Mutu 33

1 Iyi ndiyo daliso yamene Mose kapolo wa Mulungu anadalisa bana ba Israeli akalibe kumwalila. 2 Anakamba: Yehova anachokela ku Sinai nakunyamuka kuchoka ku Seir pali beve. Anawala kuchoka ku pili ya Parani, nakubwela nabali teni sausandi woyela. Kukwanja kwake kwa manja kunali kunyemizila kwatuleza. 3 Zoona, akonda banthu; bonse banthu bake woyela bali mu manja yako, ndipo banagwada pansi mamendo yako; banalandila mau yako. 4 Mose anatilangiza lamulo, mu cholowa cha wosonkana ba Yakobo. 5 Ndipo kunali mfumu ku Jeshurn, pamene basogoleli ba banthu banakumana, yonse mitundu ya Israeli pamozi. 6 Lekani Rubeni ankale naumoyo asafe, koma lekani bamuna bake bankale bang'ono. 7 Iyi ndiyo daliso ya Yuda. Mose anati: Yehova, nvelani, mau ya Yuda, nakumubwelesa ku banthu bake nafuti. Mumenyeleni; nkalani tandizo yake mosusana na badani bake. 8 Pali Levi, Mose anati: Zovala zako zaunsembe zizankhala za awo ali wokulupilika pakati pa iwe, bamene banayesedwa ku Massa, bamene unavutika nawo ku manzi yaku Meriba. 9 Mwamuna wamene anakamba pali batate bake na mai bake, "Sininabaonepo." Ndipo sanazibe babale bake, ndipo sanazibe chibelengelo cha bana bake. Chifukwa analanganila mau yanu na kusunga chipangano chanu. 10 Amapunzisa Yakobo malangizo yako na Israeli lamulo yako. Azaika nsembe pakati pako na nsembe zoshoka zonse pa guwa. 11 Dalisani, Yehova, yonse katundu yake, na kuvomela nchito za manja yake. Pwanyani mafupa yamumusana ya bamene bamunyamukila, na abo banthu bamene bamuzonda, kuti basakanyamuke futi. 12 Pali Benjamini, Mose anati: Okondedwa na Yehova ankala mu kuchingiliziwa kwake; Yehova amuchingiliza siku lonse, na kunkala pakati pa manja ya Yehova. 13 Pali yosefe, Mose anati: Lekati Yehova adalise malo yake navinthu vabwino vakumwamba, na mame, na zapansi. 14 Lekani malo yake yadalisike na vinthu vabwino vakukolola nakazuba, na vinthu vabwino vochaka mumwezi, 15 na vintu vabwino va mapili yakudala, na vinthu vabwino va mapili yamuyayaya. 16 Lekani malo yadalisike na vinthu vabwino na vambili va paziko lapansi, navabwino kuli uyo ali musanga. Lekani daliso libwele pamutu wa Yosefe, na pamwamba pa pamutu wa uyo anali wobadwa ku ufumu pasogolopa babale bake. 17 Mwana woyamba kubadwa wa ng'ombe, ndi wamkulu, ndipo nyanga zake ndizo nyanga zamphongo. Ndi iwo akankha anthu, onsewo, kufikira malekezero adziko lapansi. Awa ndiwo zikwi khumi za Efraimu; awa ndiwo zikwi za Manase. 18 Za Zebuloni, Mose adati, Kondwerani, Zebuloni, potuluka iwe, ndi iwe Isakara, m'mahema ako. 19 Adzaitanira mitundu ya anthu kumapiri. Kumeneko adzapereka nsembe zachilungamo. Pakuti adzayamwa kuchuluka kwa nyanja, ndi mchenga wa m'mbali mwa nyanja. 20 Za Gadi, Mose adati, Wodala iye wakulitsa Gadi! Adzakhala momwemo ngati mkango waukazi, ndipo adzakhadzula dzanja kapena mutu. 21 Anadzipezera gawo labwino kwambiri, popeza panali gawo la mtsogoleriyo losungidwa. Iye anabwera ndi mitu ya anthu. Anachita chilungamo cha Yehova ndi malemba ake ndi Israyeli. 22 Za Dani, Mose adati: Dani ndi mwana wa mkango yemwe adumpha kuchokera ku Basana. 23 Za Nafitali, Mose anati, Nafitali, wokhuta chisomo chake, wodzala ndi dalitso la Yehova, alandire dziko kumadzulo ndi kumwera. 24 Ponena za Aseri, Mose anati: “Aseri adalitsike koposa ana ena onse; akhale wololeka kwa abale ake, ndipo aloŵetse phazi lake m'mafuta. 25 Mizati yanu ikhale yachitsulo ndi yamkuwa; malingana ngati mudzakhala masiku anu, chitetezo chanu chidzakhalabe. 26 Palibe wina wonga Mulungu, Yeshuruni, woongoka, amene akwera kumwamba kukuthandiza, ndi muulemerero wake m'mitambo. 27 Mulungu wamuyaya ndiye pothawirapo, ndipo pansi pake pali mikono yosatha. Iye adathamangitsa adani pamaso panu, ndipo adati, "Ononga!" 28 Israeli amakhala mosatekeseka. Kasupe wa Yakobo anali wotetezeka m'dziko la tirigu ndi vinyo watsopano; Ndithu, thambo lake ligwetse mame pa Iye. 29 Madalitso ako achuluka, Israyeli! Ndani angafanane ndi iwe, anthu opulumutsidwa ndi Yehova, chikopa cha thandizo lako, ndi lupanga la ukulu wako? Adani ako adzabwera kwa iwe akunjenjemera; Iwe udzapondereza malo awo okwezeka.