12
1 ndipo yona anapempela kuli YEHOVA MULUNGU wake mumimba ya nsomba. 2anakamba, ''nina itana YEHOVA pa vuto yanga ndipo ana niyanka; kuchokela mumimba mwa nsomba nina lilila tandizo! munamvela liu yanga.
34
3 mwenze munani ponya mukati pansi, mukati mwa mutima wa nyanja, na chimpepo chinani zunguluka; -----------------------------------------------------------------------------------------. 4ninakamba.' na pishiwa kuchosewa pa manso panu; koma futi niza yangana kufupi na tempele yanu yoyela.'
56
5manzi yana nivalila mukosi wanga wonse; kuzama konse kunani zunguluka; mauzu yamu nyanja ya nani pomba mutu. 6nina yenda kunyansi nyansi kwa ma pili; ziko na vi nsimbi vake vinani valililatu. koma muna leta moyo wanga kuuchosa muchi mugodi, YEHOVA, MULUNGU wanga!
78
7pamene moyo wanga unakomoka mukati mwanga, nina itana YEHOVA kumaganiza; ndipo pempelo yanga ina bwela kuli imwe, ku tempele yanu yo yela. 8ba ika nzelu ku ku tumilungu tulibe pindu pamene batailila kukulupilika kwa pangano.
910
9 koma kuli ine, nizapeleka nsembe kuli imwe na liu yo kamba zikomo; niza fikiliza vamene nalumbila. chipulumuso chichokela kuli YEHOVA!'' 10 ndipo YEHOVA anakamba na nsomba, ndipo inaluka yona pa ntaka yo yuma.