Mutu 13

1 Caka ca twenti-fili cha Joash mwana wa Ahaziah mfumu ya Yuda, Jehoahaz mwana wa Jehu anayamba kulamulila Israyeli Samaria; analamulira zaka seventini. 2 Anacita cinthu chamene cinali choipa pa menso ya Yehova na kukonkha machimo ya Jeroboam mwana mwamuna wa Nebat, analenga Israyeli kuchimwa; Jehoahaz sanacoke kwa beve. 3 Ukali wa Yehova unashoka Israyeli, anapitiliza kubapasa mu manje ya Hazael mfumu ya Aram na mmanja ya Ben Hadad mwana mwamuna wa Hazael. Koma 4 Jehoahaz ana pempha Yehova, na Yehova anamvela kwa eve chifukwa anaona kumuutsira kwa bana ba Israyeli, mwamene mfumu ya Aram inababvutisira beve. 5 Ndipo Yehova anabapulumusa bana ba Israyeli, bana pulumuka mu manja ya Arameans, na banthu ba Israyeli banayamba kunkhula mu manyumba yao monga kudala. 6 Komatu, sibanacokeko machimo ya nyumba ya Jeroboam, amene analengesa Israyeli ku cimwa, anapitiliza mu macimo ayo; na kupitiliza na fano mu Samaria. 7 Aramean anamusiya Jehoahaz na banthu bapa kavalo bali fifite, naboyenda pansi bali teni sauzandi, na akavalo teni ya mfumu yaku Aram anaononga anabapanga monga dothi yopodelapo. 8 Pankani zina zija Jehoahaz, anacita na mphamvu, kodi sivinalembewe mu mabuku ya zocitika mu mfumu ya Israyeli? 9 Ndipo Jehoahaz anagona na makolo ake, ndpo bana muika ku Samaria. Johoash anankhala mfumu ku malo kuja. 10 Mu caka ca theti-seveni Joash mfumu ya Yuda, ulamuliro wa Jehoahaz unayamba mu Samaria na mu Israyeli; analamulira zaka sikisitini. 11 Anacita coipa ku Yehova. Sana siye macimo ya Jeroboam mwana mwamuna wa Nebat, mwa ichi anapanga Israyeli kucimwa, koma anayenda muli eve. 12 Vocita vinango va Jehoash, na vonse vamene anacita, mwa mphamvu yake kuti anamenya Amaziah mfumu ya Yuda, kodi sivinalembe mu buku ya vocitika mfumu ya Israyeli? 13 Jehoash anagona na makolo ake akudala, na Jeroboam anakhala pa mpando wa cifumu. Jehoash anaikwa mumanda mu Samaria na mfumu yaku Israyeli. 14 15 16 Manje Elisha anabwela adwala mateda ndipo anabwela afa, amufikira Johoash mfumu ya Israyeli nakulira kuli iye. Anati," Atate banga, atate banga, gareta wa Israyeli na akavalo na banthu bake batengewa kuli iwe!" Elisha anati kulin eve, "Tenga uta na colasila," Ndipo Joash anatenga uta na volasila. Elisha anakamba kuli mfumu ya Israyeli Kuti," Ika manja yako pa muvi," Anaika kwanja yake pa ichi. Elisha anaika kwanja yake pa manja ya mfumu. 17 Elisha anati," Bvula ma windo yaku m'mawa," ndipo anayasegula. Pamenepo Elisha anakamba kuti," Mulase!", Ndipo ana mulasa. Elisha anati," Uyu ni mukondo wa Yehova wa ciaonjeco, mkundo woganyesera Aramu, kuli iwe uzamenya ba Aramean mpheke mpaka ubasilize bonse. 18 Ndipo Elisha anakamba kuti," Tenga ka mkondo," Joash anatenga. Anati kuli mfumu ya Israyeli," Menya pansi na yeve," na menya katatu pansi, naleka. 19 Koma munthu wa Mulungu anakalipa kwambili na eve anakmba," Sembe unamenya pansikali faive kapena kali sikisi. Sembe wa menya ba Aram mpaka wa basiliza, koma manje uzamenya Aram kali katatu." 20 Ndipo Elisha anafa, anamuika kwamene kuja. Ndipo gulu ya Moab inatenga malo ya kuyamba kwa caka. 21 Pamene bakali kuika munthu wina, banaona gulu ya a Moab, banataya thupi ya munthu uja mu manda ya Elisha. Pamenepo munthu uja wakufa anakumiya mabozo ya Elisha, anauka nakuimilira futi. 22 Hazael mfumu ya Aramu anabvutisa ba Israyeli masiku yonse ya Jehoahaz. 23 Koma Yehova anali anakondo ba Israyeli, anabactilira cifundo ba kwambili, cifukwa ca pangano pakati pa iye na Abrahamu, Isaki, na Yakobo. Manje Yehova sana ba ononge beve, sana chose pa menso pake. 24 Hazael mfumu ya Aram anafa,ndipo Ben Hadad mwana wake anaikiwa mfumu mumalo mwake. 25 Jehoash mwana wa Jehoahaz anatenga cosa kwa Ben Hadad mwana wa Hazeal malo yamene yanatengedwa kucosa kwa Jehoahaz na Atate ake mwa nkondo. Jehoash anamenya iye katatu, anatenga futi malo yonse ya Israteli.