Mutu 11

1 Manje pamene Atalia, mai wa Azalia, anaona mwana wake mwamuna anafa, anauka nakupaya bonse bantu baku nyumba ya mfumu. 2 Koma Johoseba, mwana mkazi wa mfumu Jehoram na mulongosi wake Ahazia, anatenga Joash mwana wa Ahazia, naku mubisa kumuchosa pabana ba mfumu bamuna bame bana paiwa, na bonse bomusunga; anabaika mogona. 3 Anamubisa kwa Atalia kuti asapaiwe. Anankala naye kwa zaka sikisi, obisama mu nyumba ya Yehova, pamene Atalia anali kulamulila mumalo yaja. 4 6 Muchaka cha seveni, Jehoiada anatuma uthenga na kubwelesa asilikali akulu akulu bali hundiledi baku Karatise nao londa, nakubaleta kuli eve, mapephelo mwa Yehova. Anapanga cipangano nabeve, anabauza kuti balapile mu nyumba ya Yehova, ndipo anabaonesa bana ba mfumu ba muna. 5 Anabalamulila nakubauza, " Ivi ndiye vamene mufunika kuika bo kwana batatu mubweler pa sabata muzankhala mulonda nyumba ya mfumu. Ndipo na bamenango batatu mubwele pa colobela, na benango bali batatu kumbuyo kwa nyumba naku cingiliza." 7 Ma gulu ena yabili yamene siyatumikila pa sabata, mulonde nyumba ya Yehova ya mfumu. 8 Mfunukuila kuzungulilra mfumu, mwamuna aliyesense na cida cake mumanja. Aliyense amene aloba pa ukulu wanu, apaiwe. Munkale na mfumu pamene iyenda kunja, napamene iloba. 9 Mkulu wa nkondo anamvela vonse vamene anabalamulila wa sembe Jehoida. Aliyense atenga amuna bake, banja bamene sibali kutumikila pa sabata, na baja bamene bali kuleka kutumikila pa sabata; bana bwela kwa Jehoida wa sembe. 10 Koma Jehoida wa sembe analamulira mazana amikono na mikondo za Davide nazonse zinali mu nyumba ya Yehova. 11 Ndipo otumikila, mwamuna aliyense na cipangizo cake mumanja, ku manja yamanja ya mopekelela naku manzele, pafupi na guwa na mopepelela, kuzungulila mfumu. 12 Pamene apo Jehoida wa sembe analeta bana ba mfumu Joash, amunaika cisote caumfumu pali eve, ndipo anamupanga mfumu nakumuzozan eve. Bana tota mumanja nakukamba kuti," Mfumu munkale muyaya." 13 Pamene Atalia anamvela chongo ca olonda na bantu, anabwela kuli bantu mu tempele ya Yehova. 14 Anayangana, ndipo, ana ona kuti, mfumu yaimilila pa choimilila, monga mwa cikhalidwe chao cinali, asogoleri na oliza lipenga anali na mfumu. Bantu bonse bamu maiko yaja anali okodwa ndipo analiza malipenga. Ndipo Atalia anang'amba vomvala vake naku punda mokuwa,"milandu milandu!" 15 Ndipo Jehoiada wa sembe analamulira akulu akulu ba bantu bambili bankhondo, nakukamba,"mubweleseni pa mpanda. Aliyese wamene amukonka, mupayeni na lupanga." Chifukwa wa sembe akamba ," Musalole kuti apaiwile mu nyumba ya Yehova." 16 Anamuleka pamene analikufika pafupi na malo pamene akavalo alobera mu'malo amfumu, ndipo anapaiwa. 17 Ndipo Jehoiada anapanga chipangano pakati pa iye na Yehova na mfumu na banthu. Kuti bankhale banthu ba yehova, ndiponso pa banthu na mfumu. 18 Ndipo banthu mu malo banayenda ku nyumba ya Baala nakuononga. Banapaya mattani, wa sembe wa Baala pa guwa onse aiona. Ndipo Jehoiada wa sembe anasankha olonda nyumba ya Yehova. 19 Jehoiada anatenga olamulira akulu ona banthu mahandiledi, ndi onse na otumikila, nabanthu bonse bamuchalo baja, onse banaleta mfumu pansi coka ku nyumba ya Yehova anayenda ku nyumba, kuloba pa colobela ca otumikila. Joash anatenga malo yake ya umfumu. 20 Anthu onse amu malo yaja anakodwa, malo yanalibe chongo pamene Athalia anapaiwa ku nyumba ya mfumu. 21 Joash anali nazaka seveni pamene anayamba kulamulila.