malo yaja. 15 Kukamba pankhani zina zokamba za Shallum na ciwembu anapanga, zinalembewa mubuku yazocitika mubuku ya mafumu ya Israyeli. Pamenepo 16 Menahem anacitira ciwembu Tipsah na onse anali pamenepo, na malire yaku Tirzah, cifukwa sibanasegule malo kuli eve. Ndipo anamenya icho, anatumbula bakazi bonse bamamimba mu munzi uja. 17 Caka ca feti-naini ca Azariah mfumu ya Yuda, Menahem mwana wa Gadi anayamba kulamulira Israyeli; analamulira kwa zaka teni mi Samaria. 18 Anacita coipa pamenso pa Yahwe. Mumoyo wake wonse, sana coke ku macimo ya Jeroboam mwana wa Nebat, amene analengesa Israyeli kucimwa. 19 Pamenepo Pul mfumu ya Assyria anabwela kumenyana a calo, na Menahem anapasa Pul wanu sauzande matalanta ya siliva, kuti Pul manja yake yankhale naye kupasa mphamvu ufumu wa Israyeli mu manje yake. 20 Menahem anasonkhesa ndalama za cuma cao kuti apase masekeli fifite asiliva kuti apase mfumu ya Assyria. Pamenepo mfumu ya Assyria anakana nabweza sanakhale mu malo muja. 21 Koma kukamba za Menahem, na vonse vamene acita, kodi sivina lembewe mubuku yazocitika mu mfumu ya Israyeli? 22 Sopano Manehem anagona na makolo yake, na Pekahiah mwana wake mwamuna anankhale mfumu. 23 Mucaka ca fifite ca Azariah mfumu ya Yuda, Pekahiah mwana mwamuna wa Menahem anayamba kulamulira Israyeli mu Samaria; Analamulira zaka tuu cabe. 24 Anacita coipa pamenso pa Yahwe. Sanasiye macimo ya atate bake Jeroboam mwana wa Nebat, mwaichi apanga Israyeli ku cimwa. 25 Pekahiah anali na ofisa zina yake Pekah mwana wa Remaliah, amene anapanga ciwembu caiye. Na amuna bali fifite baku Gileadi, Pekah anapaya Pekahiah na Agrob na Arieh mu Samaria, mu katedeo mu nyumba ya mfumu. Pekah anapaya Pekahiah nankhsls mfumu mu malo mwake. 26 Koma Kukamba pa nkhani zokamba pa za Pekahiah, zonse anacita, zinali zolembewa mubuku ya zocitika mu umfumu ya Israyeli. 27 Caka ca fifite-tuu ca Azariah mfumu ya Yuda, Pekah mwana wa Remaliah analowa mu ufumu wa Israyeli mu Samaria; analamulira zaka tuu. 28 Anacita camene coipa pamenso ya Yahwe. Sanali anacoka koma cimo ya Jeroboam mwana wa Nebat, amene anapanga kuti Israyeli kucimwa, 29 Mu masikiu ya Pekah mfumu ya Israyeli, Tiglath-Pileser mfumu ya Assyria anabwela nakutenga Ijon, Abel Beth MMaacah, Janoah, Kedessh, Hazor, Gilead, Galilee, na calo conse ca Naphtali. Anabatenga kupita nao ku Assyria. 31 Ndipo Hoshea mwana mwamuna wa Elah anapanga ciwembu kuli Pekah mwana mwamuna wa Remaliah. Anamumenya nakunupaya iye. Anabwela ankhala mfumu mu nyumba ya mfumu mu caka ca twente ca Yotamu mwana mwamuna wa Uzziah. 30 Pali nkani zina za zonena pali Pekah, zonse zamene anacita, zinalembewa mubuku yazocitika mu ufumu wa Israyeli. 32 Mu caka ca tuu ca Pekah mwana mwamuna wa Remaliah, mfumu ya Israyeli, Yotamu mwana mwamuna wa Azariah, mfumu ya Yuda anayamba kulamulira. 33 Anali na zaka twenti-faivi pamene anayamba kulamulira; analamulira cabe zaka sikisitini mu Yerusalemu. Amai ake zina anali Jerushah; anali mwana mukazi wa Zadok. 34 Yotamu anacita zabwino pamenso ya Yahwe. Anakokha cisanzo ca atate bake Azariah anacita. 35 Komatu, malo yapamwamba siyanatengewe. Banthu bali kupereka nsembe zoshoka pamwamba Yotamu anamanga cipata cakumwamba ca nyumba ya Yahwe. 36 Koma pa nkhani zina zokamba pa Yotamu, na zonse zinalembewa mubuku ya zocitika mu umfumu wa Yuda. 37 Mu masiku ayoYahwe anayamba kutuma bomenyana na Yuda Rezim mfumu ya Aram, na Pekah mwana mwamuna wa Remaliah. 38 Yotamu anagona na makolo ake anaikiwa pamonzi mu malo ya Davide, makolo ake bakudala.Pamene apo Ahaz, mwana mwamuna wake, anankhala mfumu mumalo mwake.