Mutu 12

1 Mu chaka cha nambala 7 cha Jehu, kulamulila Joashi kunayamba analamulila zaka fote mu Yelusalemu. Amai bake zina anali Zibiah, waku Beersheba. 2 Joashi anachita voyenela pamaso pa Yehova ntawi zonse, chifukwa Yehoiada wa nsembe anamuza kuata iye. 3 Koma malo ya anasmbe sanate ngedwe. Banthu banapitiza kuyereka nsembe izo shoka nazo nunkhula pa malo ya pa mwamba. 4 Joashi anati kwa ansembe, "Ndalama zonse zamene zipereke ngati choyera chopereka mu nyumba ya Yheova, ndalama izo aliyense ayesedwe-ngati ni 5 Wansembe aalandile zopereka zonse kuchoke,a ku bantu osunga ndalama kuti apange futi zonse zo-onogeka mu nyumba ya Mulungu. 6 Koma pakati pa zaka 23 chaka cha ulamulilo wa Joash, wa sembe ali kukonza zoonongeka ma tempere. Mfumu Joash anaitana Jehoiada wa sembe na benengo asembe; nakamba kuli beve " Nichifukwa chani simunakonze mu nyumba ya Mulungu? 7 Manje musatenge ndalama iliyonse kwa osonkhesa, koma tengani zamene zatengewa kudala zokozela tempere zipaseni kuli awoamene afunika kukoza kachisi." 8 Asembe anakana kutenga ndalama zili zonse kuchokela ku banthu na kuti basakonze malo opephelela beve beka. 9 Mumalo mwakuti, Jehoiada wa sembe anatenga cifuba chake, cholasila chake na chovalira, nakuchiika pafupi na guwa kun mbali ya liiti pamene wina angena mu nyumba ya Yehova. Asembe amene anali kulonda tempere polobela nakuika pamodzi ndalama zonse zamene zina bwelesewa mu nyumba ya Yehova. 10 Pamene banaona kuti muli ndalama zambili mucosungilamo, mfumu ya sudukju na wa sembe mkulu anali kubwela nakuika ndalama zopezeka mu tempere ya Yehova. 11 Bana pasa ndalama zamene zinaonge'a mamapya ya banthu bamene banali kusunga tempere ya Yehova. Banapasa bopala matabwa (okonza mipando) na omanga manyumba, amene anali ku konza nyumba ya Yehova, 12 ndipo kwa amasoni na ojuba miyala naku konza tempere ya Yehova, na zonse zimene zizofunika kupasiwa kuti akonze. 13 Koma ndalama zobwelesewa mu nyumba ya Yehova sizinaperekewe kuti apange kapu ya siliva, hoimbilako liti, kabata, lipenga, kapena golidi kapena sliva yoonesela bwino. 14 Banapasa ndalama ii kwa bonse bamene bana guwira nhito mu nyu nyumba ya Yehova. 15 Kuonjelapo, sibanafune ndalama kuibelengelako amene inapasiwa ba nchito ba muna, chifukwa anthu aba benze bonkhulupilika. 16 Koma ndalama zopereka chifukwa ca machimo na ndalama ya chimo yopereka sizinali kubwelesewa mu nyumba ya Yehova, Chifukwa zinali za asembe. 17 Hazeal mfumu ya Aram anamenya naku paya a Gathi, nakutenga icho. Hazeal anabwela nakumenya Yerusalemu. 18 Joash mfumu ya Ayuda anatenga zinthu zonse zamene Jehoshaphat na Jehoram na Ahaziah, atate bake, mfumu ya Yuda, nakuika pa tela, na golide yonse imene inapezeka mosungilamwa nyumba ya Yehova na mfumu inatuma Hazziel mfumu ya Aran, Ndipo Haziel anachoka ku Yerusalemu. 19 Koma kwa nkani zina zamene pa Joash, zimene anacita niku, sizinalembewe mu buku ya zocitika mu mafumu ya Yuda. 20 Anchito bake anaukira pamodzi, naku menya Joash mu Beth Millo, yamene igandelela kufika ku Silla. 21 Jozabad mwana wa Shimeath, na Jehozabad mwana wa Shomer, wa nchito wake, anamumenya eve, anafa. Anamuika mumanda, Joash na makolo ake akudala mu malo ya Davide, na Amaziah, namwana waka mwamuna, anankala mfumu mu nyumba yake.