zekariya mutu 4

1 Pamenepo mthenga wakulankhula ndi ine anatembenuka, nandiutsa ngati munthu wodzutsidwa kutulo. 2 Anati kwa ine, Uona chiyani? Ine ndinati, “Ndikuona choikapo nyale chopangidwa ndi golidi, chili ndi mbale pamwamba pake. 3 Chili ndi nyale 7 pamwamba pake, ndi nyale 7 pamwamba pa nyale iliyonse. 4 1mwa ichi ninakamba futi na mungeli wamene enze kukamba na ine. ninakamba, ''ivi vintu vitantauza chani, mbuye wanga?'' 5 5mungeli wamene enzo kamba na ine ana yanka na kukamba kuli ine, ''siuziba kuti ivi vintu vitantauza chani?'' nina kamba, ''iyayi, mbuye wanga.'' 6 6 ndipo anakamba kuli ine, ''aya nimau ya YEHOVA kuli zerubabele: osati na mpamvu kapena kulimba, koma koma na muzimu wanga, akamba YEHOVA wamakamu. 7 7ndiwe chani, pili ikulu? pamenso pa zerubabele uzankala malo yalibe chintu, ndiponso azachosa mwala wa pamwamba ku punda kwa, chisomo! chisomo pali weve!''' 8 8mau ya YEHOVA bwela kuli ine, kukamba. 9 9''manja ya zerubabele yana ika maziko ya nyumba iyi ndiponso manja yake yaza isilizisa,'' mwa ichi muzaziba kuti YEHOVA wamakamu anituma kuli imwe. 10 10nindani anasula siku ya vintu ving'ono? aba bantu baza sangalala ndiponso kuona mwala wo ononga mukwanja ya zerubabele.(izi nyali zili 7 ni menso ya YEHOVA yamene ya yenda yenda pa ziko lonse lapansi. 11 11ndipo nina mufunsa mungeli, ''nanga izi mitengo zibili za olivi zili kumazhele na kukwanja ya manja ya choikapo nyali?'' 12 12 futi ninamufunsa, ''nanga izi ntambi zibili za olivi kumbali kwa mipopi zibili zagolide zamene zili na chotililako mafuta kuchoka mukati mwake?'' 13 ndipo anakamba kuli ine, ''siu ziba kuti ivi ni vichani?'' ninakamba, ''iyayi, mfumu yanga.'' 14 14ndipo anakamba, ''aba ni bana bamuna ba olivi ya fresh bamene ba imilila pamenso pa AMBUYE ba ziko yonse.''