1 Pamene vipupa vina siliziwa ndipo nina ikaviseko mumalo mwake, na bosunga viseko na boimba ndi Alevi ana sankiwa, 2 nina ika mubale wanga Hanani kuyanganila Yelusalemu, pamzi ndi Hananiya, oyanganila zotetzela, kamba kwakuti anali okulupilika oyopa Mulungu kupambana abili. 3 Nina kamba kwabenve, "musa segule viseko va Yelusalemu kuvikila ka zuba kapya. Pamene oyanganila umalonda mu nga vale viseko naku vikoma. Sakani amalonda amene ankale mu Yelusalemu bena mumalo polindila pabo umalonda wake, ndipo bena pa sogolo pama nyumba yabo." 4 Manje mu zinda unali otambalala ndipo waukulu, koma munali bantu ba ngono mukati mwake, kunalibe nyumba iliyonse yamene ina mangiwamo futi. 5 Lekani Mulungu leke mumutima mwanga ku leta pamozi aufulu, ndi olamulila, naku sauka bantu mua banja yambo. Ninapeza bukula mibado bamene abo bana bwelela oyamba na kupeza zo satila zolembedwa mukati mwake. 6 "Aba ndiye bantu amu muzinda amene benze bana yenda mundende mu ziko la babulo kuli mfumu Nebukadineza anabatenga mundende. Anabwelela ku Yelusalema naku Yuda, aliyense kumuzinda wake. 7 Anabwela ndi Zerubabele, Jesuwa, Nehemiya, Azariya, Raamiya, Nahamani, Modekai, Bilisani, Misiperete, Bigivai, Nehumu, ndi Baana. Kupenda kwa azibambo kwa bantu bamu Isilayeli kuikalako zo khokapo. 8 Obadwa mumbuyo mwa Parosi, 2,172. 9 Bobadwa mumbuyo mwa Shafatia, 372. 10 Bobadwa mumbuyo, 652. 11 Bobadwa mumbuyo mwa Pahati-Mohabu, kupitila kuli bobadwa mumbuyo mwa Yeshuwa na Yahabu, 2,818. 12 Bobadwa mumbuyo mwa Elamu, 1,245. 13 Bobadwa mumbuyo mw Zattu, 845. 14 Bobadwa mumbuyo mwa Zakkai, 760. 15 Bobadwa mumbuyo mwa Binnui, 648. 16 Bobadwa mumbuyo mwa Bebai, 628. 17 Bobawa mumbuyo Azagadi, 2,322. 18 Bobadwa mumbuyo mwa Adonikamu, 667. 19 Bobadwa mumbuyo mwa Bigvi, 2,067. 20 Bobadwa mumbuyo mwa Adini, 655. 21 Bobadwa mumbuyo mwa Ateri, mwa Hezekiya, 98. 22 Bobadwa mumbuyo mwa Hasumu, 328. 23 Bobadwa mumbuyo mwa Bezai, 324. 24 Bobadwa mumbuyo mwa Harifa, 112. 25 Bobadwa mumbuyo mwa Gibiyoni, 95. 26 Amuna kuchokela mu Betelehemu na Netofa, 188. 27 Amuna ochokela ku Anatoti, 128. 28 Amuna aku Beti Azmaveti, 42. 29 Amuna aku Kiriati Yearimu, Kefira, na Beerroi, 743. 30 Amuna aku Rama na Geba, 621. 31 Amuna aku Mikmasi, 122. 32 Amuna aku Beteli na Ai, 123. 33 Aumna akwina Nebo, 52. 34 Bantu ba kwina kwa Elamu, 1, 245. 35 Amuna aku Harimu, 320. 36 Amuna aku Yerico, 345. 37 Amuna aku Lodi, Hadidi, na Ono, 721. 38 Amuna aku senna, 3,930. 39 Muku wa sembe: Bobadwa mumbuyo mwa Yedaiya (Munyumba ya Yesuwa), 973. 40 Bobadwa mumbuyo mwa Immeri, 1,052 41 Bobadwa mumbuyo mwa Pashurio, 1,247. 42 Bodwa mumbuyo mwa Harimu, 1,017. 43 Alevi: Bobadwa mumbuyo mwa Yesuwa, mwa Kadieli, mwa Binnui, na mwa Hodevali, 74 ***kweze kufunikila mwa Binnui ndi mwa Hodeva kumashilila kwa sopano bali bo badwa mumbyyo mwa Hodeva.*** 44 Ama imbidwe: Bobadwa mumbuyo mwa Asafu, 148. 45 Bosunga viseko bobdwa mumbuyo mwa shalumu, bobadwa mumbuyo mwa Ateri, bobadwa mumbuyo mwa Talmoni, bobadwa mwa Akkubu, bobadwa mumbyuo mwa Hatita, bobadwa mumbuyo mwa Shabai, 138. 