Chapta 9
1
Kunali munthu ochokela ku Benjamini, mwamuna wochuka. Zina yake anali Kishi mwana wa Abiele mwana wa Zelolo mwana wa Bekonathi mwana wa Aphiya , uja mwana wa mu Benjamayiti.
2
Anali na mwana mwamuna zina yake Sauli , m'nyamata wokongola . Kunalibe munthu pakati pawanthu waku Israeli wamene anali wakongola manngi kupambana uyu munyamata . Kuchokela mumapewa ake kuyenda kumutu anali mutali maningi kupambana munthu wina aliyonse .
3
Apo madonke ya Kishi , tate wake wa Sauli , yanali yatasowa . Apo Kishi anati kwa Sauli m'nyamata wake ,''Tengapo m'mozi mwa wanchito uyendenaye , nyamuka ndipo yenda kusakila madonke.''
4
Manje Sauli anapitila njila yamumalipili ya Ephremu nakuyenda kupitila mumalo yaku Shalisha , koma sanayapeze . Pasogolo pake anapitila mumalo ya ku Shaalimu , koma malaweve kunalibe yaja madonke. Chokonkhapo wanapitila mumalo yakuma Benjamayiti , koma nakweve kunalibe sanayapeze.
5
Pamene wanabwela kumalo yaku Zufu , Sauli anakamba kuli wanchito wake wamene analinaye kuti ,'' Tiye tibwelele , ngati sitizachita ichi wa tate wanga wazaleka kudandaula ma donke nakuyamba kutisakila.''
6
Koma wanchito anawena kuti kwa yeve , '' Nimvele , muli munthu wa Mulungu muli uyu muzinda . Nimunthu wamene amapasiwa ulemu ukulu maningi ; chilichose chamene akamba chimachitika zoona . Tiye tiyende ; kapena azatiuza tipitile njila yiti paulendo wathu .''
7
Apo Sauli anafunsa wanchito wake , ''Manje ngati tizayenda timupelekela chani munthu wa Mulungu ? Kawili buledi yenze mumathumba yathu yamasaka yasila , ndipo palibe mphaso yapasa munthu wa Mulungu . Tili na chani?''
8
Wanchito anayankha Sauli kuti , pano nili na mpimo umozi mwa vigawo folo va ma shekelo ya siliva yamene nizapasa munthu wa Mulungu , kuti atiuze njila yamene tizayendela paulendo wathu.
9
(Palamulo mu Israeli , pamene munthu anayenda kufunsa nzelu za Mulungu , anali kunena kuti bwerani tiyeni kuli wa menso mphenya .'' Pakuti aneneli amasikuwano kudala anali kuwayita kuli wamensomphenya.)
10
Apo Sauli anati kuwanchito wake, '' Wakamba bwino . Bwela , tiye tiyende .'' Basi wanayenda mumuzinda mwamene munthu wa Mulungu anali kunkhalamo.
11
Pamene anali kuyenda mokwezeka impili mumuzinda , anapeza asikana wachokela mumuzinda kubwela kutapa manzi , Sauli nawanchito wake anati kufunsa , ''Aliko woyang'ana kuno?''
12
Banayankha nakunena kuti , '' Aliko ; onani , alipasogolo panu . Fulumilani, ndawa abwela lelo mumuzinda , ndaba wanthu lelo waza peleka nsembe pa malo apamwamba.
13
Mukango lowa mumuzinda muzamupeza , akalibe kuyenda kukwela kumalo ya pamwamba kuyenda kudya. Banthu siwazadya mpaka afike , chifukwa azadalisa nsembe ; kuchoka apo waja woyitaniwa wazadya . Apa yendani , pakuti muzamupeza musanga - musanga.''
14
Choncho wanayenda mumuzinda , pamene wanali kulowa mumuzinda weve wana Samweli abwela kwamene wenze lili mowa lungama , Kuti ayende ku malo apamwamba.
15
Manje siku imozi Sauli akalibe kufika , Yehova anali ataulula kuli Samweli:
16
''Mayilo monga thawi zino ine nizatuma mwana wachichepele kuchokela kuziko ya Benjamini ndipo uzamuzoza kuti ankhale kazembe wolamulila wanthu wanga Israeli . Aza pulumusa wanthu wanga kuwachosa mumanja ya ma Philistina chifukwa nawayang'ana wanthu wanga na chifundo chifukwa kuyitana kwao kufuna thandizo kwa fika kuli ine.''
17
Pamene Samweli anaona Sauli , Yehova anamuuza , ''Alipano munthu wamene ine ninakuuzapo ! '' Niyeve wamene azalamulila wanthu wanga.''
18
Pasogolo pake Sauli anabwela pa fupi na Samweli mu geti nakukamba kuti, ''Niwuzeni koni ilikuti nyumba ya m'neneri?''
19
Samweli anayankha Sauli kuti ,'' Ndine wamenso mphenya . Kwelani pasogolo panga kumalo apamwamba , pakuti lelo iwe nzadye na ine. M'mawa nizakulola kuti uyende , ndipo nizakuwuza zonse zamene zili mu mutima wako .
20
Kukamba zamadonke yako yamene yanasowa masiku yatatu yapita , osadankhawa za weve ,pakuti yapezeka . Ndipo nipali ndani pali zakumbwa zonse za Israeli? Sipali iwe na wonse wakunyumba ya tate wako?''
21
Sauli anayankha kuti , ''Sindine waku mutundu wama Benjamiti , kuchokela kuli mutundu wung'ono maningi wamu Israeli ? kodi mukoka wanga sindine ung'ono maningi pa mikoka ya pa mutundu wama Benjamini ? Lomba nichi fukwa chanji kuti mwakamba kuli ine munjila yamusango uyu?''
22
Apo Samweli anatenga Sauli nawa nchito wake nakuwaleta muchipinda chikulu nakuwa nkhazika pamalo yapamatu ya waja wamene wanayitaniwa wonse pamozi wanali pafupi fupi wanthu thirti.
23
Samweli anati kwa khukhi ,''Letani chigawo chamene ninakupasani , chamene ninanepo kuli imwe kuti ikani pambali .'''
24
Apo khukhi analeta chibelo na zonse nyama zamene zenzepo na kuyika pamene panali Sauli . Chonkonkhapo Samweli anati , '' Ona zenze zosungiwa zaikiwa pali iwe. Idya , chifukwa yenze yasungiwila iwe mpaka nthawi yoyikika ikwane , kuchokela pa nthawi yamene yamene ninakamba kuti , ' Nawayitana wanthu .''' Apo Sauli anadya na Samweli siku ija.
25
Pamene wanaseluka kuchokela kumalo yapamwamba mumuzinda , Samweli ana kamba na Sauli pamutenge wa nyumba pamwamba.
26
Ndipo pakutulukila kwa mbandaku cha , Samweli anayitana Sauli pamwamba pa mutenge wanyumba na kunena kuti , '' Nyamuka kuti nkutume kwanu ndipo Sauli anauka , ndipowonse awili iye na Samweli anayenda kunja mumusewa.
27
Pamene anali kutulukila kunja kwa muzinda , Samweli anati kuli Sauli ,''Muwuze wanchito wako kuti asogoleko ulwendo pasogolo pa ife - '' ndipo ana fende pasogolo-'' Koma iwe uyenela kusalila kuno pakanthawi , pakuti ninga ulule uthenga wa Yehova kuli iwe.''