Mutu 123

1 Nyimbo yokwezeka. Nikweza menso yanga kuli imwe, imwe onkazikisiwa mumwamba. 2 Onani, monga menso ya wanchito yayanga kumanja yabwana wake, apenyerera dzanja la mbuye wao, monga maso a mdzakazi ayang’ana dzanja la mbuye wace, momwemo maso athu ayang’ana kwa Yehova Mulungu wathu, kufikira aticitile cifundo. 3 Tichitileni chifundo, Yehova, timveleni chifundo, pakuti tazuliwa na manyazi. 4 Ndise bozula na manyozo ya bachipongwe na minyozo pa bozimvela.