MUTU 2

1 Panapita masiku yatatu pamene kuna nkhala ukwati ku kana wa ku Galileya.na amai bake ba Yesu analiko ku ukwati uyu. 2 Yesu ndi opunzila bake anaitanidwa ku pezekako ku ukwati. 3 Kunapezeka kuti vinyu inasila ndi amai bake Yesu ana muuza kuti, ''vinyu yasila.'' 4 Yesu anane kuti, ''muzimai, ni chani ubwela kwaine? popeza kuti ntawi yanga ikalibe kufika.'' 5 Amai bake ba Yesu ana uza banchito kuti, ''chilichonse chamene akamba kwa iwe,chita.'' 6 Panapezeka kuti,kunali manongo asanu ndi imozi yamene yanali kusebenzesa mwambo wosambilamo waba yuda , iliyonse inali na muyeso wa 80 ndi 120 litazi. 7 Yesu anabauza kuti, a ''azuzye aya manongo na manzi'' . Ndipo anazuzha maningi. 8 Ndipo anauziwa banchito, ''kutengamo manzi ena ndi kupasa mukulu ogabisa.''ndipo anachita. 9 Uyumukulu ogabisa manzi pamene analabamo mu manzi,anapeza kuti ni vinyu ichi,chinamudabwisa koma,(banchito bamene anatapa aya manzi anali kuziwa ).anaitanila mukwatibwi ndipo ananena kwa iye, 10 Uyu mukulu ogabisa anapita ku mukwatibwi nakumuuza kuti, '' Muntu aliyense apasa vinyu vabwino pachiyambi ndipo zo chipa kumasilizilo kuchila manje.'' 11 Ichi chinali chodabwisa choyamba chamene Yesu anachita mumuzinda wa kana wa mu galileya.Anavumbulusa ulemelelo wa ke ndipo punzila bake anakulupilila. 12 Kuchoka apo Yesu,amaibake,abale bake,ndi opunzhira bake anapita ku capenamu ndi kunkalako masiku yango'no. 13 Manje ntawi ya paskha yaba yuda inali pafupi,ndi Yesu atapita komweko ku yelusalema. 14 Yesu anapeza ogulisa ng'ombe, mbelele, ndi nkunda naosintisa ndalama alinkhezi. 15 Ndipo anatenga ndi mukwapu nakuchosamo onse mukachisi, kufakilako mbelele ndi ngo'mbe.Anatulusa aja amalonda ochinja ndalama na kupindimula ma tebulo yao. 16 Kulibaja ogulisa nkhunda anabauza kuti, ''chosani zonsezi, Siyani kusandusa nyumba yaba tate kunkala yamalonda.'' 17 Opunzhira bake anakumbuka kuti nicholembendwa , '' kuti chilakolako cha nyumbayanu chandidya''. 18 Pomwepo ayuda ana mufunsa kuti, '' kodi ni chiziwiso chabwanji Chamene muzatiyanganicila zamene muchitilamo zonse izi''. 19 Ndi Yesu anabauza kuti, ''Pwanyani kachisi iyi,ine nizamznga masiku atatu.'' 20 Koma,akulu ba yuda banakamba kuti kodi,ungamange bwanji kachisi iyi mumasiku atatu popezakuti tinamanga mu zaka makumi anayi ndi zisano nakamozi? 21 Koma , Yesu anali kukamba pakachisi yatupiyake. 22 Pamene anauka kuakufa,ophunzira bake anakumbukila chamene Yesu anakamba mumalemba mumakambidwe yake ndi kukulupilila malemba yamene anakamba. 23 Koma pamene anali kuma phwando ya pasakha muyelusalema ,ambiri amene anabwela ana kulupilila zinalake pamene anaona zichitidwe zake. 24 Koma,Yesu sianakulupilile ali onse chifukwa analikuziwa zinali mumutima mwao, 25 chifukwa sianalikufunikila wina kupasila umboni pa munthu chifukwa analikuziba zonse zamukatikao.