Chapta 10
1
Manje Samweli anatenga chikho cha mafuta , nakuthira pamutu pa Sauli , nakumu muyontha kissi. Anati, ''Kodi Yehova sanakuzoze iwe kuti unkhale musogoleli wa wolamulila chokolo chake?
2
Mkasiyana na ine lelo , uzapeza amuna abili pa fupina manda ya Recho , mumalo ya Benjamini pa Zeliza . Weve wazakamba kuti kwa iwe , ' madonke yamene wenzo sakila yapezeka . Apa manje batate bako waleka kusakila madonke koma ada nkhawa za iwe , akuti, ''Nizachita bwanji pali mwana wanga?''
3
Koma uza pitililako kuyenda kuchokela apo, ndipo uzafika kumutenga wa oaki waku Tabori . wanthu watatu oyenda kwa Mulungu pa Bethele azaku mana naiwe pamene paja , m'mozi wonyamula tumbazi tung'ono tutatu winangu wonyamuna mikate itatu. Na winangu wonyamuna thumba yachakukumwa.
4
Wazakuposha nakukuposa mikate ibili yabuledi , yamene uzalandila kuchoka mumanja mwawo.
5
Zitapita izo uzabwela ku phili ya Mulungu , pamene kagulu ka asilikali wazida wa m'tundu wama Philisti kalili. Pamene uzafika pali uyu muzinda ,uzakumana nagulu ya aneneri ilikuseluka pansi kuchokela kumalo yapamwamba ali na choyimbila choumbidwa moponyongola , tambolini , mutolilo , na uta wa tunthambo woliza ; azapezeka navo azankhala ali kunenera .
6
Muzimu wa Mulungu azakuntha maguduka pali iwe , ndipo uzanenera nawo , nakuti uzachingiwa kusanduka munthu winangu .
7
Apo pemene izi zizindikilo zizabwela pali iwe , uchite chilichonse chamene manja yako yazakwanisa kuchita , pakuti Mulungu ali naiwe.
8
Seluka mumanso mwanga kuyenda ku Giligali . Pambuyo pake ine nizabwera kuselukila kwa iwe kupereka vopeleka voshoka nakupeleka nsembe ya chopeleka chamutendele . Ukayembekezele pa masiku yali seveni mpaka nikabwele kwa iwe kukuonesa vamene ufunika kuchita .''
9
Pamene Sauli anapiliwuka kuchoka pali Samweli , Mulungu anamupasa mutima winangu . Ndipo izi zizindikilo zonse zina kwanilisika yamene ija siku.
10
Pamene wana fika pa tupolo , gulu ya ananeli inaku mana naye , ndipo muzimu wa Mulungu unamu gudukila kwakuti ananewera pamozi nawa.
11
Pamene aliyense anamuziwa kudala anamuona anewera pamozi na aneweri banthu wanakambisana kuti , ''Nichani chamene chachitika kuli mwana wa Kishi ? Kodi Sauli naye nimumozi wa aneneri manje?''
12
Munthu wamene anachokela naye kumala amozi anayankha kuti , ''Ninshi tate wawo ndani?'' Chifukwa cha ichi , ayamau yanasanduku mwambi wakuti, '' Kodi Sauli naye nimumozi wa aneneri?''
13
Pamene anasiliza kusesema anabwera kumalo apamwamba .
14
Apo malume wake Sauli anati kuli yeve wawanchito wake , '' Mwenze mwayenda kuti?'' Iye anayankha , ''Mukusakila madonke ,pamene tinaona kuti sitinaya peze , tinayenda kuli Samweli.''
15
Malume wake Sauli anati , ''Chonde niwuzenikoni chamene Samweli anakamba kuli imwe .''
16
Sauli , anayankha kuli bamalume bake ,''Anatiuza potuwa kuti madonke yanali yatapezeka .'' Koma anabisa zaukhani yo khuza zaumfumu, yamene Samweli anakambapo.
17
Samweli anayitana wanthu pamozi pamene pa Mulungu pa Mizipa.
18
Anati kuli a Israeli , ''Ichi ndiye chamene akamba Yehova , Mulungu wa Israeli : 'Ninatulusa Israeli kunja kwa Egypti , nakukupulumusa iwe kuchoka mukwanja kwa ma Egypito , namukwanja kwa maufumu onse yamene yanali kukupondeleza iwe.'
19
Koma lelo mwakana Mulungu wanu , wamene anakuleselelani imwe kuli yonse mavuto na zo sausa ; ndipo mumakamba kuti kuli eve , '' Tinkhazikileni mfumu yoti lamulila ise .' Manje zileteni mweka pamenso pa Yehova kukonkha mitunda na viwongo.''
20
Choncho Samweli analeta yonse mitundu ya Israeli pa fupi , ndipo mutundu wa Benjamini unasankhiwa .
21
Ndipo analeta mutundu wa Benjamini pa fupi kukonkha viwongo . Ndipo mukoka wa Matriti unasankhiwa ; naye Sauli mwana wa Kishi anasankhiwa . Koma pamene wana yenda kuwusakila sanapezeke.
22
Apo wanthu anali kufuna kufunsa Mulungu mafunso yambili , '' Kodi kukali munthu winangu wamene a funika kubwela ?'' Mulungu anayankha , ''Wazibisa yeka pavi katundu va machola.''
23
Apo wanathawa nakuyenda kumu fukulula Sauli kuchoka pamene anliti . Pamene anaimilila pakati pa wanthu anali mutali kuchilapo wonse kuchokela mumapewa kuyenda kumwamba .
24
Ndipo Samweli anati kuli banthu , ''Mumuona munthu wamene Yehova asankha ? Palibe winangu futi pakati pawanthu wonse ! '' Wonse wanthu wanakuwa , '' Lukhale moyo utali mfumu! ''
25
Apo Samweli anauza wanthu myambo na malamulo ya zaufumu , nakuya lemba mubuku , nakuyiyika pamenso pa Yehova pambuyo pake Samweli anatumiza banthu bonse kutali , aliyense kunyumba kwake.
26
Sauli naye anayenda kunyumba kwake ku Gibeya , ndipo anayenda naye pamozi amuna olimba , wamene Mulungu anakumya mitima yawo.
27
Koma wanthu wachabechabe wanakamba kuti , '' Nanga uyu munthu azatipulumusa mutundu bwanji ? '' Awa wanthu wana pepusa Sauli ndipo sanali kuleta mphaso iliyonse kuli Sauli . Koma sauli anankhala chabe zii.