Mutu 126

1 1Pamene Yehova anabweza bogwiliwa a Ziyoni, tezenli baja bolota 2 Pamenepo mukamwa mwatu munazaza nakuseka na lulime yatu na kuimba kwachikondwelelo. Pamene anakamba kuli bamitundu, Yehova abachitira vikulu; 3 Yehova anatichitila ife vikulu; tinali okondwa bwanji nanga! 4 Bwezani bankondo bantu, Yehova, monga mumana ya ku Negebu. 5 Boshanga na mumisozi bazakolola na nakupunda kwa chikondwelelo 6 Iye wamene ayenda olila , anayamula mbewu nshanga, azabwelanso na kupunda kwachisangalalo, poleta vokolola vao mu nyumba pa ntawi yavokolola.