Mutu 11

1 Kufika apo bonse A'Isreali anabwele kuli Davidi ku Hebroni nakukamba kuti, '' onani, ife ndife thupi yanu na fupa yanu. 2 Mumbuyomu, pamene Saul enze mfumu yatu, ndimwe muna sogolela gulu ya nhkondo ya Isreali. Yehovah Mulungu wanu anakamba kuli imwe kuti, iwe uzasogolela bantu banga A'Isreali, ndipo uzanhkakala olamulila bantu banga ba Isreali. '' 3 Bonse bakulu ba Isreali bana bwela kuli mfumu ku Hebroni, na Davidi anapangana nawo chipangano pamenso ya Yehovah. Eve anamuzoza Davidi mfumu ya Isreali. Munjila mumeneyi , mau ya Yehovah yamene analengezewa na Samuel yanabwela yachitika. 4 Davidi na bonse A'Isreali anayenda ku Yerusalemu ( ndiye kuti, Jebusi). Manje A' Jebusi , bantu bonhkala muziko iyi, banali kwameneuko. 5 Bantu bonhkala muziko iyi A'Jebusi anakamba kuli Davidi, '' Simuzabwela muno.'' Koma Davidi anatenga mzaki ya Ziyoni, iyi, mzinda wa Davidi. 6 Davidi anakamba kuti, '' Aliyense amene azamenya nhkondo na A'Jebusi azanhkala musogoleli wa mukulu.'' Ndipo Joab mwana mwamuna wa Zeruiah anayambilila kumenya nhkondo, na eve anapangiwa musogoleli wa mukulu. 7 David anayamba nhkunhkala muzika. Beve banauyita ziko ya Davidi. 8 Eve anamanga muzinda kuzungulila konse kuchokela ku Millo mpaka nakufika ku zungulila chipupa. Joab anabwelesa muzinda wonse. 9 Davidi anakulilakulila chifukwa Yehovah wamakamu anali na eve. 10 Aba ndiye asogoleli Davidi analinawo, amene anamulimbikisa eve mu ufumu wake, pamozi na bonse ba Isreali, kumupanga iye mfumu, kumvelela mawu ya Yehovah zokhuza Isreali. 11 Iyi ni mundandanda wa amuna wamphamvu a Davidi: Jashobeami, mwana mwamuna wa Hachmoniti, anali wamkhulu wama bwana. Eve anapaya amuna three hundredi na mkondo wake pa nthawi imozi. 12 Pakuchoka iye nali Eleazar mwana mwamuna wa Dodo, mu Ahohiti, wamene anali umozi paba muna ba mphamvu batatu. 13 Eve anali na Davidi ku Pas Dammim, a Philistine anasonkana pamozi kukamenya khondo, kwamene kunali munda wa barley na gulu ya nkhondo inataba kucokela kuli a Philistines. 14 Beve banayimilila pakati pa munda. Ana tetezela nakudula a Philistine na Yehovah anabampulumusa na chigonzezo chachikulu. 15 Ndipo batatu pa basogoleli sate banayenda kumwala kunali Davide, ku kavu ya Adulamu. Ngulu ya nkhondo ya Philistine anamanga msasa mu chigwa cha Refaimu. 16 Pa nthawi ija Davide anali muzaki yake, mu kavu, pamene a Philistines ana khazikisa msasa wawo ku Bethlehemu. 17 Davide anafunisisa manzi naku kamba kuti, ngati wina anganipaseko manzi yokumwa yamene yachokela ku chisime chili ku Bethlehemu, chisime chilipamupata! '' 18 Aba baso bamuna ba mphamvu batatu bana ngonjeza gulu ya nkhondo ya 19 afilisi nakutapa manzi kucoka mu chisime cha Bethlehemu, chisime chiliku mupata. Bana tenga manzi nakupelekela Davide, koma eve anakana kuyamwa. mwayichi anatayila mwa Yehovah. Kuchoka apo eve anakamba kuti, '' zitheka kuti ine sinifunika sinifunika kuchita izi! Kodi nimwe magazi a amuna aba amene anayika moyo zawo?'' Chifukwa beve anayika pachiswe moyo zawo, Davide anayakana kuyamwa. Izi zinali zo chita za amuna atatu amphamvu. 