Mutu 11
1
Ndipo ndziko lonse lapansi ina sebanzesa chilankulindwe chimozi ndipo banali namau yamozi.
2
Pamane benzeli kuyenda yenda ku mawa, bana peza malo ku shina ndipo banankala kwamene.
3
Banakambisana, "Bwelani, tapange naku shoka bwino mchelwa." Banali na nchelwa mu malo mwa myala na manenekela ngati ndaka.
4
Bana kamba, Bwelani tiyeni tizipangile teka muzinda na nsanja yamene izafika kumwamba, ndipo tizipangile zina ife teka. Naati sitizachita, tizapasulidwa mudziko lonse lapansi.
5
ndipo Yehova anaseluka pansi kuti aone muzinda na nsanja vamene bana ba adamu banamanga.
6
Yehova anakamba, ''onani, nibanthu bamodzi nachikambidwe chimodzi ndipo bayamba kuchita ivi! manji manji kulibe chizankala chovuta kuchita pali vamene baganiza kuchota.
7
Bwelani tiyende pansi nakusokoneza chilankulidwe chao, kuti basanvelane,"
8
Ndipo Yehova anaba mwandza- mwandwa kuchoka kuja mu ziko lonse yapansi ndipo banaleka mumanga muzinda.
9
Cifukwa chaichi, ziko yaka inali Babelo ku chofukwa kuja Yehova anasokoneza chilankulidwe cha ziko yonse lapansi ndipo kuchokela kuja Yehova anaba mwazamwaza pa ziko lonse.
10
Aba banali bana ba Shemu. Shemu anali nazaka handredi, ndipo anankala tate wa Arphaxad zaka zibili pamene ciina pita chigumula.
11
Shemu anankala zaka 500 Pamene anankala tate wa Arphaxad. Anankala futi tate wabana bamuna nabana bakazi benangu.
12
Pamene Arphaxadi anali zaka 35 anankala tate wa Shela.
13
Arphaxadi ananakala zaka 403 pamene anankala tate wa shela. Anankala futi tate wa bana bamuna na bakazi benangu.
14
Pamene shela anali na zaka 30 anankala tate wa Eberi.
15
Shela anankala zaka 403 pamene anankala tate wa Eberi. Anankala futi tate wabana bena bamuna na bakazi.
16
Pamene Eberi anali na zaka 34, anankala tate wa Pelegi.
17
Eberi anali na zaka 430 pamene anankala tate wa Pelegi. Anankala futi tate wabana bamuna na bakazi benangu.
18
Pamene Pelegi anali na zaka 30 anankala tate wa Reu.
19
Pelegi anankala zaka 209 pamene anankala tate wa Reu. Anankla futi tate wabana bamuna na bakazi.
20
Pamene Reu anali na zaka 32 anankala tate wa Serugi.
21
Reu anankala zaka 207 pamene anankla tate wa Serugi. Anankala futi tate wabana bamuna na bakazi benangu.
22
Pamene Serugi anali na zaka 30 anannkala tate wa Naholi.
23
Serugi anakala zaka 100 pamene anankala tate wa Nahori. Anankala futi tate wabana bamuna na bakazi benangu.
24
Pamene Nahori anali na zaka 39 anankala tate wa Tera.
25
Nahori anankala zaka 119 pamene anankala tate wa Tera. Anankala futi Tate wa ban bamuna n a bakazi benangu.
26
Pamene Tera anali na zaka 70, anankala tate wa Abrahamu, Nahori na Harani.
27
Ndipo aba banli bana ba Tela. Tela anankala tate wa Abrahamu, Nahori, na Harani ndipo Horani anankala tate wa Loti.
28
Harani anafela pa pamenso ya Tela tate wake muziko yamene anabadwilamo ku Uri mu Kalidea.
29
Abrahamu na Nahoro bana tenga bakazi. Zina yamukazi wa Nahoro inali Milika, mwana wa Harani, wamene enzeli tate wa Milika na Isaki.
30
Ndipo Sarai anali mkazi wamene senzekubala; anali mwana.
31
Tela ana tenga Abramu mwamuna wa mwana wake mwamuna Harani, na Sarai mupongozi wake, mukazi wamwana wake mwamuna abranu, ndipo pamozi bana choka mu Uri waku Kalidea, kuyenda ku Harani ya Kenani. Koma bana bwela ku Harani ndipo banankala kwamene.
32
Tela anankala zaka 205 ndipo anafela mu Harani.