1
Yahova anaikako nzelu kuli Sara monga mwamene ana kambila, na Yahova anachitila Sara vamene ana kamba.
2
Sara ana nkhala na mimba nakubala mwana mwamuna wa Abrahamu mu ukhalamba wake pa nthuwi yamene Mulungu ana kamba.
3
Abrahamu anamu pasa zina mwana wamene kuli eve, wamene Sara anamu balila, Isaki.
4
Abrahamu anamu duka mwana wake Isaki pamene ana kwanisa masiku eiti, monga mwamene Mulungu ana lamulila kuli eve.
5
Abrahamu anali ana zaka handiladi pamene mwana wake Isaki anabandwa.
6
Sara anati, " Mulungu ani lengesa ku seka; bonse banza nvela baza seka naine." Ni ndani ana ganizila kuti.
7
Ndiposo Sara anati, " Ni ndani ana ganizila kuti Sara anga nkale na bana koma namu balila mwana mwamuna mubu nkalamba wake.
8
Mwana ana kula nakuleka ku nyonkha ndipo Abrahmu ana panda chikondwelelo chacikulu pamene ana siya ku nyoka Isaki.
9
Sara ana ona mwana wa Haga waku Egipito, wamene ana balila Abrahamu amuseka.
10
Tsopano anati kuli Abrahamu, " Mu choseni pano kapolo na mwana wake, chifukwa mwana wa kapolo saza nkala oloba pamodzi na mwana wanga Isaki."
11
Ichi chinamu nkalila chomu vitisa abrahamu chifukwa cha mwna wake.
12
Ndipo Mulungu anati kuli Abrahamu, " Osa nkala ovutisiwa chifukwa cha mwana, na kapolo wako. Nvele mau yake yonse yamene akamba pali iyi nkani, chigukwa ni muli Isaki mwamene bonse bodwa bakupaza pasiwa zina.
13
Ndipo niza pangaso mwana wa kapolo mukazi ziko, chifukwa nobo badwa wako.
14
Ndipo Abrahamu anacita kuseni, naku tenga mukate na chikumba cho tengelamo manzi, naku pasa Haga no ika mwana pamusana pake. Ana yenda ku chipululu ku Bereseba.
15
Pamene manzi yanasila muchi kumba cho tengamo manzi, anasiya mwna munsi mwa mtengo.
16
Ana yenda, ankala patali na mwana, mutunda wa Muvi, anazi kambisa eka, nisaoneko kufa kwa mwana wanga, "' Ndipo ana nkalapo oneka naye, ana bwela ayamba kulilamo kuwa.
17
Mulungu anamvela kulila kwa mwana, ndipo mungeli wa Mulungu anaitana kuli Haga ku chokela ku mwamba, naku kamba kuli eve, "Ni chani chaku vuta, Haga? Osa yopa chifukwa Mulungu anamvela kulila kwa mwana kwamene alili.
18
Nyamuka imika mwana nakumulibisa: chifukwa Nizampanga eve kunkhala ziko ikulu.
19
Ndipo Mulungu anamu segula menso, nakuona chisime cha manzi. Ana yenda nakuika manzi muchi tumba cha manzi, no pasa mwana kumwa.
20
Ndipo Mulungu anali mwana uja, ndipo ana kula. Ana nkala mu chipululu Nunkhala wopaya nyama.
21
Ana nkala mu chipululu cha Parana, ndipo amai bako anamu tengela mukazi waku malo ya Egipito.
22
Ina fika ntawi pamene Abimeleki na Fikolakulu ankonda ana kamba kuli Abrahamu kuti, "Mulungu ali na iwe mu vonse vamene uchita.
23
Tsopano vomele na ine pa Mulungu kuti suza chita boza na ine, olo bana banga nangu bonse bo badwa kuli ine. Ni langize malo yemene unali ku nkalamo monga wachilendo mubu bwino chimozi mozi.
24
Abrahamu anati, "Na vomela."
25
Abrahamu ana dandaula pali chisime chamene anamupoka kuli anchito ba Abimeleki.
26
Abimeleki anati, " Siniziba wamene ana chita ivo. Koma futi sunai uzepo; panka apa manje."
27
Ndipo Abrahamu ana tenga mbelele na ng'ombe naku pasa Abimeleki, na amuna abili naku panga chi pangano.
28
Tsopano Abrahamu ana tenga bana ba mbelele seveni zikazi naku zi ika [a zeka.
29
Abimeleki anati kuli Abrahmu, " Tantauzo ya izi nyama zamene wa ika pa zeka ni chiyani?
30
Ana yankha tenga mu manja mwanga zizani nkalila umboni, kuli nina kumba chisime."
31
Ndipo malo aya anaya ita beresheba, chifukwa bonse babili bana panga lonjezo.
32
Ana panga ma panyano pa Beresheba, na Abimeleki na Fikol, mukulu wa nkonda, ana bwelela ku malo ya filisiti.
33
Abrahamu ana shanga chi mtengo cha tamariski ku Beresheba. Napamene apo ana pempeza Yahova, wamuyayaya Mulungu.
34
Abrahamu ana nkala wachi lendo mu malo ya Filisiti masiku yambili.