Genesis 18

1 Yehova anaonekela kwa Abraham pa mtengo wa Mamre, pamene anankhala pa ciseko pa kazuba ka siku. 2 Anayanga kumwamba ndipo, onani anaona bamuna batatu baimilila pasogolo pake. Pamene anabaona, anathamanga kukumana noa kucoka pongenela pa nyumba na kugwanda kuika mu wake pansi. 3 Anati, "Ambuye banga, ngati napeza mwai mumenso mwanu, napapata musapitilire wanchito wanu." 4 Lekani manzi yang'ono yabwekesewe, sambani kumendo, pumulani pansi pa mtengo. 5 Lekani nibwelese cakudya cing'ono, kuti muzipumulise imwe mweka. Kucoka apo mungayende, pakuti mwabwelela kwa wanchito wanu. " Bananyankha." Cita monga mwamene wakambila. 6 7 8 Ndipo Abrahamu Anayenda kuli Sara