Chapta 15
1
Samueli anati kuli Sauli , ''Yehova anatuma ine kukuzoza ufumu pa banthu bake Israeli . Manje mvela mau ya Yehova .
2
Ichi ndiye chamene Yehova wamakhamu anena , ' Nasunga mumutima mwanga chamene Ameleki anachita kuli Israeli pakuwa lesa njra nthawi yamene wanachokela ku Egypti .
3
Manje yenda nakunuyamba nkhondo Ameleki nakuwanongelatu pasasiyako kanthu zinthu zonse zamene walinazo . Osawasiyako , koma payani wabili bonse wamuna nabakazi , mwana naka cheche , ng'ombe na nkhosa , ngamila na mundoke.''
4
Sauli anasonkhanisa banthu nakuwawawelengela pamuzinda wa Telayimu - twu handeledi sauzande wanthu woyenda pansi na Teni sauzande amuna aku ludeya.
5
Apa Sauli anabwela kumuzinda wa Amaleki nakuyembekeza mu vale.
6
Nipo Sauli anati kuli mo kenayiti. '' Yendani chokani , fumani moni pakati pa wa Ameliki pakuti ine nisaku onongeleni pamozi nawo. Pakuti munaonesa chifundo kuli bathu bonse waku Isreali , pamene wanachokela ku Egypti .'' Mwa ichi makananayiti wana fendela kutali kuchoka pama Amaleki.
7
Ndipo Sauli anawayamba nkhondo ma Ameleki kuchokela ku Havila mpaka ku Shuwa , yamene ili chakumumawa kwa Egypti.
8
Ndipo anatenga Agagi mfumu ya Ameleki ali wamoyo ; anawonongelatu ko sasiyako banthu wonse na nsonga ya panga.
9
Koma Sauli na banthu wanalekelela Agagi pamozi naviweto vabwino maningi vonse, monga ng'ombe , nkhosa, kuyikapo na toyina tuwana twa ng'ombe na nkhosa. Vonse vamene vinali vabwino sibanaviononge . koma banaononga chili chonse chamene sichinali bwino na kuti chinalibe nchito.
10
Ndipo mau yamulungu yanabwela kuli Samueli , kuti,
11
''Chinikalipo kuti ninankhazikisa Sauli kunkhala mfumu , pakuti akoneka misongo kuchoka kukonkha ine , ndipo sanachite malamulo yanga .'' Samueli anakwiya ; analila usiku wonse mokuwa kwa Yehova .
12
Samueli anauka kuseni seni kuti akumane na Sauli m'mawa . Samueli anauziwa , ''Sauli anabwela anabwela anabwela ku Carmeli na ku nkhazika chowumba cha yeve mwine wake , nakukoneka nakupitiliza ulendo kuselukila ku Giligali .''
13
Apo Samueli anbwela kwa Sauli , ndipo Sauli anati kwa yeve , '' Odalisika ndiwe wa Yehova ! Nakwanilisa chilamulo cha Yehova .''
14
Smueli anafunsa , ''Nanga nichani kuuluma kwa nkhosa mumutu mwanga , makulila kobangula kwa ng'ombe kwamene nimvela?''
15
Sauli anayankha , '' Wavichosa kuli ma Ameleki . pakuti banthu wanasiyapo vabwino maningi pa pankhosa na ng'ombe , kuti avipeleke nsembe kwa Yehova Mulungu wako . Vosala taonongelatu .''
16
Apo Samueli anati kwa Sauli , '' Yembekeza ndipo ine nizakuwuza zamene akamba kwa ine usiku walelo '' Sauli anati kuli yeve , ''kamba!''
17
Samueli anati , '' Loko ndiwe mung'ono ukaziona , siunapangiwe mutu wa mitundu ya Israeli ? Ndipo Yehova anakuzoza mfumu pali Israeli yonse,
18
ndipo Yehova anakutumani kwanu kunena kuti , ' Yenda nakuonongelatu osasiyako wochimwa , ma Amaleki , ndipo umenyane nao mpaka wawonongekelatu .'