20 Abishai mubale wa Yowabu anali musogoleli wa amuna atatu. Pa nthawi ina eve anasebenzesa lupanga moshushana na fili hundredi nakubapaya. Ana kambiwa na pamozi nabili batatu. 21 Pali batatu bamene bana pasiwa ulemelelo nakunkhala mukulu wawo, ngankhale sanali umozi wa beve. 22 Benaya mwana mwamuna wa Jehoiada anali wankhondo wolimba mutima kuchokala ku Kabzeel, anachita zodabwisa . Anapaya bana bamuna babili ba Ariel waku Moab. Eve anayenda pansi pamugodi nakupaya mukango pasiku yamene mame inali kugwa. 23 Eve anapaya munthu waku Egypto, munthu mutali mikolo isanu. Uyu mu Egypto anali na mikondo monga wogwila, koma anayenda pansi kuli eve na mkondo wake.Anapoka mkondo kuchosa mu manja wamu Egypto nakumupaya eve na mkondo wake. 24 Benaya mwana mwamuna wa Jehioada anachita izi, na eve anayitanidwa pambali ya amuna ba mphamvu batatu. 25 Anali wolemekezewa kupambana ba shilikali bali sate. Koma sanali olemekezewa kupambana bamuna batatu ba mphamvu, koma Davide anamufaka mukulu waba malonda bake. 26 Bamuna ba mphamvu benze Asahel mubale wa Joab, Elhanan mwana mwamuna wa Dodo waku Bethlehemu, 27 Shammoth mu Harorite, Helez mu Pelonite, 28 Ira mwana mwamuna wa Ikkesh waku Tekoite, Abiezar mu Anathothite, 29 Sibbekai mu Hushathite, Ilai mu Ahohite, 30 Maharai mu Netophathite, Heled mwana mwamuna wa Baanah waku netophithite, 31 Itai mwana mwamuna wa Gibeah mubadwe wa Benjamin, Benaya mu Pirathonite, 32 Hurai waku magodi ya Gaash, Abiel mu Arbathite, 33 Azmaveth mu Baharumite, Eliahba mu Shaalbonite, 34 Bana bamuna ba Hashem waku Gizonite, Jonathan mwana mwamuna wa Shagee waku Hararite, 35 Ahiam mwana mwamuna wa Sakar waku Hararite, Eliphal mwana mwamuna wa Ur, 36 Hepher mu Mekerathite, Ahijah mu Pelonite, 37 Hezro mu Carmelite, Naarai mwana mwamuna wa Ezbai, 38 Joel mubale wa Nathan, Mibhar mwana mwamuna wa Hagri, 39 Zelek mu Ammonite, Naharai mu Berothite( wonyamula zida zake za Yowabu mwana wa Zeruya), 40 Ira mu Ithrite, Gareb mu Ithrite, 41 Uriah mu Hittite, Zabad mwana wa Ahlai, 42 Adina mwana mwamuna wa Shiza mu Reubenite ( mukulu wa a Reubenite) ndipo makumi atatu anali na eve, 43 Hanan mwana mwamuna wa Maachah, na Joshaphat mu Mithnite, 44 Uzzia mu Ashterathite, Shama na Jeiel bana bamuna ba Hotham mu Aroerite, 45 Jediael mwana wa Shimri, Joha ( mubale wake mu Tizite), 46 Eliel mu Mahavite, Jeribai na Joshaviah bana bamuna ba Elnaam, Ithmah mu Moabite, 47 Eliel, Obeb, na Jaasiel mu Mezobaite.