Mutu 1

1 Pachiyambi panali mau ,ndipo mau anali ndi Mulungu,ndipo mau anali Mulungu. 2 uyu anali pachiyambi ndi Mulungu. 3 Zonse zinalengedwa na iye ndipo palibe chamene chinalengedwa popanda iye. 4 5 Mwayeve mwenze umoyo na umoyo wenzeli kuunika kwabanthu onse . kuunika kunaonekela mumdima koma mudima siunakwanise kuigonjesa. 6 Penze munthu wamene anachokela kwa Mulungu amene anali Yohane 7 Anabwela kupelekela umboni nyali kuti anthu onse akakhulupilile kupitila mulieve. , 8 Yohane sanali Nyali koma anabwela kupeleka umboni kuti nyali. 9 Inali nyali yazoona isanika ku anthu onse lapansi,yamene inabwela mu ziko lapansi. 10 Eve enze muziko lapansi na vonse 11 Niyeve anavipanga koma sibanamuzibe,anabwela kubanthu bake koma sibanamulandile nafuti sibanamukhulukile 12 koma kuli onse anamulandila,anamukhulupilila anabapasa mupata kunkhala bana ba Mulungu, 13 , osati bana obadwa na mwazi kapena kubadwa muchifunilo cha munth, koma obadwa mwachifunilo cha Mulungu. 14 Mau anasanduka munthu nabwela kunkhala pakati ise ,tinaona ulemelelo wochekela kwa iye yeka ochokela kwa Atate,wozula na chisomo na choonadi. 15 Yohane anachitila umboni paliyeve ,nakupunda kuti"Uyu niwamene ninakambapo,iye obwela pasogolo,apambana ine pakuti analiko. 16 koma kuchokela kwayeve kuchokela chisomo pamwamba pa chisomo, 17 lamulo inabwela na Mose koma cisoma na choonadi vinabwela na yesu Christu. 18 kulibe wamene anaona mulungu panthawi iliyonse,.Mulungu yeve eka wamene apumulila pachifuwa cha Atate,Amene apumulila pa chifuba cha Atate ndiye avumbulusa Atate. 19 Uyu ndiye umboni wa Yohane pamene Ayuda atuma Ansembe na Alevy kuchokela ku Yerusalem kumufunsa kuti "Nanga ndiwe ndani ?Ndiwe Eliya,ndiwe Muneneri kapena ndiwe mesiya? 20 Yohane anabauza vazoona kuti ine sindine Christu, 21 Anamunsa nisnhi ndiwe ndani?Eliya?Anakamba kuti sindine,Nanga ndiwe muneneri?anati sindine 22 Banamufunsa Yohane kuti tiuze ndiwe ndani kuti tipeleke yankho kuli bamene batituma,"ukamba chani pali wemwine? 23 Anabayankha kuti ine ndine chabe mau yofuula mu chipululu kuti " konzani njira yambuye siteleti,monga momwe muneneri yesaya ananenera. 24 Baja bamene banatumiwa anatumiwa na APharisi 25 .Amufunsa kuti "Nanga nichifukwa ninji ubatiza banthu pamene wakana kuti sindiwe Eliya,Muneneri kapena Christu? 26 Yohane anabayankha kuti Ine nibatiza na manzi,koma alipo pakati kanu wamene simuziwa,wamene nansapato zake sinikwanisa kumasula, 27 Abwela pasogolo panga. 28 zonsezi zinachitika ku Berthany kuja kumbali kwa Yolodani,kwamene Yohane anali kubatiza. 29 Kuseni kwakaena Yohane anaona Yesu alikubwela kwa eve nokamba ati""Taonani Nkhosa yochokela kwa Mulungu amene achosa machimo laziko lapansi. 30 Uyu niwamene ninakambapo kuti kuli wamene azabwela wamene,iye wamene abwela pambuyo panga "nimukulu kuchila ine chifukwa analiko, 31 sininamuzibe koma chinkhala tele kuti akavumbulusidwe kwa Israeli kuti ninabwela kubatiza na manzi.. 32 Ndipo Yohane anachitila umboni kuti ninaona muzimu Oyera alikubwela pa iye monga nkhunda kuchokela kumwamba,muzimu unakhala pa eve. 33 sininamuzindikile iye koma amene ananituma kubatiza na manzi ananaiuza kuti amene Muzimu uzasikila,nakukhala paiye. ndiye wamene abatiza ndi Muzimu Oyera. 34 nayangana nakuchitila umboni kuti nimwana wa Mulungu. 35 Kuseni kokonkhapo Yohane anali naophunzila bake babili 36 ,Anaona Yesu alikuyenda nati" Taonani Nkhosa ya Mulungu" 37 Ndipo ophunzila ace anamumvela alikulankhula izi 38 ,Ndipo anamulondola iye.ndipo yesu anabafunsa kuti "mufuna chani ,anati muphunzisi kubondi nikuti? 39 Anati Tiyeni mukaone anapita naye yesu kunyumba kwake chifukwa inalinso nthawi yamumazulo. 40 Umozi waiwo amene anamvela Yohane kulankhula nalondola Yesu anali Andeleya mubale wa simon Petro, 41 Anapeza mubale wake Petro poyamba namuuza nati"Tamupeze Mesiya(kutanthauza Christu) 42 Atamubwelesa kwa Yesu anaona iye ,Anati "Ndiwe Simon mwana wa Yohane koma kuyambila lelo uzachedwa Cephas(kutanthauza Petro) 43 Siku yokonkhapo pamene Yesu anafuna kupita ku Galileya akumana ndi Philip ndipo anamuuza kuti amulondole. 44 Manje Philip anali kuchokela ku Betsaida komwe Andeleya ndi Petro anali kuchokela. 45 Pamene philipe anapeza Natan anamuuza nati Tamupeza uja wamene Mose anakambapo mumalamulo na aneneri kale paja ,mwana wa Yosefe waku Nazareti. 46 Natan anafunsa Philip kuti "Nichani Chabwino chingachoke ku Nazareti?Ndipo anati tiye uwone, 47 Pamene Yesu anamuona anati "Taonani Israeli weni weni amene mwaiye mulibe chinyengo. 48 Natan anafunsa kodi waniziba bwani?Yesu anamuuza kuti pamene mukalibe kuwonana na Philip Nenze nakuona ninshi ulinkhale panyansi pa chimtengo cha Mkuyu. 49 Ndipo Natan anamuyankha kuti Muphunzisi ndinu mwana wa Mulungu, 50 Ndimwe mfumu ya israeli. Yesu anamuuza kuti , chifukwa chakuti nakuona panyansi wa mtengo waMkuyu ndiye pamene ukhulupilila? Yesu anamuuza kuti uzaona vikulu kupambana ivi. 51 Nikamba chazooona kwaiwe uzaona kumwamba kuzaseguka nangelo ba Mulungu nakwela nakuseluka pali mwana wamunthu.