Mutu 24

1 Mu masiku ya Jehoakim, Nebuchadnezzar mfumu ya babiloni anakukira Yuda; Jehoakim anankala kapolo wake kwa zaka zitatu. Jehoakim anabwelela nakupandukila Nebuchadneza. 2 Yehova anatumiza kwa Johoakim gulu ya akalonga, Asiriya, mowabayiyt na Amonayiti, anatumiza kuli Yuda kuti bawononge. uku kunali kusatira namawu yamene ya Yehova anakamba muli bakapolo bake baneneli. 3 Inali mu mwezi wa Yehova pamene ivi vina bwela kuli Yuda, kuti avichose pamenso oake, chifukwa chama chimo ya masene, nazonse ve anachita, mankope yamu Hebeli yakale yakamba kut, inali chifukwa chakukalipa kwa Yehova, 4 ndipo nafuti chifukwa chagazi losalakwa lamene anatila, chifukwa anazuzya Jerusalema nagazi losalakwa. Yehova sanali kufunisa kulekelela ivi. 5 Kuvintu vina vokumaniza Johoiakim, na vonse ve anachita, sikuti nivolembewa muma buku yamachitidwe ya mfumu za Yuda? 6 Jehoiakim anagona namakolo bake, ndipo Jehoiamkim mwana wake anakala mfumu pamalo yake. 7 Mfumu ya Iguputo sana kukire nafuti kuchokela mumalo yake, chifukwa mfumu ya babiloni ina gonjesa malo yonse yanali kulamulidwa na mfumu yaku Iguputo, kuchokela ku sinje ya Iguputo kufikila kumumana wa Yufuretisi. 8 Jehoiakim anali na zaka eyitini pamene anayamba kulamulila, analamulila mu Jerusalema kwa mwezi itatu. Zina ya bamai bake inali Nehushta; banali mwana wa Elnathan waku Jerusalema. 9 Anachita zochimwa pamenso ya Yehova; anachita vamene ba bale bakee banachita. 10 Pa ntawi ija gulu ya nkondo ya Nebuchadneza mfumu ya Babiloni inakukira Jerusalema nakuzunguluka muzinda. 11 Nebuchadneza mfumu ya Babiloni anabwela mu muzinda pamene basilikali bake bakali kuzunguluka, 12 ndipo Jehoiakin mfumu wa Yuda anayenda kuli mfumu ya Babiloni, enve, bamai bake, bakapolo bake, baka kalonga bake, bamalonda bake. Mfumu ya Babiloni anamugwila mu mwaka wake wa eyiti wa lamulila. 13 Nebuchadneza anachosa vintu vonse vofunika mu nyumba ya Yehova, na vonse vamu nyumba yachifumu. Anajuba muzidunsa dunswa vintu vonse va golide vamene Solomoni mfumu ya Isilayeli anapanga mu tempele ya Yehova, mwamene Yehova anakamba kuti vizachitika. 14 Anamanga bonse bamu Jerusalema, basogoleli, na bonse ba muna nkondo, ogwilidwa bali teni sauzandi, naba baza bonse naba chisulo. kulibe banasala kupatulila bo saika maningi mu ziko. 15 Nebuchadneza anamanga Jeroiakim mu Babiloni, kumozi naba mai ba mfumu, bakazi, bake, bamalonda, na bamuna bakulu ma malo. Anabanga kuchokela ku Jerusalema kufika ku Babiloni. 16 Bonse bamuna bakondo, seveni sauzandi pamozi, na wani saun=zandi bobaza na bamuna basula, na bonse bayenela nkondo-mfumu wa Babiloni analeta bamua aba nakubangisa mu Babiloni. 17 Mfumu wa Babiloni anapanga Mattaniah, abale ba batate ba Jehoiakim, mfumu pa malo yake. nakumuchinja zina kunkala Zedekaya. 18 Zedekaya anali nazaka twenti wani pamene anayamba kulamulila; analamulila kwa zaka ileveni mu Jerusalema . zina ya mai bake banali Hamutal; anali mwana wa Jeremaih waku libnah. 19 Anachita zochimwa pamenso ya Yehova; Anachita vonse vamene Jehoakim anachita. Kupitila mukukalipa kwa 20 Yehova, ya machitidwe anachitika mu Jerusalema na Yuda, kufikila pamene anabachosa pamaso pake. Ndipo Zedekaya anapandukila mfumu ya Babiloni.