1 Yuda Kapolo wa YesuKristo, ndi m'bale wake Yakobo kwa anyiyao atanitwa okondendwa ndi ambuye mulungu atate yao asungidwa kwa ndande ya Yesu Kristo. 2 Lisungu ndi mndele ndi chikondi vikuchogoleleni kwanu. 3 Okondendwa, nyengo iyo nimachita chokozeka kulembelani anyaimwe kukhuza chipulumusi chatu taonche, nidafunika kulembelani kwa chifuko cha kukushaulini muyambanile pa ntendele iyo idaninkidwa mala kamoji pendi yao aamini. 4 Kwa chifuko wanthu wakuti ajilovya kwa chisisipakati panu - wantu anyiyao adaikidwa chidindo cha chilango - wanthu anyiyao sadaele anyiyao ang'anamula neema ya Mulungu watu kukala unkungu, kwa kumkana Mulungu watu ndi Yesu Kristo. 5 Chipano nikonda kujimichani anyaimwe ingakale kuti kuli nyengo mmajiwa bwino kuti Ambuye adawalamicha wanthu kuchokela mjikola Misri, nampo pambuyo pake wadawamanga anyiwaja osakulupalila. 6 Ndi angelo anyiyao sadapenyelele nyengo yao achinawene nampo adasiya maloyao yokala Mulungu adawaika mvingwe va muyaya, mkati mwa mdima, kwa chilango cha siku ya ikulu. 7 Ngati muja Sodoma ndi Gomola ndi miji idazungulila, ndi idajilovyamo ene mkati mwa chiwelewele ndi adachata kumbilo lopande chiyambo adalangizidwa ngati mano ya anyiwaja ovutika mkati mwa chilango cha moto osata. 8 Ingakale kwa njila imweija olosa adachecha matupi yao, ndi adaka malamulo, ndi kunena unami pakati pa oela. 9 Nampho ata Mikaeli angelo wa mkulu nyengo iyo wamanyambana ndi satana ndi kufunchana kwa chifuko cha tupi la Musa. Siwadaese kupeleka chilango cha unami pakati pake, nampho pambuyo pake, wadakamba ambuye akupalipile. 10 Nampho wanthu anyiyawa apeleka unami pakati pa chinthu icho sachinjiwa. Ndi chija sachinjiwa - ndi chija ambacho zinyama zopande njelu ajiwikana kwa vichito ndi ya meneyo nde ya yo yawananga. 11 Ole wao! Kwa chiuko aenda mnjila ya Kaini ndi kuchata kulakwa kwa Balaamu, adapwetekedwa mkati mwa kulakwa kwa Kora. 12 Anyiyawa ni myala pa chisangalalo chanu cha chikondi, asangalala popande nchoni, ndi kuja achinawepe. Ndi mitambo yopandemaji, yatengedwa ndi mphepo, ndi mitengo yopande machamba ndi vipacho iyoyamwalila kawili, iyo yazulidwa mizo. 13 Ndi maunde ya nyanja yayoyapeleka mapokoso ya manyazi ya achinawene, ndi nthondwa izozizungulila zungulila zilindi mdima wakuda wasungidwa kwa chiuko chao muyaya. 14 Enoki wa saba wadalosa pakati pao anyaio, wadakamba, penya! Ambuye akuja ndi maelu ndi maelu ya wanthu wake oela, 15 ili wachite chilango pakati pa kila munthu, nikutilani mmanja mwaonche osamkulupilila Mulungu pakati pa njila zosati zoela, ndi kwa mau yao yonche yokalipa osati oela wayakamba paka pake. 16 Anyiyawa nde anyiwaja odadaulao, achata kumbilo la kulakwa kwao kwa volakwa kwa madama kupunda, anyiyao kwa mphoto zao wanamiza wina. 17 Lakini anaimwe, okondendwa kumbuki lani mau yayoyadakambidwa kale ndi atumiki wa ambuye Yesu Kristo. 18 Adakamba kwa anyaimwe, "kupitila nyengo yo tela sikukale wanthu anyiyao amuesela anyiao alichata kumbilo lao lopande loela". 19 Wanthu anyiyawa ndi opatulichana, atawalidwa ndi kumbilo la chiyambo. 20 Lakini anyaimwe, okondendwa, mjimange mkati mwa chikulupi chanu choela kupunda, ndi umo mpemphela Mzimu Oela. 21 Jisungeni pakati pa chikondi cha ambuye, ndimulindilile ulemelelo wa ambuye watu Yesu Kristo uyo wa apacha umoyo wa muyaya. 22 Langizani mtendele kwa anyiwa ali ndi mantha. 23 Alamicheni wina kwa kuwanyamula kuchoka pakati pa moto. Kwa wina langizani lisungu ndi kuopa, mkatengelelana ndi chovala ichochatilidwa chidindo ndi tupi. 24 Chipano uyawakuza kukupenyelelani msajikuwala, nikuchitani muime pachogole pa mtendele wake, papanda chidindo ndi kukala ndi chisangalalo, 25 kwa Mulungu yoka mpulumusi kupitila kwa Yesu Kristo atate watu, ulemelelo ukale ndi iye, ukulu ndi mphavu nyengo zonche, ndi chipano mbakana muyaya. Amina.