46 Osebenza mu nyumba ya Mulungu: Bobadwa mumbuyo mwa Ziha, bobadwa mumbuyo mwa Hasufa, 47 bobadwa mumbuyo mwa Kerosi, bobadwa mumbuyo mwa Sia, bobadwa mumbuyo mwa Padoni, 48 Bobadwa mumbuyo mwa Lebana, bobadwa mumbuyo mwa Hagaba, 49 bobadwa mumbuyo mwa Shamai, Bobadwa mumbuyo mwa Hanani, bobadwa mwa Gahari. 50 Bobadwa mumbuyo mwa Reaiya, bobadwa mumbuyo mwa Rezini, bobadwa mumbuyo mwa Nekoda, 51 bobadwa mumbuyo mwa Uzza, bobadwa mumbuyo mwa Pasea, 52 Bobadwa mumbuyo mwa Meunimu, bobadwa mumbuyo mwa Nefusheimu. 53 Bobadwa mumbuyo mwa Bakbuku, bobadwa mumbuyo mwa Hakufa, 54 bobadwa mumbuyo mwa Hariuru, bobdwa mumbuyo mwa Bazluti, bobadwa mumbuyo mwa Mehida, bobadwa mumbuyo mwa Harisha, 55 Bobadwa mumbuyo mwa Barikosi, bobadwa mumbuyo mwa Sisera, bobadwa mumbuyo mwa Tema, 56 bobadwa mumbuyo mwa Nezia, bodwa mumbuyo mwa Hatifa. 57 Bobadwa mumbuyo mwa Solomoni ba nchito bake: bobdwa mumbuyo mwa Sotai, bodwa mumbuyo mwa Sofereti, bobadwa mumbuyo mwa Perida, 58 bobadwa mumbuyo mwa Jaala, bobadwa mumbuyo mwa Dakoni, bodwa mumbuyo mwa Giddeli, 59 bobadwa mumbuyo mwa Shefatia, bobadwa mumbuyo mwa Hattili, bobadwa mumbuyo mwa Pochereti Hazzebaimu, bobadwa mumbuyo mwa Amoni. 60 Bonse ba nchito mu nyumba ya Mulungu, nabo badwa mumbuyo mwa ba nchito ba Solomoni, banali 392. 61 Aba ndiye bantu banali bana yenda lu Teli mela, Kerubu, Addoni, na Immeri, koma siba na onesele kuti benve ma banja yama kolo yabo kuti benze bobadwa mumbuyo kwa Isilayeli: 62 bobadwa mumbuyo mwa Delaia, bobadwa mumbuyo mwa Tobia, na bobadwa mumbuyo mwa Nekoda, 642. 63 kumbali yaba nsembe: Bobadwa mumbuyo mwa Habaiya, Hakkozi, na Barzillai (anatenga mu kazi wake ku chokela kuli mwana mukazi kuli Barzillai kuli Giliyadi ndipo ana itaniwa kuma zina yambo. 64 Aba bana sakila zolembedwa zabo pakati pabaja ani lembedwa muma banja yabo. Koma sibana pezeke, ndipo ana chosewapo. ku nkala ba sembe ngabo desedwa. 65 Ndipo kazembe ana kamba kwa benve kuti basa vomekezedwe kudia bali ya chakudia chopeleka sembe kufikila kuta nyamuka mukulu wa sembe na urimu na Thummimu. 66 Ku sonka kwa bantu bonse kunali 42,360, 67 kumbali kunali bamuna banchito naba kazi babo ba nchito, bamene banali 7337. Banali na 245 bama imbidwe bamuna naba kazi. 68 Akavalo anali 736 muku belenga, mphambu, 245, 69 ngamira zabo, 435; ndi mphambu zabo, 6,720. 70 Bena ochokela pakati azisogoleli ama banja yama kolo yabo anapasa pa nchito. Akazembe ana pasa ku osunnga tumba yandalama wani sauzande ndala ya golide, 50 madishi, na 53 zovala zaba kuluba sembe. ***zolembedwa zakale muchi Hebeli zobeli zili sate akulu asembe zovala, koma ni chovata ku vesesa maka maka ku masulila kwa manje kuli 530 zovala ansembe. nga kale choncho, ena avomekeza kusogolela sante akuti asembe zovala na faivi handiledi ndalama zasiliva.*** 71 Bena azisogoleli kuma kolo yama banja yabo yanapasa kutumba yandalama ku nchtio tuweti sausande ma koini ya golide na 2,200 ma koini ya siliva. 72 Bantu bonse ana pasa tuweti sausande ma koini ya siliva na sikite seveni sovala akulu ba nsembe. 73 Ndipo ba kulu ba sembe, Alevi, osunga pachiseko, bama imbidwe, bantu bena, osebenzela munyumba ya Mulungu, ndipo bonse ba Isilayeli ana kala mu muzinda zabo. Pa miyezi zisanu ba ziweli bantu bamu Isilayeli ana kazi kisiwa mu mizinda yabo."