Mutu 12

1 Chifukwa cha ici, ifenso, popeza tizinguluziwamanthu ambili ochitila umboni, tileke colemagiliyonse cimatipele kucimo, mwamsanga, tiyeni tamanga na kupilila luwilo yamene ali pa sogolo pa ise. 2 Tiyene tiyanganile kwa Yesu, anayamba wokonza bwino chikulupililo. Pakuti cimwemwe cinaikika pa iye, ana pilika pa mtanda, anacitisiwa manyazi anakhala pa zanja la mpando wa cifumu wa Mulungu. 3 Tsopano ganizani pa eve, amene apilila kususana kocokela kwa ocimwa kwaeve yeka, kuti musabvutike naku teya mtima. 4 Ukalibe kukanapo kapena kulimbanapo na ucimo kufika pamyeso wocosa mwazi; 5 Ndipo waiwala cilimbikitso camene ndi nakupa ngati bana banga: " Mwana wanga usaganizile capafupi ku langiwa na Ambuye kapena akubvutisa pamene ulangiziwa na eve. 6 Chifukwa Ambuye ama langa muntu wamene bakonda, komanso bamalanga mwana aliyense wamene bamalandila. 7 Pakuti Ambuye alonga aliyense amene amukonda, amlanga aliyense amene amulandila kwa eve. Pilila masauso ngati ana ake. Pakuti ni mwana bwanji amene atate ake sammulonga? 8 Koma ngati ulibe cilangizo cimene anthu onse agawana, ponepo ndipo ana amuchigololo osati ana ake amuna. 9 Mopitilila, tilinao atate anthu akuthupi amatilonga ndipo timabapasa ulemu. Koposa kotani kugonjela kwa atate anthu aku uzimu ndi wa moyo? 10 Azi tate anthu ati longa kwa nthawi in'gono cabe pakuti anaganizila ni kwa bwino. Koma Mulungu atilanga ise kwa ubwino wathu, kuti tigabane mu ciyelo cake. 11 Kulibe cilango camene cipasa cimwemwe, koma kupasa kubaba. Koma posilizila cipereka cipatso ca mtendere ca ciyelo kwa eve amene aphunzisiwa naicho. 12 Mwa ici limbikisani manja yanu oyondolokawa nkhongono zana zofoka. 13 Pangani njila zanu za mendo yanu, kuti colemala sicigafalilala koma ku cilisiwa. 14 Fumisisani mtendele na chiyene na ciyelo pakuti popanda izi kulibe azaona Ambuye. 15 Onesesani kuti kulibe amene uso weka cisomo ca Mulungu, kuti palibe njila ya ukali izakula mpaka ku mabvuto, kuti ambili saza onongeka nacho ichi. 16 Nkhale mozi wa cigololo, kapena wa manyozo, ngati Esau, amene mwa chakudya anagulisa ukulu wake wobadwa nao. 17 Ziwa kuti papita izi pamene ana funa kutenga kupyana madaliso ake, anakaniwa cifukwa kunalibe mwai wolapa, nga khale kuti analila nachosa misozi. 18 Pakuti simunabwele ku lupili yamene inga gwililiwe, lupili ya yoyaka mulilo, mdima, yabili na cimphepo. 19 Simunabwele ku lupenga yolila, kapena ku liwu yamene ikamba mau yamene omvela apempa kuti osati mau ena anenewa kwa eve. 20 Pakuti sunakwanise kusunga camene anakulamulila: " Ngakhale nyama ekagwila lupili ifunika ku ponyewa maila." 21 Malo yoyofia yamene Mose akamba, anacita mantha naku njejemela." 22 Koma mwabwela ku lupili ya Zion na muzinda wa Mulungu wa moyo, Jerusalemu wa ku mwamba, na zikwi khumi ya angelo mu ku kondwela. 23 Mwa bwela mu musonkano wa ana obadwa oyamba, amene a lembewa ku mwamba. mwabwela kwa Mulungu, oweluza wa zonse, ku mzimu wa cilungamo, eve apangiwa bwino. 24 Mwa bwela kwa Yesu, amene ankhala pakati pa cipangano casopano, naku waza kwa mwazi wa bwino wosiyana na wa Abeli. 25 Yanganani kuti simukana amene akamba. Pakuti sanatawe pamene anakana amene ana wa cenjeza pa ziko lapansi, mwa pang'ono muzathawa ngati mwaleka kukamba amene acenjeza za ku mwamba. 26 Pa nthawi ina , liwu yake inagwendeza ziko. Koma tsopano alonjezawa kuti, "Kamozi kanthu imozi ndizagwendeza ziko osati ziko yeka, koma mumwamba." 27 Mau awa, " kwa kamazi kutanthauza kucosa zinthu izo zamene zigwendezeka. Ndiye ici , pa zinthu zamene sizingagwendezeke ziza nkhala. 28 Tsopano, landilani ufumu wamene sunga gwendezeke, tiyeni tiyamike mu njila iyi yopempeza Mulungu na ulemu na mantha. 29 Pakuti Mulungu wathu ndi mulilo wothentha.