19
Nichi fukwa chabwanji chamene chalengesa kusamvela liwu ya Mulungu , koma m'malo mwake imwe mwatenga mopanda lamulo na kuchita choyipa mumenso mwa Yehova ?''
20
Apo Sauli anati kwa Samueli , ''Ine ninamvela zoona mau ya Yehova , ndipo ninayenda munjila yamene yawe ananituma . Ninamuleta mogwilila mwachikamizo Agiga , mfumu ya Amaleki, ndipo ninawaononga mosasiyako ma Amaleki wonse.
21
Koma bathu wanatengako vinangu mwa voshukiliwa pankhondo - nkhosa na ng'ombe , vabwino maningi pavinthu vonse vamene venzo funikila kuwonongeka , kuti tipeleke nsembe kwa Yehova Mulungu wako ku Giligali.''
22
Samueli anayankha , '' Kodi Mulungu amakondwela nazo maningi zopeleka zoshoka na nsembe , kulinganizana na kumvela mawu ake? Kumvela nikwa bwino maningi kuchila nsembe , ndipo kumvesesa nikwabwino maningi kupambana ma futa ambelele zimuna.
23
Pakuti kuukila kulingana nachimo yachita matsenga , ndipo kusaweluzika kuli monga uchimo wa uchipondo . Chifukwa wakana mau ya Yehova , nayeve akukana iwe kunkhala mfumu.''
24
Apo Sauli anati kwa Samueli , ''Nachimwa ; pakuti napwanya lamulo ya Yehova na mau yanu , chifukwa ninayopa banthu nakumvelela mau yawo.
25
Manje , napapata khulukani chimo yanga , ndipo mubwelele na ine pakuti ningapembeze Yehova .''
26
Samueli anati kuli Sauli , '' Sinizabwelela na iwe ; ndaba wakana mau ya Yehova , ndipo Yehova akukana kuti siuzankhala mfumu ya Israeli .''
27
Pamene Samueli anapiliuka kuti azi yenda , Sauli ana fwemba mupelela mukhanjo wake ndipo nkhanjo wa Samueli unang'ambika .
28
Samueli anati eve, '' Mulungu anyonsolako ufumu wa Israeli kuchoka kuli iwe lelo nakuupeleka kuli munthu wamene unkhala naye pafupi , yeve maningi kuchila iwe.
29
Chinangu , mphamvu ya Israeli sazanama kapena kuchinja nzelu zake ; ndaba yeve simunthu , pakuti angachinje uzelu zake .''
30
Apo anati , ''Nachimwa . Koma chonde nipaseni ulemu pamenso pa azisogoleli wa wanthu wanga na pamenso pa Israeli . Bwelelani futi na ine , kuti nikapemphele Yehova mulungu wanu.''
31
Apo Samueli anabwelela kukonkha futi Sauli , ndipo Sauli anapembeza Yehova .
32
Ndipo Samueli anati Muleteni Agagi mfumu ya Amaleki pano pali ine .'' Agagi anabwela kwa iye aliomangiwa ma chain nakunena kuti, '' Zoona kukwinyilila kwa imfa kwa pita.''
33
Samueli anayankha kuti, '' Monga mwamene lupanga yako ya pangisa azimayi kwakhala alibe bana ndiye mwamene awayi wako wazankhalilila bamayi wako walibe mwana pakuti pa bazimayi .'' Apo Samueli anajuwa Agagi mumagawo mumenso mwa Yehova ku Giligali.
34
Samueli anayenda ku Ramah , ndipo Sauli anayenda kukwela kunyumba kwake ku Gibeya ya ya Sauli.
35
Samueli sanamu onepo Sauli mpaka siku yakufa kwake chifukwa analila malilo ya Sauli . Mulungu anakwinyilila kuti yeve enze anakhazikisa Sauli kunkhala mfumu ya Israeli.