1 Kano Yehova amanga nyumba,basebenza pachabe chabe ,baja bo manga. Koapanda Yehova kusunga muzi, malonda yalonda palibelibe . 2 Nikwachabechabe kuti uuke kuseniseni, nakubwela mochedwa ku nyumba, kapena kuti udye chakudya chogwila nchito yampamvu , pakuti Yehova apasa chakudya kuli okondedwa bake pamene ba gona. 3 Onani,bana ni cholandila kuchokela kuli Yehova, na chipaso cha mumimba ni mpotho yochokela kuli eve. 4 Monga mivi mumanja ya muntu wankondo, monga bana bauchifana baumozi 5 . Odalisiwa muntu wamene ali navo vojenjemela vambili. Eve sazachita manyazi akakumana na badani bake pachipata.