zekariya mutu 13

1 pasiku ija manzi aza seguliwa pali nyumba ya davide na bonkala mu yelusalema, pa machimo yao na kusayela kwao. 2 2 pasiku ija-uku nikukamba kwa YEHOVA wa makamu-niza juba ma zina ya vipembezokuchoka paziko ndiponso siyazaka kumbukiwa futi. niza chosapo baneneli na mizimu ya kusayela pa ziko. 3 ngatu ali onse muntu apitiliza kunenela, atate na amai bana mubala baza mu uza,'si uzankala, pakuti ukamba boza muzinA ya YEHOVA!' ndipo atate na amai bana mubala baza mulasa aka nenela. 4 4 pasiku ija muneneli aliyense azamvela nsoni na manso mpenya yake akafuna kunenela. aba baneneli sibaza vala futi nkoloko ya usako, kuchitila kuti baname bantu. 5 5ndaba aliyense azakamba,'sindine muneneli! ndine muntu amene asebenza pa doti, pakuti ntaka ndiye inankala chinto yanga pamene nenze munyamata 6 6koma wina azakamba kuli eve, 'nivachani vilonda vili pakati pa manja yako?' ndipo azayanka, 'ninachitiwa nabamene bali munyumba yaba nzanga.''' 7 '' lupanga! kalipila mubusa wanga, bamuna bamene ba imilila pafupi na ine- uku nikukamba kwa YEHOVA wa makamu. menya mubusa, na nkosa ziza mwazyikana! popeza niza nyamula kwanja yanga pali ba pansi pansi. 8 8Pamenepo padzakhala kuti m’dziko lonselo, atero Yehova, magawo awiri mwa magawo atatu a dzikolo adzadulidwa. Anthu amenewo adzawonongeka; limodzi mwa magawo atatu okha ndi amene adzatsale. 9 9Ndidzalowetsa gawo lachitatu pamoto, ndipo ndidzaliyenga monga kuyengedwa kwasiliva; Ndidzawayesa monga golide ayesedwa. Iwo adzaitana pa dzina langa, ndipo ndidzawayankha, ndi kunena, Awa ndi anthu anga; ndipo adzati, Yehova ndiye Mulungu wanga;