Mutu 14

1 Mucaka cacibili ca Jehoash mwana wa Jehoahaz, mfumu ya Israyeli, Amaziah mwana wa Joash, mfumu ya Yuda, anayamba kulamulira. 2 Anali wazaka twenti-faivi pamene anayamba kulamulira; analamulira kwa zaka twenti-naine mu Yerusalemu. Amai ake zina anali Jehoaddad, waku Yerusalemu. 3 Anacita zabwino pameso pa Yaweh, koma sanali monga atate bake Davide. Anacita zonse zomwe Joash, atate ake anacita. 4 Koma malo yapamwamba siyanatengedwe. Banthu banapitiliza kuereka sembe ana shoka pamwamba paja. 5 Zinali pamene kulamulira kwake kumunkhazikisiwa, anapaya wa nchito amene anapanga atate bake mfumu. 6 Manje sanafune kupaya mwana waya wopanga kuti Atteli; koma, malo mwake, anacita monga vinalembewa mu buku ya malamulo ya Mose, monga Yaweh analamulira kuti, " Atate asapayewe cifukwa ca banabawo, kapena bana kupaiwa cifukwa ca macimo ya makolo yawo. Malo mwake, aliyense pawine cifukwa ca macimi yake." 7 Anapaya masauzandi ten ya asilikali baku Edom ku ku cigwa ca Salt; anatenga Sela mu nkhondo naikuipasa zina kuti Joktheel, ndiye mwamene ikambiliwa nalelo. 8 Pamenepo Amaziah anatuma banthu bake kuli Jehoash mwana wa Jehoahaz mfumu ya Israyeli, anati," Bwelani tikumane menso na menso mu nkhondo." 9 Koma Joash mfumu ya Israyeli anatuma banthu bake kuli Amaziah mfumu ya Yuda, nakuti," Ine ame utumikila ku Lebanon kuti atuma uthenga kuli mkunguza waku Lebanon, nakuti,' Mpase mwana wako mukazi kuli mwana wanga mwamuna ankale mukazi wake; koma cinyama cofoya caku Lebanon iliti kuyeela moteyela naku dyaka pa colila. 10 Watimenya zoona kuno ku Edom na mtima wako wakungamula pamwamba, iwe na Yuda na iwe?" 11 Amaziah sanamvelele. Motero Jehoash mfumu ya Israyeli anamenya Amaziah mfumu ya Yuda anakumana menso na menso ku Beth Shemesh, malo ya Yuda. 12 Yuda anali anagonjesewa anayenda ku nyumba kwao. 13 Joash mfumu ya Israyeli, anagwira Amaziah, mfumu ya Yuda mwana wa Jehoash Ahaziah, ku Beth Shemesh. Anabwela ku Yerusalem kuononga vomanga vaku Yerusalem kucokela ku cipata kuli Ephramu cipata kung'ono kuja, za mikono handiredi anali kulipha kwake. 14 Anatenga golide na siliva yonse, na zinthu zonse zinali mu nyumba ya Yahwe, vinthu vonse va mtengo wapamwamba vamu nyumba ya mfumu, nabo ongwiliwa onse, ndipo banabwelera ku Samaria. 15 Kwa macitidwe ena onena pa Joash, zonse anacita, mphamvu yake, namwamene anamenyerana na Amaziah mfumu ya Yuda, sizinalembedwe mu buku ya zocitika za mfumu ya Israyeli? 16 Ndipo pamenepo Joash anagona na makolo ake chokonkhao ana ikiwa mu Samaria na mfumu ya Israyeli, na Jeroboam, mwana wake, mankhala mfumu munalo mwake. 17 Amaziah mwana wa Joash, mfumu ya Yuda, anankala zaka fifitini pambuyo yaifa ya Jehoash mwana wa Jehoahaz, mfumu ya Israyeli. 18 Monga mwa manje pankhani zokamba Amaziah, kodi sizinalembedwe mu buku ya zocitika za mfumu ya Yuda? 19 Anapangira ciwembu Amaziah mu Yerusalem, na yanda ku Lachish, koma anatuma banthu ku Lachish na kumupaya kwamene kuja. 20 Boma muleta pa kavelo, anaikiwa na makolo ake mu malo ya Davide. 21 Banthu bonse ba Yuda anatenga Azariah, amene anali zaka sikisitini, nakupanga mfumu mumalo mwa atate bake Amaziah. 22 Anali Azariah anamnga Elath ndipo ansbweza kwa Yuda, mfumu iyi inaikiwa na makolo aka. 23 Mu caka ca fifitini ca Amaziah mwana wa Joash mfumu ya Yuda, Jeroboam mwana wa Jehoash mfumu ya Israyeli anaymba kulamulira ku Samaria; analamulira kwa zaka fote-wanu. 24 Anacita chamene cinali coipa pa menso ya Yahwe. Sanacoke ku macimo ya Jeroboam mwana wa Nebat, amene analengesa Israyeli kucimwa. 25 Anabwezela ku malile ya Israyeli kucokela ku Lebo Hamath mpaka ku manzi ku Arabah, kukonkha kulamulira kwa Yahwe, Mulungu wa Israyeli, anakambapo kwa anchito a Jonah mwana wa Amittai, muneneli, amene anali kuchokera ku Gath Hepher. 26 Pakuti Yahwe anaona kubvutika kwa bana ba Israyeli, cinali cobaba kwa aliyese, bonse akapolo na bosamangiwa, nakuti kunalibe obapulumusa bana ba Israyeli. 27 Potero Yahwe anati sazaononga zina la Israyeli pansi pa kumwamba; koma, anabapulumusa na kwanja yakwa Jeroboam mwana wa Jehoash. 28 Koma pa nkhani zina zobvutika zonena pali Jeroboam, pazonse anacita, anacita nkhondo naku tenga Damascus na Hamath, yamene yanali ya Yuda, za Israyeli, kodi sizinalembewe mu buku ya zocitika za mfumu ya Israyeli? 29 Jeroboam anagona na makolo ake na mfumu za Israyeli, na Zakaria mwana wa mfumu mumalo mwake.