Mutu 38

1 Muma siku ya Hezekaya anadwala kufikila kuna kufa Chakuti Yesaya mwana waba Amosi, muneneli, anabwela kuli enve, anati, "Yehova akamba kuti, 'konani nyumba yanu bwino; ndaba muzafa, simuzankala na umoyo."' 2 Manje Hezekiya, nkope yake ana yangana pachi pupa nakupempela kuli Yehova. 3 Anakamba kuti, "Napapata, Yehova, nikumbukileni mwamene mwachikulupililo na pansi pamutima wanga nina yenda pamenso yanu."' Manje Kezekaya analila maningi nakupunda. 4 Ndipo mau ya Yehova yana bwela kuli Yesaya, kukamba kuti, 5 "Yenda umuze Hezekaya, musogoleli wa bantu banga, "Ivi ndiye vamene Yehova, Mulungu wa Davide makolo banu, akamba kuti; namvela pempelo yako, ndipo naona misozi yako, yangona, niza lundako zaka 15 mu umoyo wako. 6 Ndipo niza kupulumusa na muzinda wako ku zanja ya mfumu yaku Asiliya, ndipo niza chingila uyu muzinda. 7 Ichi chizankala chiwonesela kuli imwe kuchokela kuli Yehova, kuti nizachita chamene ninaku uzani. 8 Yanganani, niza fendeza chinvwili nvwili pa ma stairs ya Ahazi kubwelela kumbuyo ma sitepu yali 10."' Ndipo chinvwili nvwili chinafendela kumbuyo masitepu 10 pama stairs pamene chenze chinafika. 9 Iyi inali pemepelo yolembewa ya mfumu Hezekaya mfumu ya Yuda, pamene anali kudwala na pamene anapola: 10 "Ninakamnaba ivio nili pakati ka moyo wanga nizapitamo mumi lyango ya sheoli; natumiwa kumene kuja zaka zanga zonse. 11 Nina kamba kuti siniza muona, Yehova mu chalo chaba moyo; Siniza bapepusa bantu bonse bonkala mu ziko lapansi***bantu bonse bonkala mu ziko lapansi: bena matembenuzidwe asopano bali natantauzo iy. Ma kopi yakudala yaba Hebeli batantauza malo yamene bantu sibakalamo. (ndiye kuti mofupikisa munkalo)*** 12 Umoyo wanga uzachosewa mwaine naku pelekewa monga musasa wa bobeta; na pomba umoyo wanga monga wo tunga; mwani chosamo motungila pakati ka siku na usiku mwa usilizai umoyo wanga. 13 Nina lila maningi ***liwu la chi Hebere ingabelengewe: Nina lila kapena nina zitontaza.***. kufikila kuseni; monga nkalamu apwanya yonse mafupa yanga. Pakati ka siku na usiku mwa usiliza umoyo wanga. 14 Manga imbiya nikuwaa; nikuwa monga njiba menso yanga yalema kuyangnila kumwamba, aAmbuye, nitadizeni. 15 Niza kamba chani? Ba kamba naine, ndipo bakwanisa; niza yenda pangano pagono zaka zonse pakui nagonjesewa nama dandaulo. 16 Ambuye, mavuto yamene mwatuma niya bwino kwa ine; nibwezeleli umoyo wanga kwa ine; mwani masulila umoyo na zau moyo zanga. 17 Chinali chokondwelesa kwa ine kupitamo mu madandaulo yabo mwani pulumusa mumu godi wa imfa; pakuti mwaponyela ma chimo yanga kumbuyo kwanu. 18 Na Sheol samayamikila iwe; imfa simamikila iwe; binse bamene bongena mumu godi balibe chikulupililo na chidalilo chanu. 19 Bantu bali na umoyo, nibamene batipsa zikomo, mwamene nachitila lelo; Batate bama onsesa ku bana ku daliliwa. 20 Yehova afuna kuni pulumusa ine, ndipo tiza kondwela na nyimbo masiku yonse ya umoyo watu munyumba ya Yehova. 21 Manje Yesaya akamba kuti, "Lekani batenge mutolo wa mpesa naku zola pa chipute, ndipo aza pola." 22 Hezekaya naye ana kamba kuti, "kodi nichilangizo chiti chamene chizalangiza kuti niyendo ku nyumba ya Mulungu?"