MUTU 27

1 Yobu anapitiliza kukamba na kuti, 2 "malinga Mulungu ali na moyo, wamene atenga ciweluzo canga, Wampamvu, wamene apanga moyo wanga kubaba, 3 pamene moyo wnga ukali muli ine, na kupema kwa Mulungu kuli mumpuno mwanga, ici ndiye camene nicita. 4 Milomo yanga siyazakamba voipa, kapena lilime yanga kukamba vaboza; 5 sinizavomela kuti imwe batatu mykamba va zoona; mpaka nikafe sinizakana cilungamo canga. 6 Nizagwilila kuli cilungamo canga ndipo sinizacitaya; maganizo banga sibazanivomeleza (siabanikumudwisa) malinga nili na moyo. 7 Lekani badani banga bankale monga ni muntu woipa; lekani anyamuke bamene banukila momga ni muntu alibe cilungamo. 8 Pakuti niciyembekezo ca bwanji ca muntu alibe Mulungu pamene Mulungu amujuba, pamene Mulungu atenga moyo wake? 9 Mulungu azakamela kulila kwake pamene mavuto yabwela pali eve? 10 Azazikondwelesa muli Wampamvu na kuitana pali Mulungu ntawi zonse? 11 Nizakupunzisa pali kwanja kwa Mulungu; sinizaulula za maganizo ya Wampamvu. 12 Yangana, monse imwe mwaona ici mweka; mukambilanji ivi vonse vilimeke nchito? 13 Iyi in gawo ya muntu woipa na Mulungu, cotenga ca ovutisa camene ovutisa alandila kucokela kuli Wampamvu: 14 Ngati bana bapaka, ni bamupeni; bana bake sibazakankala na vakudya vokwalanila. 15 Baja bamene bazapuluka bazashikiwa na matenda, na ofewa bao sibazalilila. 16 Angakale kuti muntu woipa aunjika siliva monga ni dothi, na kuunjika vovala monga ni matika, 17 angaunjike vovala, koma bantu bolungama bazavivala, na bantu bosacimwa bagabana siliva pakati pao. 18 Amanga nyumaba yake monga ni kangaude, monga kanyumba kamene wolaonda apanga. 19 Agona pa bedi wolemela, koma sazapitiliza kucita izo; Asegula menso yake, na vintu vonse vayenda. 20 Voyofya vimuteng (vimupitilila) monga ni manzi; usiku cimpepo cikulu cimamutenga. 21 Mpepo ya kumumawa imamutenga, ndipo amanyamuka; imamucosa pamalo pake. 22 Imaziponya pali eve ndipo simaleka; amayesa kuzimasula mu kwanja yake. 23 Imamuombela mu manja na kumuimbila mufyoli kumucosa pamalo pake.